Enafe kuthekela tilibe, koma zikoli nchokhumba chathu kuti lizikhala ndi ulamuliro okomela aliese posaona kuti ndi wandala bwanji, all we do is kukuikiza mmapemphelo pa zabwino zimene ukupanga and pazuke gulu limene lili nkuthekela ngati mmene ulili iweo kuti zikoli tichose and tithane ndi azisogole ndi adindo opanda pake mziko muno , and zikoli likukanika kutukuka kuposa maiko ena chifukwa cha gulu lochepa chabe kubomako , God continue to bless you mr kamangila.

Yes I agree with you mr we need to change the system
At first I was not understand you but this time around eeeish you're playing great row in this nation
Mwati ndiyaliti kodi live iyi
Lerlori
Go ahead brother dziko lizasintha coz of you and God
kodi taonera kaletu izi pa facebook live page yake munthuyi
Ena sali pa Facebook Boss.
Please mulandu wa bakili muluzi ujaso muzauone bwino bwino, umeneuso ukulimbikisa katangale mziko muno.
Mwadula dulanso nanga chavuta ndichani?
Brilliant
Anthu omwe mukumayakhura Kuti uyu ndichitsilu onama
1/ anthu ake ndiomwewa akumatiponda ndichiphaziwa chilinga kufuula kwa anthu osauka kusamveke,
Zitsilu ndizomwe zikuti zakutulukazo ndizomwe ndimadya ndi mbava zakukhothiko, kuteloko akutsira nchinga mumpunga wanu zitsilu inu
Chilungamo chimawawa
Pano uyu anangosanduka chitsilu coz amangobwebweta
Ndipo inu kkkk kma anthu akanapita naye mwachangu ku mental hospital
You don't know what you are talking about
You are stupid yourself, he is opening our eyes.
anthu akatangale amabakilana ndikuomberana mmanja
@@gracem-y8p Ndatha kuona chitsilu chimenechi