DPP IDAONONGA INFRASTRUCTURE KU MALAWI - DR JOHN PAUL- TREASURE GENERAL WA MCP WAUZA BRIAN BANDA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 вер 2024
  • DPP IDAONONGA INFRASTRUCTURE KU MALAWI - DR JOHN PAUL- TREASURE GENERAL WA MCP WAUZA BRIAN BANDA

КОМЕНТАРІ • 54

  • @ChimwemweKamanja
    @ChimwemweKamanja Годину тому +4

    Brain boma agwesa yekha 😂😂😂😂😂😂 proud to Brian

  • @ChimwemweKamanja
    @ChimwemweKamanja Годину тому +4

    Aziyakha fuso amaneo osamagoti Dpp

  • @KenAipa-r3r
    @KenAipa-r3r Годину тому +3

    Kod njanji yake yaku Mozambique akunyadilayo ????

  • @KhooMadex
    @KhooMadex Годину тому +3

    I think Brian banda is a blessing to malawi

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i Годину тому +2

    Kma uyu akunama Dpp ikubwelera m'boma ndipo ulira sunati ife olo titavota lero Dpp ikhoza kuwina ndi 89 % osalawo mutha kugawana

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira Годину тому +4

    Sakuyakha ma fuso uyo

  • @stanleymollen7273
    @stanleymollen7273 Годину тому +1

    Sangaloze zomwe current government yapanga..Chixungu chimaonesa ngati munthu akunena za mzeru..Garbage...

  • @KelvinPhiri-z9d
    @KelvinPhiri-z9d Годину тому +1

    Tiwawonera amenewo akungwa chagada😂😂😂😂 njanjiyotu ndiyamozambique asatisokose ameneyo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani Годину тому +1

    Padziko lonss lapansi chsru choyamba kapen chidebe chophikira makata kusimba ndye ichi osamaiwal chitukuko cha 16tillion ijatu muitchule njanji ndye siyan Joyce Banda anatiuza kale

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Годину тому +1

    Kudzivuta ndi mtima uku... DPP ikubwera ndithu m'bomamo😂😂😂

  • @ChancyWilly
    @ChancyWilly Годину тому +1

    Zomwe mwapanga a mcp ndikubweresa njala komaso kugwesa kwacha zomwe anthu sazakuiwalani

  • @DavieAlumenda
    @DavieAlumenda Годину тому +1

    Kunama kopanda Nako manyazi ineyo ngwa ku nsanje komweko koma zomwe akuyamkha akuluwa nzabodza zokhazokha

  • @ElizabethMtuwa
    @ElizabethMtuwa Годину тому +1

    Taziyakhani mafuso bwanawe njanji ndi yamozabque.

  • @stanleymollen7273
    @stanleymollen7273 Годину тому +1

    Doctor kukanika kuyankha funso... Mediocre

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Годину тому +2

    Achimwene Mudziwopa MULUNGU

  • @HashimKanjanga
    @HashimKanjanga 2 години тому +1

    Awa ndi achitsiru bwnj 4yrs azitiwuza zanjanji

  • @ThanksKamlanje
    @ThanksKamlanje Годину тому +1

    Amariza bwanji njanji ndarama atagawana mkudya

  • @GiftGeliati
    @GiftGeliati Годину тому +1

    Kkkkk DPP my vote

  • @MussaJafali-q4c
    @MussaJafali-q4c Годину тому +1

    Achisilu awa

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 2 години тому +1

    Koma Ka background sound always do touch my soul! Who did that sound

  • @AlickyMatola
    @AlickyMatola 40 хвилин тому

    Brian doctor uyu akusepa mafuso😂😂😂😂 dpp 2025 boma

  • @kingstonekalonga8435
    @kingstonekalonga8435 Годину тому

    Brian mumatha akukanika kuyanga galu ameneyo angamuvotere ndani mbuzi yamuthu chakwera ndindani

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Годину тому

    Koma abale tikuziwa kuti ana anu akusangalala muziyankhulako zoopa mulungu plz plz ulendo wanjanji ife tizipita nazo kutiko

  • @YasinAdam-pn4bh
    @YasinAdam-pn4bh 7 хвилин тому

    Akuluwa atichimwisapo apa bola ndisunde kaye aaaaaa

  • @PhillipAcquaron
    @PhillipAcquaron 48 хвилин тому

    Njanji yake iti zoba ameneyu a Malawi angadye njanji chitsiru ichi

  • @ElizabethMtuwa
    @ElizabethMtuwa Годину тому

    Mwamuna wadzeru sabrama mwamuna wakare mukaone oterewa dziwani banja lamumvuta basi

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Годину тому

    Scandal after scandal...By the way which indicators , coz when we talk of inflation nde eeeeeehhh zosakambika

  • @mphatsomalenga
    @mphatsomalenga Годину тому

    Chabwino njanji ikugwila vepi koma zasintha moyo motani?

  • @FortyoneHarwa
    @FortyoneHarwa Годину тому

    Inu. M. C. P kwanu nkunama basi tidzakutchotsani m boma inu dzitsilu inu

  • @WakisaNjeghenje-i2n
    @WakisaNjeghenje-i2n Годину тому

    Dpp itenga boma chikwangwan ndizinkhale ng'oma

  • @AmirGeloo
    @AmirGeloo Годину тому

    Kodi amenewa amadziwa zimene akuyankha kapena akungoyayankha kuti akome kwa mabwana awo ?

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 5 хвилин тому

    Iwe chimutu chako mcp yakoyo fwetseke

  • @petrokagona1708
    @petrokagona1708 Годину тому

    Kkkkkkkk. Ndiye ma indicators kuti zinthu zikuyenda bwino ndi ati?

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 31 хвилина тому

    So angokamba za Dpp why malo moyankha mafutso? 🤔

  • @CarolyneGunda
    @CarolyneGunda Годину тому

    Anthu akuba awa akuzinamiza kuti awinaso kkkk koma MCP kkk umbava wakeo

  • @GerladMingu
    @GerladMingu Годину тому

    Khani ndi pa ground not on papers such as,he talks about minister of transport,what is that?

  • @PhillipAcquaron
    @PhillipAcquaron 49 хвилин тому

    Vuto nd ndalama chitsiru ameneyu

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 Годину тому

    Koma ma doctor aku mcp abale 😂😂😂😂😂

  • @AnusaChiwale
    @AnusaChiwale Годину тому

    Akulu yankhani funso straight

  • @francismungu7749
    @francismungu7749 Годину тому

    Uyu ndising'anga akuoneka makani 😂

  • @WakisaNjeghenje-i2n
    @WakisaNjeghenje-i2n Годину тому

    Maboza basi tatopa ndizaboza a mcp azaona 2025

  • @UmaliIshmael
    @UmaliIshmael 29 хвилин тому

    Anthuwa ndi oyipa awa

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Годину тому

    Abwana muli ndi wabodza

  • @Kiyamachilipa
    @Kiyamachilipa Годину тому

    Yankhani chilungamo

  • @LastbornEnd-r9c
    @LastbornEnd-r9c Годину тому

    Uyu machende ake

  • @mphatsofost
    @mphatsofost Годину тому

    Awa ndiwupenga

  • @WilsonMbendela-d4o
    @WilsonMbendela-d4o Годину тому

    Achisiru awa

  • @MussaJafali-q4c
    @MussaJafali-q4c Годину тому

    Achisilu awa

  • @MussaJafali-q4c
    @MussaJafali-q4c Годину тому

    Chizilu inu

  • @LobertSamuel
    @LobertSamuel Годину тому

    Awa amatha mr brian

  • @LobertSamuel
    @LobertSamuel Годину тому

    Kkk