Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Man you are an impressive journalist. Keep it rolling
Achewa ndiye amachita bwino
Straight to the point a mdala awawa nd munthu anaimba phone wa onse nd mbanva 😂😂😂😂😂
Kuli ma ufumu ena 3 kuphatikizapo wa Malemia anthu akungokangana ndipo akapanga masewera apwetekana 😢
Phanani
Uyu mandala otsokonedza ophetsa
Za ufumu kawiri kawiri anthu amaphana zaziiii
Vuto ndaona ine apa ufumu unalakwika poyamba kalowesedwe wina akafa kupita ku banja lina akafa uyu kupitanso kubanja kwina izi izi ndi zovuta kwambili day ina olo awawa akazamva kukoma azakananso
Kod..muli chani mufumu kufuna zaulele bas
Zimafuninika zizingoyenda banja limoz
Ufumu ndiwositha ndimene mwakambilamo olo kwathu timatero ndipo zimayenda bwino popanda chovuta
Nkhan zake zovuta ndithu
Uyu madala alibe chilungamo mwana ndiwakulu angafotoze mbiri ndindan
2025 kukhala ndalama za campaign....pavuta apa
Nkhani zovuta izi
Zaufumu eeeeee zomvuta zedi anthu amaphana
Uyu wafotokoza pomalizayo ndi mbava yeniyeni
Zaziii zimene akukangana apa ,anthu amangofuna kuphana pa zinthu zaziiiì