Only evil fools will not like what Mtanmbo said but he speaks with love and dedication to his country....zinangochitika but yhis guy wanted the best for the nation....
Mbambande bwana a mtambo don't give up my bro big strong we need your help plz my allah guide and protect you all the time allah akbar respect to 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🤲
Congratulations to our opposition chifukwa cha mgwilizano wanu pobwera poyera ndi mtima imodzi uku ndiye kukonda anthu ndi dziko lanu musasiyire pomwepo pitilizani ❤❤❤❤
Uyu ali ndi nzelu izi lero?? He is one of the guy amene anatiika mmavuto omwe tili nao pano ,,anthu inu pamsana panu you are fighting for your bellies not poor people,,MCP ,DPP ,UTM and AFORD onsewa si anthu abwino
Bakili muluzi tv ndimachini ananena kuti kwabwela smart matic
Exactly amwene
Only evil fools will not like what Mtanmbo said but he speaks with love and dedication to his country....zinangochitika but yhis guy wanted the best for the nation....
Mtambo chigewenga
you are good speaking Mr Timothy Tambo
Mr Ntambo yomweyo...... Moto buuuu🔥🔥❤️
Mbambande bwana a mtambo don't give up my bro big strong we need your help plz my allah guide and protect you all the time allah akbar respect to 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🤲
Keep it up guys,,God b with yu all our leaders,,nkhani iyi ndiyosakambiranadi iyaaa
Which God. Wa Baal Mtambo mkhito munaphetsa anthu osalakwa.
Mtambo waiwala Nkhani yaku karonga
Never give up Mr comrade we fear no death but defeat (this is not 1964 this is 2024)
Mtambo is back Moto undi Timothy 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Bravo Comrade. Osaopa osafooka osatopa
Powerful speech mr mtambo keep it up
Let's work together all opposition parties keep it up good work 😇
Muzichangamuka chonchi osati zopusa zija, we love you guys more than you know ❤️ ❤❤❤
M one of a big fun of you Mr, koma osatengela zotukwanazo timawerengera kuti tili Ndi anthu a mphamvu u are one of them..
More fire akatundo umakwana Mr Ntambo.
When I meet fearless Malawians...I feel proud to be born this era
Thank u Mr mtambo your speech is very powerful
Congrats good team mu matiyi milira
Vote ndiyanu kale mtambo❤❤❤😂😂😂😂
Yes yes powerful speech Mr mtambo ❤
Mr mtambo you should be AVP indeed
Our country needs peoples like you.
Tili pambuyo panu Mr ntambo❤❤
powerful speech comrade Mtambo
leaders unite !!
Bwana mtambo timenyereni nkhondo maso anthu ali kwa inu bas❤❤❤
Osaopa
Osafooka
Osatopa
Bwana mtambo timenyeren nkhondo
Mmakwana bwana timothy
Thats Original Comrade Mtambo more fire Comrade
We are speaking from experience not just a say big up Mr ntambo🗣️
Smart Matic musayilore imabera ndikuziwa ine ku Kenya sizinali bwino
Powerful speech Mr mtambo
I was waiting for you Mr mtambo, more fire
Congratulations to our opposition chifukwa cha mgwilizano wanu pobwera poyera ndi mtima imodzi uku ndiye kukonda anthu ndi dziko lanu musasiyire pomwepo pitilizani ❤❤❤❤
Makwana keep it up
ng'alulaaaaaa koma amalawi munalusa😂😂😂😂😂
Mtamboyu amakhalad nd amalawi just imagine my fellow youth ❤
The Boy Who Harnessed National Unity
Paja you always fight for your pocket. Zikakuyendera ukamadya ndalama umakhala ziii
Congratulations mtambo ❤❤❤❤❤❤
Powerful words Mr mtambo
Uyo nde mtambo ndimaziwa ine good job
Mtambo man of the moment
Ulemu wanu brother Timophy osaopa osafooka osatopo chilungamo
Dats my Comrade Timothy Mtambo I salute you
thanks mr mtambo for your speech
Zoonadi Zokha Zokha💪💪💪
Very good mtambo
Mutambo good speech❤❤❤❤❤
Mr mtambo God bless you 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Thanks mtambo you help us to remove dpp chipani chogawa Malawi chipani chokomela alomwe
Power said comrad ntambo
Going forward ❤❤
Good job
Following bro caryon❤❤❤❤
Malawian we will be power to people not to government
When it comes to this mtambo
Your the best.atrue patriot...
Iweyo tiyenawo agaru
More fire Mtambo
Good massage 🎉🎉🎉🎉
Mbambande Mr Mtambo
Bravo Mr mtambo
Tiri mbali yanu bwana maso aa malawi akuyang, ana pa inu ngat ntdogoreri olimba mntima
Big up bigy
Pajaso munthalika amakaniza jane answer kutula pasi udindo😂😂😂😂😂😂😂😂😂mwanyela mmadzi mwakhaula
Mr ntambo more fire
Big up Mr Timothy 👏
Uyu ali ndi nzelu izi lero?? He is one of the guy amene anatiika mmavuto omwe tili nao pano ,,anthu inu pamsana panu you are fighting for your bellies not poor people,,MCP ,DPP ,UTM and AFORD onsewa si anthu abwino
Ndipotu anthu awa satikonda olo mpang’ono
Better dpp inkaba koma zinthu zinkayenda awa akuba mwachimbulimbuli
Powerful man
🔥🔥🔥🔥Mtambo viva
Love you guys don't keep guite
Thanks Mr mutamba sure 10:54 😂
Keep it up ❤
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mkwiyo ochotsedwa ku boma mademo tinayambitsa ndife ndipo tinatseka zimenezo tamalimani tidye makobidi next year
Bakili muluzi more 🔥
zonadi 💪💪
Bravo opposition lets unite to make a better Malawi
Ndakusowani galu iwe Timothy mtambo
Yaah awa nde ndakatundu 💪💪💪💪
Nice speech
More fire Mr ntambo 🔥🔥
Ndipo akunama anya sanati sigwilisidwa kuno smart yawoyo makapewo.
Zoona zake brother ❤❤❤
Chakwera anapha Chilima full stop or atani mzimu ukudikira nayes adzafa siku lina Chakwera sakudziwa kuwawa kwa imfa ili ndi dziko adzaziona
Very good boos
Thanks mr mtambo nice speech
Yeo Yeo pawe pafupi nthe nakolako woko Wow
Good move opposition parties team up you will win
Big up to you mtambo
Kuyangula kwabwino kwambiri a Timothy ntambo timakunyadirani kwambiri
Kaliati is not enough and much in mtambo legacy
This is Comrade I know Mtambo anapha msilikali ndi mwala sapanganazo za phadazo Anakuikani pa mpando akuchosaninsoni
Ipondeni fadah🎉🎉
Amayo ku mtonso komweko auze ntambo🎉😂😂
Yes we don't want kanyamako
😂😂😂😂😂ayamba kale kulira ndíe akazaluza 2025 muzalira bwanjiiii😢😢😅
Uyu nkatundu mtambo❤❤❤
More fire Ntambo
Malawi needs prayers indeed
Uyuyu ndie ndiwachibwana akanamumanga ameneyu mesa ndi amene akasapota mcp nthaw yazisankho ija
Very nice powerful more fire
Good Messnge Mr Mutambo
Not good massage
Ndiwe wadyera Ntambo