CHINSINSI CHAKUGWIDWA KWA KALIATI KOMA CHIMENECHI - UWU NDIYE TIMATI UMODZI💪💪

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 45

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 2 години тому +2

    Mugwiri zano ndiomwewo ,dpp,aford 🎉🎉,watching from johnnsberg

  • @VioletMbale
    @VioletMbale 2 години тому +3

    Chi usi iwe ukutaniko kunyumba? Pa 17 iwe suuzakhala wa utm manyazi

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu Годину тому +1

    I see we are going to one party system Malawian we must be careful eshiii

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 49 хвилин тому

    Eeesh

  • @YusufKazembe-po6qo
    @YusufKazembe-po6qo Годину тому

    Iwe galu Michael Usi ndiamene wapangitsa

  • @DigleDafter
    @DigleDafter Годину тому

    Yooh yooh 😢 Malawi okomera tonse unja alikuti lero ndiolose ndikakutafune palibe chosatha 😢

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi Годину тому

    Ife kumalawi pheeeee kusuzumila pa zenela kuyang'ana siku lamovoti koma uyelekeze kibbela ndikudula mabatile

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga Годину тому

    Amipingo mulikuti mukufuna mpaka muyakhule anthu atafika pakuphana aPac mwatani chani moti simukuona zosezi km ndarama guys snapanga aaaaa hiiiiiiiiiiiiii manja kt buuuu kalulu nkanyama kochejera km kamanyedwa ok

  • @OwenchangnyaMkandawire
    @OwenchangnyaMkandawire Годину тому +1

    Mcp ndizitsiru za anthu.anazolowera kupha anthu amenewo.mademo basi kuotcha tima police stations tonse.

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 години тому +2

    MCP kuti mupeze mtendere mumange aliyense osusa osaiwal inenso ndiosusa mukudziwa kale zimene mukupangazi palib chopindula koma minyama yokha yokha

  • @GidionLufani
    @GidionLufani 2 години тому +4

    Palibeso kubisa mwanganya ameyo

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga 14 хвилин тому

    Walila mokweza mzimayi olalata uja kuno

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 28 хвилин тому

    Police 😊

  • @DanielTwiscombewe
    @DanielTwiscombewe Годину тому

    😂😂 apolisi mufela ndalama zot simukwanitsa kuzidya mufela kukakamiza kt dziko likhalebe lovutika ok tiyeninazon

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft Годину тому

    Manganya ndi chakwera mukutenga dzikoli ngati lanu eti

  • @TimothyKabumbuKendrix
    @TimothyKabumbuKendrix 2 години тому

    Nthawi yakwanatu yamademo guys more fire osaopa, osaopa komanso osafooka.

  • @ClementMakasu
    @ClementMakasu Годину тому

    Amasulidwe

  • @WakisaNjeghenje-i2n
    @WakisaNjeghenje-i2n 2 години тому +1

    Wina sakuziwa kut akaluza kucovion akufuna asokoneze basi😅😅😅MMM koma

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 2 години тому

    Manganya ameneyo ndiyemwe akuziwa kanthu akuwopa kukaluza komvetion

  • @FlorenceBanda-w5s
    @FlorenceBanda-w5s Годину тому

    Chomwe chikufunika tizigopephera bas marawi wayaka

  • @MACDONADLITIA
    @MACDONADLITIA Годину тому

    Tinaziona kale izi nthawi ya Bingu atamangidwa Atupele Muluzi ku Lilongwe komweko athu anagona ku police

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv 2 години тому

    Km manganya AYI ndithu ukulakwa ukufuna uchiphwasuliletu chipani chaa UTM km ukunama SKC anapanga mistake kusakha iweyo bwanji

  • @GetrduNamacho
    @GetrduNamacho Годину тому

    Manganya ndiwe d
    Galu kwa basi

  • @DanielTwiscombewe
    @DanielTwiscombewe Годину тому

    Apolisi ngat mulibe tiyegas okwanila ulendo uno mukatenge tiyegas ngat matumba achimanga ngat mukukagawa malawi yonse cifukwa eeeee,mwaojeza

  • @PhalesNotta
    @PhalesNotta Годину тому

    Koma manganya ukuziwa kut ufti umene ukuchitawo skulina zizakuvwerera wekha ndi chikangawa wakoyo anthu oyipa kwambiri inu uzikumbukira kut chilima kut aphedwe una panga plan ndiwe wemwe apanso wapangisa kut mai kaliati amangidwenso ayi zkomo

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 2 години тому

    Koma guys ulamuliro sumatengera mphamvu,,,asiyeni amalawi kuti asankhe zofuna zawo,,,azitsogoleri asiyeni amalawi apange zofuna zawo,,,felony ndichani?

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 години тому +1

    Mzapita mzomwezo kwa Mulungu just because of world material ur busy for nothing

    • @WakisaNjeghenje-i2n
      @WakisaNjeghenje-i2n Годину тому

      @@ShamimuBisani sukuziwa kut yesu analila kamba kandale?

  • @AbdulMalik-o7n1q
    @AbdulMalik-o7n1q 2 години тому

    Usi kapena kuti manganya timiyendo tatifito ukhale ku MCP komweko akutuma chakwelako waona kuti sakulephela kutenga chipani kupititsa kwa mfiti akoo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Годину тому

    Ine nkadakonda area 30 itangootchedwa bansi

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane 2 години тому +1

    Tiyeni titumize zinjoka zambiri zikazuze mumaofesi apolisiwo bwanji tiyeni afiti tose tigwile ntchito utsiku uno

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 2 години тому

      @@PetrusTlhokwane kkk osaiwal.mwala.ngt Goliat anafa chfukwa chmwal

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde Годину тому

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂ayi zikomo

    • @HabrilMalaya
      @HabrilMalaya Годину тому

      😂😂😂😂😂

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga 2 години тому

    Nde mbuzi zina zizikavotera manganya ku utm please Malawi segurani maso

  • @martintivalenji320
    @martintivalenji320 Годину тому

    This is very sad

  • @GriffinAziziSokoh
    @GriffinAziziSokoh 2 години тому

    Koma sikukhala kwa bwino kumeneko

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 години тому

    Manganyá kulibe 😂😂😂

  • @ChisomoSaiti
    @ChisomoSaiti 2 години тому

    Tikubwela komko kudzayamba mademo

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 3 години тому

    Kaotchen police pls

  • @ColleenChidimba
    @ColleenChidimba Годину тому

    Ndipo aka kayudasi sikaliyoti kamanganya mm sakuchita bwino ayi bwanji pa Malawi mm kwanyanya

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 25 хвилин тому

    Comrade Timothy Mtambo... where are you?