What we knows is Mnzeru salowera chokolo, chilima never compared with Usi chilima was gentleman man of God and a humbleman so the leadership of Chilima is from God
Mr Usi ,sadalakwise kuvomera , tisayiwale Kuti MULUNGU ANAMUTSIMIKIZILA DAVIDE,KUTI MWANA WAKO SALMON NDI AMENE ADZANDIMANGIRE INE NYUMBA .So let's wait and see ,CHILIMA was fire fire fire ,but let's wait and seee
Bryan ngt a USI avale sapato za malemu chilima nde kt 2025 azayimila ngt president WA tonse kapena sazakwanisa kutelo komaso ngt a MCP asanga a amanganya azapasa pata osogora mu 2025 ngt mwapangano mu 2020 ?
Usi chiyengo uyu inu i 15:50 think think usi he knew something or angomuphimba ndipos sangamulemekeze ngati zikhale ng'oma samalemekeza chilima who are you
Micheal USI ndi wa MCP kale chifukwa iye samapezeka ku misonkhano ya UTM koma chenjerani akuphanso ukuonena kale kuti MCP samafuna kuwadzudula akamachita zoyipa akungokhalila Kumanga anthu popanda chifukwa MCP ndi chipani cha nkhaza zazwika chakwera amadana ndi chilima mpaka kuphedwa chifukwa amafuna kuyimilila pulezident mu 2025 lero Wafa nawenso chenjerani USi.
From Cape town Brian Banda and your team we know that you hv bn captured by MCP your are not the same as u were b4 When money talks chilungamo chimakhala mtulo
Congratulations Dr Michael Usi
Bull shit
Tiwafunile zabwino zonse a Dr Usi ngati wachiwiri kwamtsogoleri wadziko lino ❤
Congratulations that's wise decision chakwela
Wabakili muluzi ujah ndikatakwe amaona muthu for one time kudziwaso atuuza zambrii mawa bass
What ever wabakili uja akamalankula zoona
Manganya congratulations ask God for more wisdom ❤
Chilima was vibrant koma he was pinned down until he was quite. Ussi can be above Chakwera?? Let's wait and see the motive.
Amanganya tamango kupangani zamasewelo osati zandale mufelapo chakwela ndiwakupha
Very good analysis times
Congratulations usi, thanks Chakwera ndakukonda kwambiri
Congratulation bwana usi
Congratulations Dr M B ussi the people are behind you
Congratulations Dr Michael Ussi, May our heavenly Father guide you
Michael ussi I'm happy to be a follower I am happy to be a follower of kindness. But open your eyes to the dunes. Open your eyes my sun
Times Radio muli uphungu wabwino. DR. USSI, these men are guiding you in a friendly way. Congregations Dr. Ussi.
That's an excellent move by MCP. You are playing your Cards very well. It might pay off. Bravo.
It will never pay off
Congratulations Dr Usi keep it up, thanks Mr President we still love you our President
All the best my favourite actor
Am Happy God guide you vp.All members of utm Loves u
Mmmmmmkkkkkk
What we knows is Mnzeru salowera chokolo, chilima never compared with Usi chilima was gentleman man of God and a humbleman so the leadership of Chilima is from God
buh chilima sangasankhe kape more over usi amapemphelaso kwambiri
“Inutu Paja mumakonda ku Phuluza mawu” 😂😂🤣🤣
Nkhan yabwino Mr Michael Usi
Usi has not come to fill in the shoes of Chilima but the shoes of the vice president. Let Usi be his own man
Ndimafuna mundifusile achakwera Kut ngat Malawi yonse osawavot era adzakhala owinabe ngat adzakhale owin😂abe ma vote adzachokera Kut chabwino achewa onse takupatsan ndiomwe amakudan omwe atengen kod tima vote taachewa tokha tingakuwinitsen? Inutu mpando wanon non muchosedwapo
inabwera kuzakhalatu mcp.
Congratulation times you inspire us very good and powerful counseling indeed we are hopping a lot from our new VP
I wish Mr Manganya Dr usi the best time in office may The Lord bless you with wisdom tolead Malawi to great heights
VERY CONGRATULATIONS DR MICHAEL BIZIWICK USI, YOU ARE A MAN AMONG MEN.........GOD BLESS YOU.....
Eya zoonadi pachoka mnzako pali malo, koma izinso Michael Usi hmm ayi mwaonjeza.
Congratulations Dr Ussi
More fire Mr Usi VP of our country Malawi
Mr president l salute you for choosing Dr Ussi to be our new vice president. God bless you, God bless Dr Ussi and God bless Malawi.
We are not serious Michael Usi got that position just to cover the mess.
Congratulations Dr Usi l believe you can take us though and for fill SKC dreams ,long live May God guide and Procter you,long live UTM
All the best
Manganya i hope you take us forward remember there is no mai sikono😂😂
Ussi not suitable may be politically but as VP or a leader no. Such position needs people with high integrity and caliber.
But Chilima choosed Usi as his vice 2019 ija. Which means Chilima akadawina nthawi imene ija Usi akanakhalabe vice tu.
@@PraiseKadzitcheeeeh nzoona
Obviously wish him all the best
Bamboo asikono😂😂😂😂😂😂😂
Ndiwawo kale ndipo usi ananena kale kuti Ali m'mimba mwa apule palibe kulemekeza apa
Congraturations Dr micheal usi the manganya ur the best geri kuchita kuposa wakusankhayo
bwana presendent mwasankha bwino kwambili mulungu akudaliseni❤
Congratulations mr usi
Wish him all the best
Congratulations to Mr usi happy 4 u may God guide u🎉
Congratulations mr usi my favorite actor❤❤
Mr Usi ,sadalakwise kuvomera , tisayiwale Kuti MULUNGU ANAMUTSIMIKIZILA DAVIDE,KUTI MWANA WAKO SALMON NDI AMENE ADZANDIMANGIRE INE NYUMBA .So let's wait and see ,CHILIMA was fire fire fire ,but let's wait and seee
Congrats Mr Usi. I know we lost a great leader but we need to move on. Mr President, we are behind you.
Zabwino zonse boss Mr Michael usi may God protects you
Chakwera simungamuthe..he is very intelligent
Congratulations to Mr usi
Pass my regards to Ndebvu zamwayi
Ngati nkufuna ndarama zanu akuru coz mukufa moyo sagura MCP imeneyo inu ndi madzi amodzakare chirimatu adari doro muripati inu
Aluka kontinua
God bless you Dr M. Ussi.
Komatu Times Radio you bring ma answers
Obanda auze kuti Tinali ndi Magufuli ku Tanzania chisazo champhavu
Well said wonder
Enafe zotukwanazo sitipanganawo.ndi mmene zimakhalila ndithu for replacement imafunika.congradulation
Dr .usi.
Good
Congregation mr usi tikufunilani kugwila ntchito yabwino nda president amr chakwera
Bravo Mr president
Chigawenga china icho
Congratulations to Dr Michael Usi
Zabwinozonse Dr Usi.
Congratulations Bwana usi
Ist's a law af a must,well come on top of laws❤
Happyfor Usi
The guy is white shirt thinks he is smarter than others. Brian is the king bro.
Keep your useless analysis with yourself, don't create competition and sow divisions where it is not needed, you must be a fool.
Congratulations Dr USI
Onesani zisudzozanu Amanganya😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😢❤😊😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Chakwera only appoints the chewa's that's not fair
Congratulations bambo asikono😂😂😂
😊😊
Koma zilikotu ife pheee pawindo kudikira amanga akusintha zinthu 😂😂😂
Avise Pule,tiwona kuti mupanga support yotaní ma artist anzanu ,woyimba ,azitsunzo, wosewera mpira yonse . Awoneni anthuwa kuwapatsanso support
Chalaka Bakha, Nkhuku singatole ayi.
Anyway congratulations to Dr Usi BUT things will never be the same.
There was one Chilima.
Brian ndikukuwuza kuti usi siwa utm and nthawiyomwechilima amapanga ma pres briefing usi amangokhala chete ndikuwonangati munthuyo ndiwa mcp
Andevu zamwai osamakonda kuperela zitsanzo za ku ntchito Kwanu , zikumatipatsa ma picture osakhala bwino amene mumakhalila ku times ko 😢😢
Bola asakhale chikwangwani potseka mkwiyo wa anthu a Utm pa imfa yowawa ya Chirima.
According to the agrement signed by the two officers on the one to be the 2025 presidential candidate for the Tonse Alliance. Will Ussi be the one
34:23 abambo asikono now Vice president republic of Malawi
Make sikono Kuli iwe KO ukumva bwanji😂😂😂😂
Achita bwino kwambir kutenga
Wa UTM❤❤❤❤❤❤❤❤🙏🙏💯
Manganya si wa Utm iwe
Ndiye Usi adzayimira mu 2025 monga mwa mgwirizano wa ma murderer ndi late Chilima?
Ngwa mcp ussi
Nanutu ndiachitsilu
@@NgomaRaheem uchisilu wainu ndi umbuli kwambiri 🐕🐕🐕🐕🐕🐕🐕🐕
Eeeh 🤔
Kkkkkk kma Brian ndege atenge family yonse ngt a pule😂😂
Kodi akanyama chiuma adasowa bwanji?😅😅😅 bakili tv tikatundu, mungotaya nthawi ndi chakwela wanu.
Zose zimachitikazija amadziwana kuti pakubwela usi
Zofoila😮😮😢
Ina nadabwa Ausi kudekha
Tili kumastandi ife😢
Wayankhula ndikupeleka chitsanzo Brayan
Kodi andalewa ngati amakonda dziko bwanji safuna kudula malipiro awo komanso kumagwilitsa ntchito galimoto zotchepa kuti azikwanutsa kupanga chitukuko chadziko kuposa kumazisangalatsa okha
Komanso kumagulitsa companys aboma zomwe ndalama mzake boma sitinamve kuti zinapanga chiani? Nanga aja anatenga ngongole zaboma azabweza litilo? Ndiye mr usi ntchito yomwe akufunika kuchita
😂😂 ati paja Inu mmakonda kuphuluza mawu hahaha
That's better.
Osayiwalatu Make a sikono akhaleso pambalipo 🎉
😂😂😂😂
Make sikono waiphula basi apa kkkkkkkkk mwina sikono uja atulukila tsopano kkkkkk
Bryan ngt a USI avale sapato za malemu chilima nde kt 2025 azayimila ngt president WA tonse kapena sazakwanisa kutelo komaso ngt a MCP asanga a amanganya azapasa pata osogora mu 2025 ngt mwapangano mu 2020 ?
Usi chiyengo uyu inu i 15:50 think think usi he knew something or angomuphimba ndipos sangamulemekeze ngati zikhale ng'oma samalemekeza chilima who are you
Micheal USI ndi wa MCP kale chifukwa iye samapezeka ku misonkhano ya UTM koma chenjerani akuphanso ukuonena kale kuti MCP samafuna kuwadzudula akamachita zoyipa akungokhalila Kumanga anthu popanda chifukwa MCP ndi chipani cha nkhaza zazwika chakwera amadana ndi chilima mpaka kuphedwa chifukwa amafuna kuyimilila pulezident mu 2025 lero Wafa nawenso chenjerani USi.
The problem is chakwela mulibe leader ship .... sizingatheke kukonza chilichonse
Okay chabwin
From Cape town Brian Banda and your team we know that you hv bn captured by MCP your are not the same as u were b4
When money talks chilungamo chimakhala mtulo
Bakili muluzi tv akulu ndikatundu amafufuza
Congratulations Mr ussi
Aliyense ndi Doctor kumalawi or opanda zoyenerela
Vp osatsuka nkamwa eti inu zithu zake