Live long BAKILI MULUZI TV. I wish I could see you personally, but regarding security reasons, I support you being unknown. you are actually the Best on how you display your exposure of what you impart
Aah uyu wamangidwa basi chifukwa Chan ukubwereza zimenezi tinayivera kale iyi " kutheka Pali zake yemwe akupanga zimenezi pofuna kuti weni weni yo "atulusidwe
Tell your Masters that this man can not be arrested only for giving the nation history alive....uyu Alipo ndipo zikhale Ng'oma sangakwanitse kumumanga.bviva BM tv
It means that they have hacked his phone and are using his UA-cam account to trap his followers 😢😢. Ni hope that he has a good lawyer and he has been released.
Kodi mwati Samuel dowe anathandizidwa ndi ma Americans and Charles teller anathandizidwaso ndi ma Americans cholinga cha ma Americans chinali chani pa zithandizo zonsezi kwa anthuwa?
Ai l think abro wa ndiomwewa but mukale osamala mcp ikupanga zainu bro apo ai izi musie okusatilafe ntilimba ntima koma tikudandaula enafe because munasegula mithu yambili ya anthu so ntikulila ife km bro basi musie please bro anthuwa akukusakani so ukupani but God atetezere inuo zkm kulikose komwe muli ulemu wanu bg
Bakili Muluzi tv is not just a man but he is a digging history man.
Very intelligent.
King history i am so proud of you brother❤
Live long BAKILI MULUZI TV.
I wish I could see you personally, but regarding security reasons, I support you being unknown.
you are actually the Best on how you display your exposure of what you impart
Never sleep waiting for this, timakunyadilani kwambili bro Allah must protect this man
I was waiting for this since yesterday
Our man is indeed arrested.. 😢😢😢 I watched this video months ago 😢😢😢 please release Free our man 😢
Koma Bakili Muluzi tv history umakhonza 100% mmmm big up
Khaaaaaa!!! Machine awa. Big up brother.
Samuel doe anali munthu oyipa kwambir palibe chinalaksika kuphsdwa anazunza anthu osalakwa komanso anapha anthu osalakwa ochuluka watching from mozambique
Aah uyu wamangidwa basi chifukwa Chan ukubwereza zimenezi tinayivera kale iyi " kutheka Pali zake yemwe akupanga zimenezi pofuna kuti weni weni yo "atulusidwe
Ndie ukayimvera wapeza kuti ndi yomweyo?
@@bakilimuluzitv3371 sorry sir ❤️ ndinayamba kukusatilani kale kale ndipo zomwe zikuvekazi Bola zisakhale zowona 🔥
Mukuyamba kuyakhula musanamalize kuvela zosiyana malume velani modekha
@@paulpaseli6310 oh yeah
Zasiana kwambiri tidikile pang'ono
I was waiting this video from yesterday, thanks Boss
Support kwa inu Sir ndpo sitizaleka support
GOD BLESS YOU FOR BEING TRUTHFUL PERSON
22
You deserve respect Mr historian
We really appreciate your information..ulemu wanu.
I salute you my brother 🕴️
❤❤❤ machine big man🎉
I really appreciate the good work dat u r doin bro.
Big love brother May almighty Allah protect you
Zoona zake man
King of history ❤❤❤
Just when they thought they had extinguished the fire, boom 🔥! 😂
Big up,mumatinvesa kukoma ndi nkhani zanu
Big up, brother. Machine awa!
Nafe timudya Chakwera Chaka Chino asamale timutafuna
😂😂😂😂😂😂
My favourite
Mwayibwerezatu boss,thanks
I once watched this same video some months ago. I've that sense that our man is indeed arrested, and this is but a deliberate and planned repitition.
No, it's another one. That one has part one, two and three.
Tell your Masters that this man can not be arrested only for giving the nation history alive....uyu Alipo ndipo zikhale Ng'oma sangakwanitse kumumanga.bviva BM tv
naneso ndikuona choncho video iyi angoibweleza , kunena chilungamo amayenera kubwela ndi voice recording ndikutiuza chilungamo chakhaniyi
It means that they have hacked his phone and are using his UA-cam account to trap his followers 😢😢. Ni hope that he has a good lawyer and he has been released.
Kkkk you are strong and true man
Aaa man mumatha keep it up
Awesome bro ❤
❤❤❤❤❤❤❤ u brother
Big up brother man 🙏🙏
MCP==Samuel Doe==Hamas
guys something went wrong tiuzeni zoona za boss man wathu
Nice history
I love this
Iwas so sad to hear that u are arrested who gonna give us best news like you
W are here keep it up
Very interesting brother continue 🔥
Great man anali katakwe kaswiri 😊
Wow
Allah protect you
Part 2 pls
Umatha
Watching from SA
Eshiii after kutopa kudikira video iyi .. ulem wan big
Our historian.
Zitiyendere ya credit yokha tidzitumiza....proud of you!
APA mwabwerandithu. Kodi sindimanvesedwa kuti this guy has been arrested??
Never give up bro
big up bro
Thank you for the information
This is true story. 100%
King of history I'm so proud
I don't know what is trending on Facebook is true that you are arrested 😢😢😢😢
KHAAAA kumenya kugwesa 🤣🤣🤣🤣🤣
apa nde wandipangila kale plot yoti nditha kujambula filimu yabwino
Welcome u brother
Koma guys adah awawa ndakatundu eishii 😮
Kha kha
Ifetso tipanga kwa president chakwera chifukwa akujayira kwambili
Wa dpp iwe umangokamba zandale umabakira dpp
Anali wa khaza samuel doe
❤❤
Izi munatiuza kale 😮 kodi Mwamangidwadi eti
❤
Respect 😢😢bg mn
Mbambande brother 😊
Wasala zikhale ng'oma nayetso ayenela aphedwe kenako ndizamudyele mpunga
ℕ𝕕𝕚𝕡𝕠 𝕝𝕚𝕧𝕖
Big up
Yes abigy
Bg up broh
so does that mean prince Jonson became the next president? nanga Charles taylor zinamuthela bwanji
Koma big tiyankhuleni pazomwe zikumvekazi
Koma cigulu ca silikali A Chakwela ku burial kwa Chilima cinaculuka kucila ca Samuel Doe..Pepani 😭
Eti kufuna kutchuka ,kumangonyoza anhhu a mcp . panopo uliko wekha or dpp soyingakuthandize
Anthu tilibe pabwino kodi Channel iyi imanyoza MCP... kapena imangotitsegala m'maso?
@@georgechikafutwa1334anthu samatha kusiyanitsa choipa ndi chabwino...asiyeni awa
Iyeyu sakudziwa history musiyen sapanga za ndale muthuyu koma chilungamo
Nduna xikutuma athu kumapha athu ndiye udzitelo ukape bwanji
nce bro
He was a wicked president
Clip yakalekale iyi... ndimaona ngati mukuponya zatsopanotu.
Mukuibwerezeranji nanga?
Mumakwana big
Koma yaaaaah Chakwera samala kwako nawenso kwatsala pang'ono kuti kuthe
Kodi mwati Samuel dowe anathandizidwa ndi ma Americans and Charles teller anathandizidwaso ndi ma Americans cholinga cha ma Americans chinali chani pa zithandizo zonsezi kwa anthuwa?
Ineyo ndkavela nkhan yazigawenga imandlimbikisa kwambili ndpo ndmafna ndtajoina ndpo mudkile pazumene Aku panga chakwela kuzuza anthu Anga Ku Malawi ndkazatuluka kumene ndli muzawona Kut zizakhala zotan
Anachita bwino kwambili,,wakhadza adzikumana ndi khadza
Doe anali munthu oyipa kwambiri.He deserved everything that happened to him.
Rfd7
Gyyy
Gy
Mesa kd akumangani inu
Taphunzirapo zambiri
Ai l think abro wa ndiomwewa but mukale osamala mcp ikupanga zainu bro apo ai izi musie okusatilafe ntilimba ntima koma tikudandaula enafe because munasegula mithu yambili ya anthu so ntikulila ife km bro basi musie please bro anthuwa akukusakani so ukupani but God atetezere inuo zkm kulikose komwe muli ulemu wanu bg
Amabwezera revenge 😂😂😂😂😂
He was a bad guy mmmh
Dzikomo big timamudziwa zambiri chifukwa cha inu ?
Where is new video muli bise ndi MA history amene munapangs kale kapena zoonadi akumanga yettiiii
Following
You are expected for everyone
Mwati bwanji 🙄🙄🙄?
Amwene inuyo mumakwana.
Akulu awamangadi eti...chifukwa video ili ndi ya kale...Zomwe amati atulutsa Ina sizinakwaniritsidwe...
Wasala chakwera
Mumaitha big
Iyitu mnaikamba kale ndipo ilipo kale bwanji zikukaikitsatu simunagwidwedi wamkulu
❤💪💪🤔👍
big mumakwana
Ulemu wanu big