Oimba omwe ananyozapo Bushiri

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 7 вер 2024
  • anthu omwe anaimbapo nyimbo zonyoza bushiri

КОМЕНТАРІ • 242

  • @sammalvitha
    @sammalvitha  Рік тому +13

    Zikomo poonera, chonde Ngat simunachite subscribe.. kumbukiran kutero ... Muchite like ...video iyi .... Zikomo

  • @harryhara6217
    @harryhara6217 Рік тому +7

    Oyimba onse amanyoza Bushiriwa, nkhani,yake ndi umphawi. Iwowo amafuna kukhala oweruza?ine si fan wa Bushiri and i've never been. Koma sindingamamuweruze.

  • @keniekaipa1997
    @keniekaipa1997 Рік тому +3

    Mbuzi iwe umanama......usiye kupanga za anthu

  • @RahmahMussa
    @RahmahMussa 5 днів тому +1

    Kodi bwanji mumazimva kuzindikira bigy kungofuna basi kulimbana ndi oyimbawa muungofuna kuwalakwitsa aaaaaàh

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Рік тому +3

    Very much Best bro please ceep it up good job bro

  • @ashraffmidu7837
    @ashraffmidu7837 Рік тому +11

    Piksy didn't liar he only says the truth moreover that song of him it's my favorite song....akutithera mtundu m'malawi ameneyo...#MartseKeepRip😥

  • @user-tf2ri2sl5s
    @user-tf2ri2sl5s Рік тому +2

    Thanks for your true report about the Prophet Shepherd Bushiri and his beloved wife (Prophetess... As well as the Malawian musicians who composed their music despising, criticize, or contempt the Prophet Shepherd Bushiri!!! Anyway... Only God knows... HE'S THE RIGHTEOUS GUDGE IN HEAVEN AND AND ON EARTH.

  • @chrissjunior8342
    @chrissjunior8342 Рік тому +5

    Proudly you my brother " nd nkhan ngat zmenez 🤟

  • @judywilliams2349
    @judywilliams2349 Рік тому +5

    That’s true, blood money. Magician full time.

  • @AuthenticV
    @AuthenticV Рік тому +1

    Pastor David Kalirani Amayenera kukhala pa number 1

  • @musicoftheviolinstudios.1109
    @musicoftheviolinstudios.1109 Рік тому +4

    zofotokoza zanu zili bwino,ndizosakolana zachindunji bwino bwino.mulipo awiri ndi big mani enake samazitchula dzina lake .

  • @JuniorAbasi-eb5ce
    @JuniorAbasi-eb5ce 10 місяців тому +1

    A Malawi ife tilibe ulemu Mr Bushiri zawo dzidayela khale chofunika ndi ulemu basi monga ine ndikuti ulemu wanu mr Bushiri .kodi A Malawi tinakhala bwanji munthu aliyitse akalemela.ali ndi vuto

  • @judywilliams2349
    @judywilliams2349 Рік тому +5

    That’s true, Bushiri is a magician and I can’t understand how people are so brainwashed.

  • @rasheedjaffali6674
    @rasheedjaffali6674 Рік тому +1

    Nice one brood good work

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 Рік тому +3

    Ndi zoona bro

  • @gracephiri1203
    @gracephiri1203 Рік тому +2

    Mwaitha bro muzibwelabwela

  • @mosesjoni2542
    @mosesjoni2542 Рік тому +2

    Best one bos

  • @user-qk9ib7hb4l
    @user-qk9ib7hb4l 11 місяців тому +1

    That's very gorgeous

  • @fradahmakwinja3835
    @fradahmakwinja3835 Рік тому +5

    Major one is Great

  • @Ishriss1999
    @Ishriss1999 Рік тому +4

    Koma Mthuzi ija simaseweratu 😂🙌

    • @sammalvitha
      @sammalvitha  Рік тому

      Anaswa

    • @hanifrego2744
      @hanifrego2744 Рік тому

      True chilugamo akuchiziwa iye urendo wa kumwamba ndi one one so let God be God

  • @AffectionateFoliage-gh6bf
    @AffectionateFoliage-gh6bf 7 місяців тому +1

    Keep it up

  • @thembalungani9347
    @thembalungani9347 Рік тому +3

    proud to him man of God...enawa yakula ndi nsanje...m'nyamata ali ndi mphatso ya utumiki uyu congratulations to major 1

  • @renardnguluwe7914
    @renardnguluwe7914 Місяць тому

    Ndazkonda❤

  • @BlessingspMponda
    @BlessingspMponda Місяць тому

    Kodi ndindan amene samaziwa zot namadingo ndi bushir amadana

  • @jaymilazi2937
    @jaymilazi2937 Рік тому +4

    Muzibwezerabwera ndi nkhani ngat izi

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 Рік тому +1

    Wasatanic uyu, ngozi mmene zikuchitikira ku malawi mukuyesa ndi chani, ngozi zoopsya zikuchitikazi chibwerere bushiri kumalawi, magazi akuwukha mwakathithi anthu akufa moopsya and tinanena bushiri atangobwera ku malawi, kuzichitika ngozi zoopsya munthu Wasatanic ameneyi akabwera.

    • @mastersubiri7934
      @mastersubiri7934 Рік тому +1

      True that brother

    • @ipyanamwanyongo4169
      @ipyanamwanyongo4169 Рік тому +1

      Yes was satanic uyo too since Ali ku Malawi everyday I hear accident why her please bro don't defense him hey,but follow Jesus Christ not men

  • @kalunguhelias
    @kalunguhelias 5 місяців тому +1

    I've ukutiuza za bushir KT titaninaye

  • @eliasleonard9448
    @eliasleonard9448 Рік тому +2

    Moyo ndikamozi ndagwirana ndinamdingo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 11 днів тому

    Atapempha ndalama ndikuwakaniza amangotukwana. Moses makawa anavomera kuti ndi mfiti pa radio.

  • @peterjcndolo5644
    @peterjcndolo5644 Рік тому +3

    I like him, he has a humanitarian motivation, big up Shepherd Bushiri. Ngati zintchito ndizonyasa kuseli let God do His of Judging

  • @NIDYBANDA-iz7xz
    @NIDYBANDA-iz7xz Рік тому +2

    Km mwatzindkilisa zambili man sam

  • @amontchuwa6876
    @amontchuwa6876 Рік тому +1

    Nanga iwe ukt bwanji
    Ine ai akuziwa ndi Yahweh

  • @user-gr6zh9zr9b
    @user-gr6zh9zr9b 10 місяців тому +1

    TNM super rige malawi

  • @NavitchaBanda
    @NavitchaBanda 2 місяці тому

    Mukasowa chati usamalimbane ndi man of god

  • @ChesterBanda-qm8fh
    @ChesterBanda-qm8fh 11 місяців тому +1

    Fire up otsogoleri

  • @MercyMachipisaMunthali
    @MercyMachipisaMunthali 4 місяці тому

    Ndimamukonda Bushiri chifukwa samanyoza munthu sayakhula mau opusa kwa munthu. Inu muli Holly lnu mukumaimba nyimbo atsikana atavula ndee oipisisa lnu mwawalimbikisa athu kut God will bless them kapena mwawatengerathu kwasatana

  • @hamdanmasuku4800
    @hamdanmasuku4800 Рік тому +2

    Timakunyadilan bro nkhan zkumveka bwn kwambiri✊👏

  • @user-id7dj6uk7t
    @user-id7dj6uk7t 5 місяців тому

    Piksy ndi mfauna oziwika ndi bouma😂

  • @KimuBanda
    @KimuBanda 5 місяців тому

    Tnx for the good report

  • @ibulakimu9380
    @ibulakimu9380 Рік тому +1

    Enewa ndi zanje

  • @MercyMachipisaMunthali
    @MercyMachipisaMunthali 4 місяці тому

    Tose tapachalu chapasi ndise wakuchimwa Bushiri nayo wali ngat lwee pala wamanya lchi suzapanga zamuthu uzamukonda kwa mbiri. God bless Bushiri so that forex yisamasowe lfeso tikapulumusike

  • @stevinmuhone877
    @stevinmuhone877 Рік тому +3

    Machitidwe awo abushiri ndi amene tikuti samapemhphera mlungu ndipo ine sindizawakhulupirirapo ata

    • @hanabrighton9903
      @hanabrighton9903 Рік тому

      Alandililatu pasipano ameneyo kumwamba kulibe mark my words

    • @hanabrighton9903
      @hanabrighton9903 Рік тому

      Ineso chimodzimodzi alikuti Gracy Chinga cz of him ulemuumene mukuunenawo ndiyekuti mphotoyake

  • @sonnymasandi1748
    @sonnymasandi1748 Рік тому +1

    Ndayikonda so much keep up agood work

  • @user-ir1mp1cd1c
    @user-ir1mp1cd1c 28 днів тому

    Nambululuka, mwaiwala kuti amambululuka koma alibemapikp .

  • @michaelkhunga3676
    @michaelkhunga3676 Рік тому

    keep it up .though am late to comment

  • @twarichissah4222
    @twarichissah4222 Рік тому +1

    Nyimbo ya namadingo ya wabwela muli uthenga wabwino kwambiri ndipo kwa munthu wawumunthu pamenepo Palibe vuto lililonse 🤔🤔

  • @zainabchikakuda6297
    @zainabchikakuda6297 Рік тому

    Komatu bushir ngodekha akayankha ndiye kuti zavuta mmmmh

  • @user-sc1ef6bb8i
    @user-sc1ef6bb8i Рік тому

    ATHU AMAMUNYOZA BUSHIRI CZ CHUMA CHAKE CHOCHOKERADI KWAMULUNGU (ziwan kuti Dziko lapasi limadana ndizochokera kwayehova}

  • @godfreybiziweck1224
    @godfreybiziweck1224 Рік тому +1

    Ndizoonadi anamunyoza prophet shepherd bushiri

  • @rhodrickchingoli3636
    @rhodrickchingoli3636 Рік тому +1

    aMalawi timakodwa wina akamavutika

  • @daudigodfrey1369
    @daudigodfrey1369 Рік тому

    Nde kuuluka mwamba ndiphamvu yaumulungu ndiyesu yekha adapang zimenezija aise plibeso akuenera kupang paziko lapasi

  • @yusufelliotanalidodoloooma9685

    Chimandisangalasa ndichoti bushiri utsogoleri ali nao sapsa ayii. Anthu ndie amathoka zaiye siku ndi siku. Koma mumpeza Alii pee . Iye bola ubale wake ndi mulungu uli bwino

  • @kennedykamoto5068
    @kennedykamoto5068 6 місяців тому

    Umakwana sam

  • @user-tu6ph6wh2z
    @user-tu6ph6wh2z Рік тому

    I like him he has a humanitarian

  • @lysonkumbwezaabdullah6075
    @lysonkumbwezaabdullah6075 Рік тому

    pamenepo zoyamikila zake ndi ziti

  • @frankleeliwonde6221
    @frankleeliwonde6221 Рік тому +1

    Namadingo sanalengezepo kuti wasiya kuyimba nyimbo zauzimu

  • @KatsekelaHassan
    @KatsekelaHassan 4 місяці тому

    Am still love bushiri

  • @PatsonSaiwala
    @PatsonSaiwala 2 дні тому

    😂😂😂 kodi zotelo

  • @shonmikemtawa3262
    @shonmikemtawa3262 Рік тому +1

    Ose oyimba sangakhare obonza koma ndi zen zen izi

  • @MabvutoManjolo-hl6px
    @MabvutoManjolo-hl6px 11 місяців тому

    Number one bushili

  • @MadjidMatola
    @MadjidMatola 5 місяців тому

    Za zii kumangolimbana ndi anthu, that's sighn of poverty 😢

  • @tawanisolungu
    @tawanisolungu Рік тому +1

    Great

  • @user-mc9ce2ug7g
    @user-mc9ce2ug7g 5 місяців тому

    Simungapezemo ndalama

  • @AmosNephan
    @AmosNephan 4 місяці тому

    Bushili ndinthu wabwino kwambiri

  • @JenniferRonnex
    @JenniferRonnex 4 місяці тому

    Haji❤

  • @Daudaustin556
    @Daudaustin556 Рік тому

    Lelo apiksy omweo kulandila ndalama Za yemweo akafuna kupepha kumangopepha Osama lankhula zopusa amafo nde awo nawo Ali khwekhwere konko

  • @user-ur1uh4sr7k
    @user-ur1uh4sr7k 10 місяців тому

    God will judge am just a mere person and our lord said let millet grow together with glass separation shall be done at the end

  • @collinsassenga3711
    @collinsassenga3711 Рік тому

    Ngati ndi wasitaniki mulung ndiye adzamuweluza, osati ine kapena iwe, chotsa chitsotso chili mmanso mwako, uwona bwanji chitsotso chili mmanso mwamzako, chako usanachotse.

  • @EnockNyirenda-nr2uj
    @EnockNyirenda-nr2uj 2 місяці тому +1

    Ayizikomo

  • @evasakelebone3144
    @evasakelebone3144 Рік тому

    Mmmmmmh mmmmh ndizapamwambadi well explained

  • @user-iu4kk6em5k
    @user-iu4kk6em5k 11 місяців тому

    Thax for information❤

  • @tamarachipokosa9633
    @tamarachipokosa9633 Рік тому +1

    Muchedwa nazo limbikirani ntchito

  • @user-bh7xr1hz5t
    @user-bh7xr1hz5t 11 місяців тому

    😂😂😂😂😂 chilungamo chimawawadi anthu a bushili akuwoneka olusa tuu samala aise

  • @HAWAHANDRWE
    @HAWAHANDRWE Рік тому +2

    Zikomo kwambili sam malvitha zaveka bwino

  • @BornfaceMbewe-dr8id
    @BornfaceMbewe-dr8id 3 місяці тому

    zikomo mupitize kusokola nkhani zotele nizofunika koposa

  • @ashiamaziti6523
    @ashiamaziti6523 Рік тому

    Nice video

  • @romanslungu
    @romanslungu Рік тому +1

    Proud of u

  • @MatiasRaphael-dl7yu
    @MatiasRaphael-dl7yu 3 місяці тому

    Anthu timakhulupilila ma prophet omwe anamwalila koma munthu yemwe timamuona zimakhala zovuta kukhulupilila komabe Pali mau Oti munthu sachuka Dela la kwao anthu azakhulupilila kuti bushiri analidi munthu wamulungu atamwalila ambili omwe Amati bushili simunthu WA mulungu sawelenga malembo oyela ngati ndioipa mulungu ndiyemwe angaone kuti akuchita choipa osati inu AI

  • @FauvorJohn-kp7yh
    @FauvorJohn-kp7yh Рік тому

    Athu ena samakodwera akamachita zabwino padziko rapasi mzawo.
    BUSHILI NDI MUNTHU WABWINO KWA MBIKI OK

  • @MercyMachipisaMunthali
    @MercyMachipisaMunthali 4 місяці тому

    God have mercy on you

  • @user-ym5jy9vl4f
    @user-ym5jy9vl4f 6 місяців тому

    Adha pasanapako ndwe galu kwambili Kod kusowa nthito ndkomwe kukuchititsa eti

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 Рік тому +1

    Adzabwera ngati akhristu koma kuti adzanyenge ochuluka.Mawu awa ali mu bible koma anthu eti kakakakaka

  • @bunayatambala310
    @bunayatambala310 Рік тому +1

    This is true 💯💯💯💯
    There is no way to like him this is Deval stan blood money God will fire him 🤞🤞🤞🤞🤞 he must repent en come back to Islam the truth he knows en Islam is straight way to go pradise plz plz bushir come back to Islam before judgement

  • @RaimundoMuquiale-yc7lf
    @RaimundoMuquiale-yc7lf 9 місяців тому

    Koma ndiye

  • @jamesbanda5633
    @jamesbanda5633 Рік тому

    Osamanyoza atumiki amulungu

  • @NjabuloMKhize501pro
    @NjabuloMKhize501pro 2 місяці тому

    Pwedo

  • @thadzaone6039
    @thadzaone6039 Рік тому

    Ananyozedwa yesu Christ bushiri ndi ndani oti asanyozedwe??? Chomwe muziwe zonse ndi zosala ndalama kuimba bwino kutchuka kulemela koma ngati zonsez tikupanga yesu mkati mwathu mulibe mmmmm tiyeni tigwile yesu molimbika basi ,,

  • @MercyMachipisaMunthali
    @MercyMachipisaMunthali 4 місяці тому

    Bushiri is man of God why God created us on his image don't judge. Just saying is not man of God 1. Ur selfish
    2.wachokapo pamaso
    pamulungu
    Only God will justify us let love one another don't trust a man trust in God.

  • @AnnahNyirenda-gl1ke
    @AnnahNyirenda-gl1ke Рік тому

    Love it

  • @user-rd3ml9qw2x
    @user-rd3ml9qw2x Рік тому

    Be careful with a word of God and don't make a mistake to follow wrong things that you will know that this is a wrong. read jobs 13 verse 14

  • @DeOffice-zz7rb
    @DeOffice-zz7rb 11 місяців тому +1

    Like

  • @danielkhinguirossejuliasse1214

    Ina ija amati musamamange nhumba kwapongozi

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 11 днів тому

    Moses Makawa anavomereza kuti amatamba pa radio. Pamenepo wasatanic ndi ndani? Bushiri sindimamutsata koma Bushiri sananene kuti iyeyo ndi otamba.

  • @user-qo9dp7vv5s
    @user-qo9dp7vv5s Рік тому

    So nice

  • @user-ru4mq5bw8i
    @user-ru4mq5bw8i 11 місяців тому +1

    Only God knows

  • @user-xq9pb7en2g
    @user-xq9pb7en2g 8 місяців тому

    Sanamunyoze koma chilungamo

    • @BraveMunyanga
      @BraveMunyanga 5 місяців тому

      Vuto anthu amafuna azikhala mbali ya olemelayo which is totally wrong

  • @judywilliams2349
    @judywilliams2349 Рік тому +3

    I have no respect for the magicians. I can’t understand how people are so brainwashed. God help us.

  • @isaachara1861
    @isaachara1861 Рік тому

    Bushiri Salimbana ndi mafana opanda vision

  • @neptunedefia656
    @neptunedefia656 Рік тому

    Ndiwe chisiru iwe chikukukhuza ndichani, or ine ndithanso kuimba zomwezo chifukwa iwo apulofeti anuwo ndiaboza

  • @user-bm5fi7ui2g
    @user-bm5fi7ui2g Рік тому

    Tikufuna Ena ngat mbiri ya bushiri