Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Tisamangoonela athu aku gahna kwathu alipo tiyeni tipangne sapot
Wow so talented man, better than making zinthumwa zotambila 🙌
Aaa km yaa✍️ greatful job
Interested thing bro keep it up
Ndimwe bakali Mr man .am juve Lusaka zambia
Wow! Amazing
Well done nchimwene
I know this guy very well Well done Mr..
Mulungu apitilize kukudalisan ndi lutso lanu la bwino.Bora oipa asakusokonezen
Adah awawa ndi fire koma poti ndikumalawi nde ndizovuta
amazing.maphunziro a mkulu ameneyo analekezera pati
Continue bra am proud of you
What a Good car
Mpaka kwathu kwa Adawa kukhala luso loteleee kkk
Good job brother
Acikulile nde mulungu adakudalitsani kwabasi mulekele app iyayi ngati nikotheka penphani boma likuthandizeni pazitsulo zikomo ndine prince Elias kuzambiya
La nkhaniwe mantha ulibe... Kumachiliza😊 uli pansi pompo kkkkkkk
Iyi tikudzatenga mutipelekeze kokaonekela pa hoyi hoyi
😂😂😂Kugwilitsa ntchito nzelu zachibadwidwe
Anthu mulinizelu ishi
😂 Kuliza hoy hoy3 uli pans pompopompo 😂😂😂
Koma eeeeeeeeee ai ku BT kuli Luso, wina kumulanje anapanga Ndege mmmmm, wina kundilande chophikira choyendera madzi komanso generator yoyendera madzi mmmm😂😂😂😂😂 BT izatigulitsa sure 😂😂😂
Hoyi hoy 3 man muli bho
Koma abare mulungu amapereka luso yooooo bambo munadalisika kwambili
Mulungu a pitilize kudalitsa nkuluyu komaso ndithokoze mibawa tv chifukwa anthu alusowa zimafunika kuwabweretsa poyera kut tsiku lina azakomana ndi ma sposer mupitilize mwaziyambazi amibawa ndakusowa kumudzi kwathu yoooo
Chinthuchi nchachikulu chimafunika mateyala akulu akulu
Uyu ndiwodabwisa
Nice
Uyu ndi big ndipo ndiofunika kucheza naye.. luso labwino
Alimbikile
😂😂 Kunoso ndizotheka
Ndadabwanawo akuluwo
Wow so amazing
zikuntheka bwan
nthax uli bho
Give him tools he can have a good workshop servicing motorbikes etc
Hoyi Hoyi 3 ndi nyatwa Phiri
Amazing
Hoyihoyi 3,Kkkkkkkkk koma vaccine abalalisa anthu kumalawi
Zoonad
Hoy hoy 3
Bola osamuletsa aboma
Salute
Abel manthatu
Linje luso lilipodi kwathu kumeneko
Had
Ili si luso
Ok ñ
Tisamangoonela athu aku gahna kwathu alipo tiyeni tipangne sapot
Wow so talented man, better than making zinthumwa zotambila 🙌
Aaa km yaa✍️ greatful job
Interested thing bro keep it up
Ndimwe bakali Mr man .am juve Lusaka zambia
Wow! Amazing
Well done nchimwene
I know this guy very well
Well done Mr..