MCP KUONONGA MA BILLIONS A AMPHAWI KUGULIRA OIMBA NDI MAMEMBALA A ZIPANI ZINA - KARONGA BOYS 28/9/24

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 8

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 19 годин тому +2

    Zoona Malawians tigwirane manja tichose mavutowa

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 20 годин тому +1

    Zomvesa chisoni misonkho ya amphawa chakwera akungogawa ....zosakhala bwino

  • @BrightKuyaka
    @BrightKuyaka 19 годин тому +1

    Koma muganiza kt Dan lufani payekha angawinitse chipani

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 14 годин тому +1

    Tupere asiyesere kutelo ayi zitinyasa wose

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 19 годин тому +1

    Koma agalu awa andikwana pa zaka 4 zokha kukhala ngati takhala zaka 20

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga 20 годин тому +1

    A chair mwachita chibwana mwadya .zomwezo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 9 годин тому

    Ai azavota oimba panopa ayamba kugula ma team sopano mumva agula team ya Liverpool ili pa no 1 ku premier league

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 9 годин тому

    Kodi mkulu iwe waiwala kale zimene inapanga DPP ku UDF? Mkulu iwe wabadwa liti? Gaza ndi Malawi zikugwirizana bwanji? Iwe tazingosapota DPP yakoyo kumbwambwama kwa mbuli ndikumeneko mzanu akachita bwino ndiwasataniki
    Iwe uzingotuwa anzako akuchita bwino. Get lost