MICHAEL USI LERO WAKAKAMIZIKA WAYENDA NDI MKAZI WAKE KU MWAMBO WA CCAP OMWE UKUCHITIKA KU LILÔNGWE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 57

  • @MarkoChikoko
    @MarkoChikoko 5 місяців тому +2

    But VP akupangisa akazi awo ngati achilendo, beautiful couple

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg 5 місяців тому +2

    Koma awusi akumulakwira nkazi wake bwanji akumuchitisa manyazi ndi nkazi wokongola kwambiri bwezi akumayenda Naye azizolowera nanga

  • @SophinerWilliamFrank
    @SophinerWilliamFrank 5 місяців тому

    May the good lord guide in everything, blessed event

  • @RitaBan-t7c
    @RitaBan-t7c 5 місяців тому

    Kkkkkkk komatu ziliko mpakana kukaniza kujambula mukuopa chani mbanva iziiii ndiye ndakujambulani kaye kungoona kuti mutani😅

  • @FathimaMaulana
    @FathimaMaulana 4 місяці тому

    Munthu aima ndi mkazi wake komatu mpaka gap ya 2 meters 😂😂

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 5 місяців тому +1

    sopano zodabwisa kwambiri zamapemphero kuretsa kujambura zovetsa chisoni mwakhara ngati muri ku zachipani za yesu zimenezo kukaniza anthu zaziii

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 5 місяців тому +1

    Mai wokongola kusiyana ndi a mrs. Chakwera a nya Gondwe, 😂😂😂😂😂😂, eish! Kukhala ngati anachi kuwapatsa a Chakwera mkazi.

    • @Randy-er2xo
      @Randy-er2xo 5 місяців тому

      Kkkkkk angosinthana akaziwo

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 5 місяців тому

    I love you my Vice president

  • @RK-xw1of
    @RK-xw1of 5 місяців тому +1

    Mmmmm HHhH anthu muli pa ntchito yoposaso yolembedwa bwanji osamangogona kkkkkkkkk

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 5 місяців тому

    more fire vice president

  • @TrebuMalunga-sr2rz
    @TrebuMalunga-sr2rz 2 місяці тому

    Akulemphela kuyima bwinobwino ndiakazawo koma masikono ndiye ogundana nawo

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 5 місяців тому

    Kkkkkk akungoti cheucheu ngati wakuba mwachiona

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 5 місяців тому +4

    Mwachita makola kuzilekeska izo zikujambula na maphone za maboza

  • @YunusuABdullah-e7g
    @YunusuABdullah-e7g 5 місяців тому

    Michael Usi ndi Galu kwabas zichani izi..aaaa anasowa zochita awaaaa

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 4 місяці тому

    PANYAPANU USI

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 5 місяців тому +1

    Kuima ndi mkazi wache bwanji

  • @ShearstonNyirenda
    @ShearstonNyirenda 5 місяців тому +2

    Takunyadilani avp

  • @stevenmakwinja9648
    @stevenmakwinja9648 5 місяців тому

    Kodi mai Skono mawawona?

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 5 місяців тому

    Wanda ndamake sikono😮😮😮

  • @lawrencemakina2882
    @lawrencemakina2882 5 місяців тому

    Mkuluyu mene akuyang'anira mmmm anachenjeresesa

  • @StoneckJali
    @StoneckJali 5 місяців тому

    Jelasi

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 5 місяців тому

    kuwapatsa uremu achakwera ndiye zayesu zimenezo mwayara masanja paripose payende achakwera ndi manganya azikupasirani zimuzimu zoyipa kumeneko 😂

  • @BrianAmbeswa
    @BrianAmbeswa 5 місяців тому

    Ambeye ziibwela za ziiiiiii

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 5 місяців тому

    A VP Ngati Galu WA 😇

  • @AgnesNjikho
    @AgnesNjikho Місяць тому

    Eeeeeee amalawi jelasi mulungu anafuna wofupikayo kukulamulani inuyo mumafuna ndani? Amene mumafuna inuyo sanakwane pamadu pamulungu ndipo mulungu amapanga zodabwisa ndipo muzadabwabe chifukwa chili chose chikuyenda ndi mphavu yamulungu munyoza mutopa muzanu alipapando

  • @Jele-mk9ip
    @Jele-mk9ip 5 місяців тому

    Si Kembo Mohadi winayo?

  • @GodfreyMbiri-x8s
    @GodfreyMbiri-x8s 5 місяців тому

    Kufupikako.kkkkkk

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 5 місяців тому

    kuti muremekeze azi busa ndiye ana chakwera nanuso ac.c.a.p ndarama zikuphani ambuye akuyendereni ndithu

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 5 місяців тому

    Nanuso mukumatumiza zopusa bwanji nanga pali chani apa zojamula mdi ka phone ka 8 Gb

  • @smartjilamu8026
    @smartjilamu8026 5 місяців тому

    Dzoka lawina ndi mwai wawina😢

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 5 місяців тому

    Koma ma church nde akuhongedwatu, dziko lapansi ndi anthu ake mmmh

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 5 місяців тому

    Uyu ndi chizeleza zinangochitika kuti ulamulilo wa dzikowu umapezedwa motelo kutu vp adzitenga malo otsogolelayo akafa koma a usi ndi oyaluka

  • @KumbukaniChimbalanga
    @KumbukaniChimbalanga 4 місяці тому

    Mavuto kwabasi

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 5 місяців тому

    Usi wa mcp leave us the Utm alone

  • @BeatriceProfessor
    @BeatriceProfessor 5 місяців тому

    Koma boma ili likungowononga ndalama ya misokho yathu zaziiiii

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 5 місяців тому

    Zaziii sizikuveka iya

  • @WilfredMwale
    @WilfredMwale 5 місяців тому +1

    Madam moni kumangowasemphatu

  • @GertrudeChifupa
    @GertrudeChifupa 5 місяців тому

    Lero anali ndi make Sikono

  • @BFWCPHIRI1978
    @BFWCPHIRI1978 5 місяців тому

    UHule onse uja tere uli ndi bomba kan?

  • @NyirongoMexonyoba
    @NyirongoMexonyoba 5 місяців тому

    Koma anthu muyakhura

  • @JustinChilinda
    @JustinChilinda 5 місяців тому +5

    Koma izi palibe chazelu ndatolapo yesan kumalanga post zinthu zot tikhoza kuvako Za zelu

    • @SoldierWilison
      @SoldierWilison 5 місяців тому

      Ngati bonza MN kungo tithela madata

  • @AwandeOkuhle
    @AwandeOkuhle 5 місяців тому +1

    Komamwawuze.aziyakhula.ndiakazi.awo

  • @SteviePatrick-g2p
    @SteviePatrick-g2p 5 місяців тому

    Uthenga wa ndioy chan pamenepa omwe ungatipindulule ife anthu

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 5 місяців тому

    A vice kutafuna chingamu mhhhh komatu ziliko
    Munthu wamzelu tafutafu kopandaso disprin

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 5 місяців тому

      Umoyo wasanje umenewo vuto lako ndi chani adalemba pati kuti munthu asatafune

  • @TamikaKaponya
    @TamikaKaponya 5 місяців тому

    Dziko ndi anthu ake

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 5 місяців тому +1

    Asayambepo kuvinatu uku kkkkk

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 5 місяців тому

    Manganya koma ziko ili ndilama drama basi

  • @GloriaKaduya
    @GloriaKaduya 5 місяців тому

    Kodi magalasiwo amavinavina kk😂

    • @kadijhahaji
      @kadijhahaji 5 місяців тому

      Komatu zoona aaaaaakkkkkkkkkkk koma kumeneko

  • @stevenmakwinja9648
    @stevenmakwinja9648 5 місяців тому

    Kodi mai Skono mawawona?