Iwe brother ndiwe chomodzimodzi oyimba wakwa American known as the game you just go straight to the point that's why I like you guys keep your head up osaopa osafooka
Chikangawa boys kulidyerera Dziko la Malawi, Chuma cha Misonkho ya Amphawi, olima ena Chaka chonse okazitafuna mkukhala Chikangawa boys opanda kukhetsera thukuta. Anyamata amuyaya amenewo. Komatu muzazisanza la 40 litakwana.
Ukana khala moyo ndikadati Bakili Muluzi TV ndi moyo wanga I mean we need to protect this patriotic guy. Bakili Muluzi TV the hope of Malawians
First one to comment from Zambia
😂😂😂😂😂😂 ineyo ndidzafela bakili muluzi tv mpaka 2025 shuwaka God bless you my friend watching from Cape town
😂😂😂😂😂
Iwe brother ndiwe chomodzimodzi oyimba wakwa American known as the game you just go straight to the point that's why I like you guys keep your head up osaopa osafooka
BAKILI MULUZI TV ALWAYS THE BEST, ,Boma lokupha,,lakatangale limeneneri. DPP MY VOTE.
Ulemu wanu big man tikuziwa zambiri because of you
God bless you and protect you continue to tell us Truth about this evils leaders.
Watching from Mozambique 🇲🇿 ulemu wanu bg brother timakunyadirani kwambir potiwuza chilungamo
Listening the best channel from Mozambique. We appreciate you for this noble work.
Koma mamvuto alipo ,HAHAHA Live with Zikhale Ng"oma ,koma Dziko lawonongeka generations to come they will be in deep Dedits.
We are here sir always following sir 🙏
Koma boma ili Ayi guys. Anthuwa anabwera kuzaonongadi ndithu🇲🇼🇲🇼🇲🇼😭😭😭😭😭😭😭😭
Ndipo usakaike
Following you bakili muluzi tv you have my support from Zambia
Thanks very much we have been waiting for this continue to give us the best political analysis of Malawi chikangawa party under demon chakwera
What can I say for this guy.... Kip it up ukutidziwitsa zambiri ndipo ukutitsuka m'maso zobisika tikuzidziwa koz of you mwana wamai
Watching from heaven angle number ten Northern cape south Africa ❤
You're the best mantha ulibe you are areal malawian ayaluke agalu amenewa
Thanks brother for news
We respect you sir Allah protect you
We are here for the truth it's only the best tv 📺 bakili muluzi channel
Kod akufuna ziko lizikomela iwowo basi khani ndiyoti awa achoka 2025
Bakili muluzi tv only nd komwe ndikuvako chilungamo keep up guys mulungu azkutetezani
I have been waiting for you.
Best TV malawi yonse❤
Whatching live from Denmark
Koma page iyi yayamba ikuonetsa zodabwitsa.
Are you still there please machenjezo amene tikulandilawa zukhala bwanji?
Ndimomwe ndimakundela tv iy chilungamo ❤❤❤pasongolo
I support Bakili Muluzi TV ndi katundu ukhalise umatha kucheza
Nkhan nd 2025 September
Sure bro you are 💯 percent true
The best TV channel
Big up brother always with you ❤❤❤
For me to solve this problem is change a relationship from old people to new generation finish
Live from cape town bakili mulizi tv ... Ana achepa mesa big up brother wathu
❤mumati imilila akolo chilungamo chowawa mau amat uyakhule chilungamo ngakhale chili chowawo motani mulungu azikudalisani akolo pot munikila
A vice nawo akuona ngati kusogolela dziko ndimasewera akutifelanji pano😢😢
Best of history ❤❤
My best Chanel
Amkulu mimbawa atansatu ndi a chithyolawa ayi zikomo 🎉
I pray for Malawi 🇲🇼
Keep up update 💪🇲🇼 best TV in Malawi chulungamo chibweleno poyela
Ku malawi umphawi uzatenga nthawi kuti uthe,aliyense akabwera mboma amafuna Kuba kaye .... Lord help us
Our economy is crushing guys
Chikangawa boys kulidyerera Dziko la Malawi, Chuma cha Misonkho ya Amphawi, olima ena Chaka chonse okazitafuna mkukhala Chikangawa boys opanda kukhetsera thukuta.
Anyamata amuyaya amenewo.
Komatu muzazisanza la 40 litakwana.
Nduna zaboma zikubela amalawi opusangati ifeyo , athakupangachilichonse chomwe angafune chifukwa amalawi ndife ogona komanso ndife makape
Asiyeni anjoye tizingoyang'ana basi
Dziko lamalwi ndalama ziripo koma atsogoleri ake muwoneso khope yachityolayo ngati manyi😂😂😂
Our own best tv❤
More respect big man!!
Always I love Bakili muludzi tv
Kodi BAKILI MULUZI TV 📺 sumungaipangile Dicoder
😂😂😂😂😂 Bakili Muluzi I love you too much
Listening live from Bolero Rumphi
Paja ndi Nthata za njalatu osamva chisoni ayi ndiye zili bizy ikukana ng'ombe yoonda kale
2025 ikubwera azapita ku mawura osewo
Ndipo kwambiri tu awawa azaona nyekhwe ndithu tu
Always ndli mbali yako biggy 💪💪💪
My best Tv bakiri muluz
Bakili muluzi tv best TV at all❤
Tiganize pokamvota chifukwa kuno ndalama izi sizitifika always kumangolila😢
Ineyo za akutundu awa Bakili Muluzi TV kaya ndinene kut chan tsopano kaya. Akamuna amalankhula mwaukatswiri awa 🙆♂️
I ❤bakili tv
Bakili TV number one ❤
Anyamata muli changu Kuma comments section 😂😂
Bakili muluzi number 1
inu mumakwa Bakili muluzi tv is number 1
Never give up bro ❤
All the best brother ❤
Zomvetsachisoni dzikolawola
Best TV, following 🙏
God is good
Ndi mbamva zokha zokha za mcp ndie ayamba kumayendelano zinthu zoti sizinathekomwe 😂😂😂😂 nkuluyudi ndiwokondadi ndalama chosecho kufuna alawasi 😂😂😂😂😂
Bwanji ndalamazo osapeleka kuma company kuti zinthu zitsike
My best tv ever
Keep it up brother
Bakilimuludzi tv 💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯💯
My best TV in Malawi
❤❤❤❤ Best TV
Koma boma ili!!! May God save Malawi
Ndipo kuvotelaso MCP ndiye minyanatu mmm
Live in capetown studio with zikhale n'goma
Malawi needs a redeemer
Wafika munthu wa mkulu kwambili timakhala maso kudikila tu thanks boss
God bless you❤❤
Akutibera Agalu amenewo
Bakili Muluzi TV the best
Mongo bwereza any time, any day any month from now anyamata azuka ngati ku Kenya ndikusesa mbava zonse
Tizingodya ndalamazo vote ndi muntima
#Best TV 📺 all the time 🎉🎉❤
Best TV ever
Forever with you big 💪💪💪💪
The best TV
Keep it up broz
Mwaitha Big koma ndi ufulu wanji wozembetsa ndalama
Mbava zimenezi zikuononga kwambili
Number 1 ❤ for malawi
Yaaaa
Best TV in malawi❤
Our hope TV
Fire 🔥🔥🔥🔥🔥🙏🙏🙏🙏💪💪💪
My best tv bkm
Mmhmh msomkho wanga umenewo akungodya ngat wamasiye
Ndipo mcp ikutumbwa bwanji. One day is one day
56 minutes, 3500 viewers. Umakwana 👍