DPP LEADERS PAY TRIBUTE TO MRS. ANNIE TAIBU - TAMVANI ULALIKI WA M'BUSA UYU - DPP LIVE TODAY
Вставка
- Опубліковано 5 лют 2025
- DPP LEADERS PAY TRIBUTE TO MRS. ANNIE TAIBU AND ADDRESS ECONOMIC CHALLENGES AND ELECTION REGISTRATION
Speaking on behalf of the Democratic Progressive Party (DPP), DPP Regional Governor for the South, Honourable Charles Mchacha, began by recalling the life of the late Mrs. Annie Taibu. Mchacha shared heartfelt memories of growing up together around the Bumbwe area, describing Annie as a sister who was dependable and someone everyone could rely on, beyond just family ties.
Turning to political matters, Hon. Mchacha addressed the ongoing fuel crisis in the country, noting that many people, including dignitaries and DPP officials, were unable to attend the event due to the lack of fuel. He acknowledged the broader economic struggles that Malawians are currently facing, including hunger.
Dpp aford and utm let's come together
Nice
Amen
Azibusa asiya kulalikira Yesu
Cadet pastor akuoneka ngati mfiti ndiposo
Lalikirani Yesu inu 2:45 2:49
😂😂😂 fire ma bomba abusa
Chakwela chakwela 😂😂😂😂😂 unya chaka chino
Atumiki itanitsani mapemphero kuti dziko lonse tipemphere, Chakwera Watikwana.
Anya ndi amako not Chakwera.
Yambaya😂😂😂😂😂
Km ndpo anthu atopa naye chakwera ulaliki ndi pamaliro pomwe chikangawa tatopa naye chakwera
Pempherani chakwera amwarire
Zoonadi abusa
Muuzeni kabambe asapange matama
Anthu atopa bas😂😂😂😂
Kkkkkk koma chaka chinu kuli kuswa kuswa basi zatopesa aliyense izi
Paja UDF ndi imene inakuikani pa mpando, koma simuyamika kuti UDF ndi mother wanu. Bakili Muluzi ngati muzimunyoza ngakhale munafuna kumumanga ndinu otembeleledwa
Anali Tanzania ukulakhulawe unali kukachasu
😂😂😂😂 at chigaza ineee
😂😂😂😂😂 ameni
Kusadutsa mwambo wachisoni malo achisangalalo kwa ena. Zomvetsa chisoni
Tatopa kkkk kut topi
Awa ummmmmmmmmm abusa a DPP
Gwirizano ndiofunika koma tizigwirizana ndi zipani zakuba ?
Chakwera ndi kape opanda nzeru nthawi anali nayo koma kupepera pano zamuvuta
Amen
Amen