NDISANACHOTSE VIDEO IMEYENEYI ONELANI PROGRAM YOFUNIKIRA CITIZEN WAMALAWI KUTI AYIVERE |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 тра 2024

КОМЕНТАРІ • 25

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 23 дні тому +6

    Chakwela akuti nyatsa akungomanga athu y dziko la democracy

  • @usherkays4379
    @usherkays4379 23 дні тому

    Shaaa thanks 🙏🙏🙏👍

  • @George-zd5le
    @George-zd5le 22 дні тому

    Ine Zina la chakwera limandinyasa chimunthu chakuba ngati ichi mmmm sinawone

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td 23 дні тому

    Vuto zipani ndalama mulibe maiko anzanu popanga zinthu apolice amakhalapo osati zikuchitika ndiye kumakatenga apolice boma limapanga ndalama njira imeneyo muzikalipira ku boma ndiye izi zomangoyenda ngati viweto akuphani lipirani kuboma apolice 8 pitala or chihanayo alipile mupanga no problem sanga bwere munthu ngati a boma alipo zipani kusawuka

  • @jamusnamwino-br2iz
    @jamusnamwino-br2iz 23 дні тому

    ukamati chakwela ndimunthu wabwino ubwinowake ulupati?

  • @mafukenimasangwi5487
    @mafukenimasangwi5487 23 дні тому

    Oyambisa ziwawawo kuma ngo wagwila ndikuwafinya Osama wapitsa ku police aziwaulula amene ama watuma mmesa akukana

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 23 дні тому

    Mumuwuze chakwera kuti dziko silake,nawe chimwendo the day will come

  • @robertbanda765
    @robertbanda765 23 дні тому

    Anthu aupandu amadzibisa popanga zaupandu kuti asadziwike pokhapokha ngati akufuna kukoreka anzao amachita zachisawawa.

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 23 дні тому

    Chilowelen lazalas ma ofes aboma sakuyenda bwino monse akut ayika ndalama kut azithana ndianthu apolice pano mphamvu zinatha zinapita Kwa pule kulekana ndikale pano mbola lazalas akuyenla kusintha sikuynda

  • @WilliamMsimuko-mx7fu
    @WilliamMsimuko-mx7fu 23 дні тому

    Chakwera anamvera Za chimwendo all minister's is below him he's King in MCP
    2025 is not far you'll out of the Government APM Will bounce back to power

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 13 днів тому

    Nzika yopanda chiphaso ku.mmwera kuno

  • @SteveNkhambule
    @SteveNkhambule 23 дні тому

    Tionesana

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l 23 дні тому

    Galu uyu ndamene amapasa anyamata ndalama kumakamenya anthu achimwendo mwazi umenewo muzaubweza lino ndi dziko ada

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2z 23 дні тому

    Kodi anthu anja ku kamuzu stadium amene anja ankati achoke achoke ankafuna ena otsatila chakwera ankafuna kuti atani zina kumafunini kupewa

  • @user-el8to1te3l
    @user-el8to1te3l 23 дні тому

    Chemwendo banda ndi chi nfit chokhwima

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 13 днів тому

    APM APM APM APM Apm

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 23 дні тому

    Chakwera amamuopa chimwendo ndi milk

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft 23 дні тому

    Chakwera ndi muntu wabwino koma He don't have a governing skills,I am a STD 2B drop out but still I can balance the economy

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi 23 дні тому

    Chakwera akuchoka 2025

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba 23 дні тому

    Kodi boma ili ndilaboza koma limangolalikila bad

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 23 дні тому

    Vuto si Chakwera mu bomamu ai, vuto ndi Chimwendo Banda ndi achina mkaka. Chimwendo Banda ndi wa nkhanza komanso akuda nkhawa poti boma lawalephela.

    • @user-og4oe5yp4w
      @user-og4oe5yp4w 23 дні тому

      I agree with you chakwera amamuopa chimwendo ndi milk

    • @user-jn9tz3li3v
      @user-jn9tz3li3v 23 дні тому +2

      If Chakwela akumuopa Chimwendo ndi Mkaka then is not fit to lead a nation. A leader must be strong like Kamuzu and Bingu.

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 23 дні тому

      ​@@user-jn9tz3li3vBasi ❤❤❤

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 23 дні тому

      Chakwera ndi Chilima ndi cabinet yawo yonse ndiopepera alephera onse