Chakwera iwe watepepelesa azungu akutenga Ngati Nyani? Wang'alura Kulu ameneyu🙌🙌

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 21

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 24 дні тому +5

    Mudatirakwira mcp kutimphera chilima mulungu yekha bas

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 24 дні тому +3

    Manganyawo ndi fiti😊

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 20 днів тому +1

    Mwaya khula bwino koma mule osamala chikangawa anga kumezeni kudana ndi chilungamo Ambuye akutetezeni zikomo ife tikulillabe Achilima chikangawa Muthu oyi chikumbuntima chimuphe

  • @UncleBusy-c6l
    @UncleBusy-c6l 24 дні тому +2

    Kodi Kuno kumalawi utangoti achakwela takwelani njinga iyi yakapalasa tikufuna tikutengeni chithuzi kwathu Kuno sangatimange Kuti tawanyozesa apule APA apule mwatipangisa manyanzi akupepelesani azungutu APA

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 20 днів тому

    Ine nidzayima and I quoted 😢😢

  • @IjilanMwalija
    @IjilanMwalija 24 дні тому +1

    Well said

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 20 днів тому

    Mmm illustration ya chithunzich itilakwasa ine sindikupanga ayii ayii ndakana

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 24 дні тому +1

    Ndichani kumene uku

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 20 днів тому

    Chikangawa alibe vote

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 20 днів тому

    ❤❤❤

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 20 днів тому

    Ndipo Ayu ada pha chilima sangakane muthu olo athu atakuuza ukhoza kukana pawekha

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 16 днів тому

    Etii chili mweeeeeee za ziiii

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 24 дні тому +1

    😂😂😂😂😂

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 23 дні тому

    Wapanga alliance ndiwe ife eniake sitidziwa... Kodi alliance tunapanga liti iwe? Kkkkkkk

  • @MexcoJepter-p5f
    @MexcoJepter-p5f 24 дні тому +2

    Ndiwomvetsa chisoni awa akuchita kuwafananiza ndinyani 🤦🤦

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 23 дні тому

    APM uja osazaphwekesa DPP UDF UTM AFORD

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 24 дні тому +2

    Electoral commission ya malawi Congress party

  • @user-zt7hy5lh4r
    @user-zt7hy5lh4r 24 дні тому +1

    ❤❤❤