Chibelekelo chikuyenda bwanji a maliro Koma farai uli bho ndi ankolo akowo ndendende Inetu ndi padela ndimadana ndi zachibwana kkkkkkkkkk Koma this team guys munabwela no mistake mumatinvesa kukoma
PADELA ndi chiyabwe cha mmudzi😂😂 ati "iwé ntchito umagwira ndi akazanga kapena ine, uwatumizira bwanji akazanga ndalama ? Azichita kuziwa kut ndimalandira ndalama zingat?" ..😂😂 Miss you FARAI😘 welcome Cindee kozatenga chiberekero 😁
Gututu more fire go for it funafunani muzapeza 😂😂 love you guys comedy ikubwera bho izikhala 1hr
kkkk kkkk. I am addicted to Tonde wadula, Mdyangu and Mfumukazi. #big up Frola Suya
Gututu Kanthu mkhama phwiti anakwatila njiwa kkkkkkkkkk osaphwekesa
I miss chiphwanya koma please
Chibelekelo chikuyenda bwanji a maliro
Koma farai uli bho ndi ankolo akowo ndendende
Inetu ndi padela ndimadana ndi zachibwana kkkkkkkkkk
Koma this team guys munabwela no mistake mumatinvesa kukoma
Kkķkk wayamba bwino Gututu keep on pushing
Kuzabwerera kwa namoyo
Love siona level 😂😂🤣
Gututu umayitha mkazi uwina meneyo keep on pushing😅😅😅😅
Woza woza Padera ...kkk..mkaka womwera kamba..kkkkk...
Giling'ande akusangalala kukhala mwamuna wa mfumu nkhani kulalata ndi chapabwalo
Gututu number 01, unditumizire size yako ya Nsapato. Well done
Mr gututu😂😂😂 Jumbo yalandilidwa osada kkkkk keep on pushing.kkkk proud of you my guy.❤
Kkkkkkk zithu zake
Iyi mwakunga iyi kkkkk
Kkk gututu mumakwana
Nice one zikuveka
Eish falai
Gututu zako ziyenda don't wary
Mr gututu mwaiphula basi
Gututu wapana kkkkk
Nice guys
Padela omweyo 😂😂😂😂
Kamba omwera more😮😮😮😮😮😮😮😮😮
😂😂😂😂😂😂😂 yafika peni peni nkhaniyi sopano sindi wafika koma nkhawa ndi yoti akakumana ndi gututu zikhala bwanji?????? Pamenepo mitima Ili dyokodyoko kuti tione
Kupereka ndi kwabwino you have to pay the price gututu😀😀😀😀 chiponda mthengo first
Koma iyi yokha mwachuna 😂😂😂😂 Ng,iling,ande sazatheka 😂😂😂
Ikalowa yalowa sibwelela jumbo pakwawo basi🥳🥳🥳🥳🥳
Mumakwana mabwana ndi madona
Akuno ,gututu wagwila mayi chisime
Jumbo yafika Mr gututu ❤❤❤
Padera umbombo kukula Shaaaaa
Apadela simasangalasa tisaname phunzilani Ku kita bwino flim mfumukazi apadela sakusangalasa tisaname
Mr gututu akufuna love😅😅😅😅😅🎉🎉
Farai wabwela ndi moto
Eeeh koma Padela aaah eeh iwe ndi one, umantha
Gilin'gande ukuntha mawu ngat pakwanu😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😀😀giling'ande ndi akazi wake amachita chikokota kwabasi, action yawonso simabeba bola adakapanga replacement
Keep it up guys you always make me smile
Abale takambiranani zinthuzi kumbali yanthawi ikuchepa kobasi sinankha zikutha zikukoma mukutisiya m'malere.
Guys keep it up mumatichotsa nkhawa
Pompano mukala mayi gututu osati mayi chisimeso ayi iyayi nkhani yabwino nditu mayi gututu
Munakawonjezera nthawi koma zilibwino tione kokatenga chiberekerio
Padela nchitsiludi ndithu😅😅😅😅😅😅😅
A padela sazatheka kkkk
Padera ndi Paderadi basi ndipo suzatheka😂
Akuti auzane 😂😂😂😂
Giling'ande tsopano kulankhula ngati ndipakwawo
kkkkk chomati kusuzumira mjumbo ndkumasekeleracho Mayi chitsime,, Mfumukazi anatengena nao chomwecho kwa giling, ande oooohooo
😂😂😂😂 mpaka lero ndi bañja... Pa malamulo adziko lino Giling'ande ndi mfumuBambo basi
Lavu siwona zimenezo😂......... Lavu ili pa mloza border
More fire
Number one
Gututu chonde ukapeza mpata tikumane.
PADELA ndi chiyabwe cha mmudzi😂😂 ati "iwé ntchito umagwira ndi akazanga kapena ine, uwatumizira bwanji akazanga ndalama ? Azichita kuziwa kut ndimalandira ndalama zingat?" ..😂😂
Miss you FARAI😘 welcome Cindee kozatenga chiberekero 😁
Agututu osadanda jumbo yarandiridwa
Gututu love ikuyenda ma kilometers angati kkkkkkk😅😅😅
😂😂😂😂ndirani jumboo
A Giling'ande mkomya wa tea, mwati muwaziziritse mtima a mfumu mwano anapangidwa ndi Farai uja?😜
Amuna muna ambalume kkkk che gututu
Gututu limbikira walora Kaye ameneo
Wafika Cindy oyeeeeeeee
Wolemekezeka bambo Padela
Padela are you related to Winiko?😂😂😂😂😂😂😂😂
Gututu sako sikuonetsa bas limbikira
Guys am proud of you 😂😂😂😂😂😂😂😂 gututu wapeza mkazi 😅😅
Ayi tathokoza pompano mukhala mayi gututu osati mayi chisimeso gututuuuuuuuu❤❤❤❤ mumativesa kukoma ife
Falayi emweto 😂😂😂😂😂 umakwana
🎉🎉😂 koma falayi
Gututu ukuilowa bwinotu ,,,,
Koma chiphwanya Ali kt?
Tafika
Macheza abwino ndithu
Anthu inuyo musazasiye mumatha heavy
Wabetsa pin Padera 🤣🤣🤣🤣
Best of malawi
Mai padera❤❤❤❤❤
Padera oyeeee😂😂😂😂😂
Nice
Giling'ande polani moto😂😂😂😂
😂😂😂😂koma padera😂
Apadera sazatheka 😂😂😂😂😂
Thanks
❤
Gututu uja simunthu wamba
😂😂
Gututu😂😂❤
Giling'ande pola🤪🔥🔥🔥🔥
Kodi sipakwathu
❤❤❤❤
Mumatimvesa kukoma pitilizani kutero abare
Farayi😂
Pali m'mawa 😂😂😂😂😂😂😂
Apadera polani moto
These guys are good cherish🎉
Giling'ande namulanda njingq