Koma oimba ndioimba basi amwene...I was not expecting this massive production and composition from Mlaka at this age...ndaimika Manja! Ndinu amfumudi..kumonkeybay kunadala kutulutsa machine a music...
Mulaka maliro you are too much this is good music. Much love from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲 I love the reggae instrument 🎸🎸🎷🎷🎷🎸🎷🎷🎷 in it.
Mlaka maliro fan's let's gather her.. let's give it more fire 🔥🔥
Makina !!!! Nyimbo yalembedwa ndikuyimbidwanso mwaluso ,,,salutes Biggy
Koma 🤔 ndi dolo baleyu😂😂
It is well
Powerful 🎉🎉
Inu ndi oimba , respect 🙏 👏
Ambuye alemekezeke
Inu munabwera kuzaimbad
.legend
This guy eish palibeso....nyimbo zomvela anthu oganiza bho....🎉
Man 2mbi u r star komano pokhapa pomutchula kamunthu aka kotchedwa Chakwera waipitsa nyimbo yako yonse
This is massive. Akulu awawa was born to sing. Everything in this song is perfect, the voices, the beat, the quality etc. Mlaka will always be Mlaka
Those who are listening on repeat please gather here I begoooo😊
Listening while driving all the way in Washington State 💃💃🔥🔥
Abale nkhalani anzanthu please nafeso timafuna kumacheza ndi anthu aku America please
Can I have your phone number or email please
Amen,ndipo yasowa ndodo eeish
More fire Mlaka uthenga wafika ku capital hill
Eish mulaka ukachedwa kt tinakusowani big nyimbo iyi ikungofanana ndi ija ya dzaja lalemba❤
Ati ngati kotheka muzandikumbuke mu ufumuwo❤❤
Mlaka ndi Mlaka basi...beautiful singing
Mlaka ndi mlaka basi 🎉🎉
Mlaka is mlaka... Mmodzi mwa oyimba omwe nyimbo zawo mumakhala uthenga wamphavu... And also meaningful
Wanva 🔥🔥🔥
Dholo🎉🎉🎉🎉
My favorite!!!!!!.... Talented @Mlaka Maliro
Ndipo yaweh awakanthe anthu akubawa. More fire Mr Mlaka. Ife tikulira chifukwa ndodo yasowa. Malo mwake tili ku Baga moyo😭😭😭😭😭. I love this song
Ku Mangochi amamutchula kuti CHE Mlaka ,one of my best musician ever ❤
Mlaka ndi mlaka...pure class act
Munthu wamkuku kuswa sound moganiza kwambili you deserve to be legend
😂😂😂 nice
The big man is born for this.....pastor mlaka you are great sir may the almighty God bless you....repeat all the way
Waphatu eeeeee🔥🔥🔥🔥
More fire mlaka ndi mlaka basi
Ana ama 2 sau ine kuimba kumafuna luso muzimva, on point Mlaka
❤❤ muli uthenga. Mlaka nd mlaka. Waluso nd waluso. Ukali wanu fada. Ng'alulan basi. Tikupitad ku Libia
Mlaka ndi mlaka bas nice tune
Yasowadi ndodo ya Moses ndimmene Malawi akuyenderamu Mmmm ..
Mlaka nfana oganiza mwakuya 🔥✨🤞
Akulu awa amaswa chilungamo ngati akulalikira, koma akuziwa yemwe akumponyela. Long live Mr mlaka
My legend now Mlaka ndi Mlaka basiii palibe chingamulake ndithu, great staff.
uyuyu amatha kuimba 🔥🔥🔥🔥❤
Yasowa basi ndodo ya moses... Tikhazikika mu bagamoyomu
that's Mlaka Maliro I knw akulu iyi mwapha🔥🔥🔥🔥
Zambians where are you?
❤️❤️
My favorite Gospel Artist is here
We're here
This legend never disappoints 🔥
Legend❤❤🎉🎉
Nili pakona
all here. Mlaka ndi Mlaka
Talented
Hey massive, song well done, mlaka ndi mlaka basi
Awa ndi machine pa nkhani yamayimbidwe 💪💪👍🤝🤝
Mlaka n3ver disappoint 🎉🎉🎉. Something new..
Watching from Lusaka Zambia 🇿🇲 👌 ♥️
Powerful message eish more 🔥
This is awesome mlaka ndi mlaka basi moto kuti buuuu
One of my favorite artist. Big up Mlaka
Wow. Well done Mlaka
Mlaka mlaka thumbs up man great music
Mlaka ndi mlaka, a true son of Nyasaland💥
Ndili pano kumvetsera mwachidwi yasowa on repeat 🎵🎵🎵
Waphaaaa mlaka
On repeat
Muraka ndi mulaka sabisala ngati oyimba enawa ❤❤❤❤🎉
That's good song an nice massage.kip it up more 🔥🔥🔥
Mlaka amatha kulemba nyimbo 🔥
Mlaka ndi Mlaka basi Chinyimbo ichi chili mbambande ❤❤❤❤
Team Mulaka never disappointed
Big man what a message 🎉🎉 malawi yasowa just imagine k6000 1kg of sugar akumanga nyumba ndi athu omwe ali kujoweni
Well done Mr Mlaka
Mbambande mlaka ndi mlaka basi🎉🎉🎉
Koma oimba ndioimba basi amwene...I was not expecting this massive production and composition from Mlaka at this age...ndaimika Manja! Ndinu amfumudi..kumonkeybay kunadala kutulutsa machine a music...
Zidaaazooo iiii yakanaka shwari wangu Mwari akubatire on iwee kkk ma 1
Blessed singer, good beat and msg
Okay this guy is on another level mmmm .
Keep it up we are behind you ❤ 💪
🎉🎉🎉 mlaka maliro good song
🎉🎉🎉 uyu ndi dolo
Mulaka maliro you are too much this is good music. Much love from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲 I love the reggae instrument 🎸🎸🎷🎷🎷🎸🎷🎷🎷 in it.
It's Mlaka Maliro not Mulaka Mulilo kkkkkk
Mlaka ndi Mlaka more 🔥🔥🔥, uthenga wamveka
Ndodo yasowa eeti😆😆😆😆
Viva Mlaka..nice song
🔥🔥🔥🔥 Mlaka ndi Mlaka
Receive your flowers 🌹🌼 while you can smell them......... great piece of music 👏👏👏
Mlaka ndi mlaka 🔥🔥🔥isowabwanji ndodo Eish apatu basi waku Libya
Mlaka Malilo best music God continue blessing you brother
Pple nice concept and it's tune 🎉🎉🎉🎉 yasowa fireee
Mwapha nyimbo iyi💪💪
Waaaaaaa woooooooo kuyimba kwa bwino
Keep tha fire burning ❤
AkaaL❤🎉
Mulaka ndimulaka basi nice one song
Mlaka ndi mlaka ❤❤❤❤❤❤
Fire mabomba 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Katundu! Maka is Mlaka❤!
This is carrie I know my dear brother, just keep it Monkey bay let's give fire , ndi bwino kudziwa pomwe wagwera mkubweranso pa carrie yako
Uyu ndimunthu wankulu 🔥🔥🔥🔥
Mlaka samakhumudwisa
good work pastor
More fire ,ulendo waku Canaan uja , wasokonezekadi apa....
Am blessed with this song I like and love it. Good hit
Uyu nde Mlaka timadziwaaa ifeeee
Nice song mr Mlaka❤❤❤
Nice song, ulemu wanu boss
He is on top of all musicians; sizongochoka pachiwaya chazigege nkumati ndine oyimba
More fire 🔥🔥🔥
Kodi ndiliudze motani dziko la Malawi kuti Mlaka akamapita ku Studio amakhala atakonzeka mokwanira. Mlaka supporters let's gather here timpatse mangolomera Munthuyu 🔥🔥🔥🔥🔊🔊🎶🎶🎸🎸🎸 🎹🎹 🥁🥁 🎤🎤
I salute you Mlaka, Mlaka li Mlaka and nobody does it better than u! More fire, yasowadi ndodo ija
Madzi auma Mlaka kkkk big up brother
Keep it up Mr Mlaka your the nomber one
Kkkkk this is the best jenz keep it up broo we are proud of u
Ulemu wanu bwana Big up
Yasowadi ndodo ya moses awakathe anthu akubawa sukunama mlaka ❤❤❤❤
Second verse...Full of wisdom❤
❤❤❤ big up Malaka maliro 😂
Yes man mlaka ndi mlaka basi
Nice one boss man
I mark my register and zoona ulendo uja wazondokera kulibia avikanthe ndimphenzi vanthu voipa ivi chilichonse chakwera Monga mwazina lawo😮
Mlaka ndi mlaka bas❤❤
Mumakwana bgy ❤❤
On repeat 🎉
Connected from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲