DZIKO LA MALAWI LIRI PA CHIOPSEZO, PRESIDENT WA MA REFUGEES WALOWA MMALAWI MUNO | BON KALINDO |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 22 тра 2024

КОМЕНТАРІ • 56

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 23 дні тому +5

    We celebrate you Mr Bon Kalindo. Your passion to fight for the poor is so genuine.
    Never give up. May God, keep protecting and adding more grace on you.
    We love you Sir.

  • @AlliSaiti
    @AlliSaiti 23 дні тому +4

    I will always stand with kalindo

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x 23 дні тому +5

    Yehova plz mutengen chakwela wa tikwana kwambili plz yehova akapume

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 23 дні тому +1

    You are the true eye of Malawi

  • @InnocentBabyTurtles-iq4ok
    @InnocentBabyTurtles-iq4ok 23 дні тому +1

    the dddddddddd cccccccccccccc dangerus child fire may God bless u kalindo

  • @nkhangani.t
    @nkhangani.t 23 дні тому +4

    good notec

  • @greymasha838
    @greymasha838 23 дні тому +3

    Ayi Zikomo Ambuye atichitile chifundo

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 23 дні тому +4

    Odana ndi the DC akudana ndi chilungamo kmso ndi makape.

  • @ZaneMbawa
    @ZaneMbawa 23 дні тому +2

    More fire big

  • @LeviNjoka
    @LeviNjoka 23 дні тому +4

    Ambuye tichoseleni chakwera watikwana

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 23 дні тому

    Good Message ❤

  • @AssanJamesAlli
    @AssanJamesAlli 23 дні тому +2

    Chakela ife watikwana mulungu chondo amutenge

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 23 дні тому

    I SUPPORT THE DC'S MWANA WOOOOPSA KWAMBIRI BON KALINDO

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 23 дні тому +3

    Kama chakwela ulindi umunthu galu iwe😂😂😂😂😂😂

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 23 дні тому

    Achamba wokha wokha womsatila kalindo palibe chanzelu apa zaziiiiie zokha zokha

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 23 дні тому

    Kalindo sanama

  • @user-et3il7pi7t
    @user-et3il7pi7t 23 дні тому

    Koma achakwela akuziwa kuti anthu akubwela kuzatitola ngati tili ndi zida zo ophya kapena ayi ndipo Ife PANO nkhani ya nyacha singayambe chifukwa chake a Tanzania ayamba kumanga doko lawo chifukwa anazativula kale kuti tilibe china chilichose kuti chingatateze Ife a Malawi mayooooo boni kalindo I respect you

  • @HanifiYaumu
    @HanifiYaumu 23 дні тому +1

    Koma chakwera guys amangolora zilizose galu ameneu ndipo dzambuyo dzake inja

  • @DicksonChibisa
    @DicksonChibisa 23 дні тому

    Zilibwino kwambili the DC amakwana

  • @user-yh3dw6qu7z
    @user-yh3dw6qu7z 23 дні тому

    Iwe amalawi ngambiri ku mozambique,ndi adapanga maziko.zimenezo usadzakambenso.udzapezetsa mavuto abale ako.

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3re 23 дні тому

    Boni kalindo ukunena zoona zaku Rwandazi mmmmm koma Paul kagame yekha eeeeee!

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 23 дні тому

    ❤❤❤

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani 23 дні тому

    Bon kalindo Mumatimirila komaso zikumachitika izi tili ndi Mintery please muyese kuchitapo kanthu

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 23 дні тому

    Kod Abon palibe njila yoti president wadziko limenelo adziwe Koma amalawi ndife opepela

  • @user-im3gn6bp4e
    @user-im3gn6bp4e 22 дні тому

    Pangolin

  • @MalakamMillie
    @MalakamMillie 23 дні тому

    Chakwela ndi galu kwambili akupeleka dziko chifukwa chandalama aaa tatha basi

  • @SaliraRaja
    @SaliraRaja 23 дні тому

    Ndiamene ndikuziwila the DC

  • @IsaacKamwendo-bb7xz
    @IsaacKamwendo-bb7xz 23 дні тому +3

    Kodi military 🪖 ikuchedwa pati kulanda bomali eeesh malawiso mmmm

    • @PaulDaka-dc3re
      @PaulDaka-dc3re 23 дні тому

      Military yaku Malawi singathe kulanda utsogoleri aaata! Mantha 🤔🤔🤔😱

  • @user-tx7xz9kf1w
    @user-tx7xz9kf1w 23 дні тому +1

    achakwela abusa mumasewela ndi mulungu kufuna Kuba mbaka kunamizila ubusa chakwela ndi galu kwabas

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 23 дні тому

      Inu mukunvera kalindoyu? Zomwe iyeyu anayambira kuyankhulira zimenezi mumazidziwa??

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 23 дні тому

    N'sinje omwe ananena atupere mu 2019 lero wathera musiizi anati chakwera sanakhalepo nduna yaboma lero mumpase upresidernt palibe chingalongosoke lero ndiizi ndalama kumangobedwa kulora anthu obwera kupanga zomwe akufuna zinthu kumangokwera mwachakwera palibe chanzeru chingachitike kuposa kuvuta zinthu 😂😂😂😂😂

  • @user-hk2ow8ey2g
    @user-hk2ow8ey2g 23 дні тому

    Zona

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 23 дні тому +1

    Zachibwana zimenezi

  • @GraceLakatika
    @GraceLakatika 23 дні тому

    Yii tiziwona Chaka chake ndichino🙆

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v 23 дні тому

    Zoduka mutuzi tsiku lina tidzalila

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py 23 дні тому

    Ngat amalakhula zoduka Mutu ,oduka Mutu ndiwe umamvera bwanji ma oudio yake amakuuza Kuti mvera oudio Yanga? Siyeni azisegura anthu maso padziko lathu

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 23 дні тому

    Awa awamangaso sure.

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu 23 дні тому

    Atakumane ndi chakwera andi tumidzire please

  • @user-lp2sd7lt8b
    @user-lp2sd7lt8b 23 дні тому

    Openga iwe

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 23 дні тому +1

    Koma ku Malawi kuli asilikali?

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no 23 дні тому

    💔💔💔💔💔💔💔💔 zovuta

  • @AlickJinamu
    @AlickJinamu 23 дні тому

    Komatu achakela lindichi wbana

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 23 дні тому

    Satana wayamba kuonekaa ndi maso

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 23 дні тому

    Kama asilikali mukutani..?

  • @VeronicaMarten
    @VeronicaMarten 23 дні тому +1

    Kmt kalindo tidzamukumhukira ndizonduka mutu zakezo ine ndatero.

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 23 дні тому

    Akulu awa zambili amayakhula zoduka mutu

    • @MalakamMillie
      @MalakamMillie 23 дні тому

      Akunena zoonad DC koma inu athu Akufutikila simukuona

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 23 дні тому

    The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC

  • @user-iw5gg8ng3p
    @user-iw5gg8ng3p 23 дні тому

    He talks a lot of nonses.he is a hepoclite and a shavalute

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o 23 дні тому +1

    Kalindo chamba chinamuinga kwambiri moti mutu wake unasikonezeka kalekale palibe cha mnzeru chomwe amayankhula zonse zimakhala zoduka mutu

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani 23 дні тому

    Bon kalindo Mumatimirila komaso zikumachitika izi tili ndi Mintery please muyese kuchitapo kanthu