Ndizomvetsa chisoni kuti amalawi ena adyera ndi olephera adanda boma mwaupando lero ndiizi zikuwavutazi o pa 10 Mulungu alowererepo,mai mukhale ndi moyo
Chigamulo cha khothi chinanena kuti tipex sanasokoneze manambala amavoti koma kuti panali zolakwika zambiri. Funso mkumati ngati ma komishonala anali olakwika nanga bwanji sanakhansule zisankho za ma mp ndi ma khansala?
Mfiti ya mayi Adali kuti nthawi yonseyi.no any nzeru mwa inu mayi. Kunena chilungamo ndi kofunika Anthu adafufuza bwinobwino even electronically how anthu adabela masankho nthawi ya inuyo. Don't talk as if you are honest person Malawi waonongeka inde koma munthawi ya chipani chomwe mudachiwinitsa nthawi imene ija zinthu zidayipanso Palibe wabwino apa DPP mbava Awa alipowa mbava And amalawi don't make a mistake yoyikanso DPP mboma Tidzaliranso Go for Chilima Basi Sitingachotse hule mbanja ndikukwatiranso hule mkumati tikukonza banja
Hearing the whole interview I don't see where she has answered directly the question, even her narration seems runs away from what she knows better, search me!!!!!
Ulemu wanu Mai. I believe you did a great job. Had it not that the other parties joined Professor Peter was winning.
Mrs tippex, jean asa mbava ya kazi
Boza lamzimayi amwene aaaa munthu mlala ngati uyu mbwenu wali kutumula aaaaaa boza vya ziiii
Adathawa tipekisi
Ntola nkhani yemwe anaulula,za mai ameneyi,anamwalila.lero, wabwela palibe zomwe amalawi,akuchitapo,koma moyo wa munthu unapita.
She is a woman of God,i know her what she is saying is true.
Wakuba uyo
Chifiti ichi nanga tippex anabwera bwa chitsiru iwe
Humble mama anthu a jealous zikuwavutatu kuyendesa dziko
Jane Jezebel Ansah, pika komwe ukuchokerako, musamubvotere uyu a Malawi, alibe chilungamo
Ok
Ndizomvetsa chisoni kuti amalawi ena adyera ndi olephera adanda boma mwaupando lero ndiizi zikuwavutazi o pa 10 Mulungu alowererepo,mai mukhale ndi moyo
Bola jane
Mcp yalephera.... Mbava ndi izi zalephera kulithanduza dzikoli
Salina uyo.
Munagudula msuzi wagulu
Tamkuvani
Iiiiii
Malawi ndiziko lovesa chison kwambiri,chomwe Malawi amafuna sachiziwa.ine Ndimat athu oyipa kwambir ndia makhothi
Mulungu anali ndi dongosolo labwino amafuna tione zomwe timkalilira paja mwana akalilira nsasi msemele
Mutu wake siukugwira ndiwa dpp uyu
Iiiii
Mcp inalandaboma amafuna kulemela modzidziswa
Iwowo akanafotokozera a marawi tikanateteza ife ndi katundu tikubwera koko ku marawi ko 2025 paribe kubera mavoti tizadurana machende
Kufotokoza kwa munthu wakuba. Zosamveka
Mayi bodza kwambiri she fooled Malawians.
Ndipo she is answering as innocent person koma mmmmmmm mulibe chilungamo
Iyeyu ndi judge why adaluza mulandawo
Ai sanaendese bwino , koma ali ndi mwai kuti amene timaganiza kuti mwina atha kuthandiza ziko kusiyana ndi mmene zinalili. Koma kunena zoona amalawi ambili DPP inanyanya and zoti atha kuchoka pampando samaziwa sanaganizepo. Moti chifukwa cha makapewa, lero a-DPP imaoneka kuti anali ma dolo koma kunena zoona anawonjeza ndipo ngati angapasidweso mwai akuenela kuphunzila kenakake Lero akamati anaziendesa bwino, ai zikomo chilungamo amachiziwa okha.
Chigamulo cha khothi chinanena kuti tipex sanasokoneze manambala amavoti koma kuti panali zolakwika zambiri. Funso mkumati ngati ma komishonala anali olakwika nanga bwanji sanakhansule zisankho za ma mp ndi ma khansala?
😂 mavuto sadzantha kuno ku malawi chifukwa cha mbavazi
Boma lozuza ili may
Olemekezeka?😂😂😂
Mfiti ya mayi
Adali kuti nthawi yonseyi.no any nzeru mwa inu mayi.
Kunena chilungamo ndi kofunika
Anthu adafufuza bwinobwino even electronically how anthu adabela masankho nthawi ya inuyo.
Don't talk as if you are honest person
Malawi waonongeka inde koma munthawi ya chipani chomwe mudachiwinitsa nthawi imene ija zinthu zidayipanso
Palibe wabwino apa
DPP mbava
Awa alipowa mbava
And amalawi don't make a mistake yoyikanso DPP mboma
Tidzaliranso
Go for Chilima Basi
Sitingachotse hule mbanja ndikukwatiranso hule mkumati tikukonza banja
Mbava iyi yiyendetsa bwino chisankho chake chiti? Tipex anamutenga kuti? Asatinamize tinaliko ndipo ndife akulu akulu. Kuba basi.
This interview is boling , mafunso alephera kufusa amibawa, this woman she need joab chakhaza, Chitha kumwamazi chimayi icho
Hearing the whole interview I don't see where she has answered directly the question, even her narration seems runs away from what she knows better, search me!!!!!
Mayiwa salakwitse anayendetsa bwino akadakhala sanayendetse bwino akadamangidwa,
uyu asatinyase. tipex uja anachokera kuti. wautsiru ameneyu. Bwanji analephera kudziteteza ku court?
Court lo lili ndi vuto bwanji ataziwa kut sanayendetse bwino chisankho analekeranji kumusegulira mlandu?
Court lo lili ndi vuto bwanji ataziwa kut sanayendetse bwino chisankho analekeranji kumusegulira mlandu?
Mzimayi oyipa mtima
Ndizomvetsa chisoni kuti amalawi ena adyera ndi olephera adanda boma mwaupando lero ndiizi zikuwavutazi o pa 10 Mulungu alowererepo