BAKILI NDI ATUPELE YAWAGWERA NKHANI IJA - WASAMBA MMANJA AISHAH MAMBO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 48

  • @MouliceChikapa
    @MouliceChikapa 9 годин тому +2

    Zikungoonetsa kt chomwe mukuchita smukuchidziwa tonse ndi ife amalawi nde chooyankhulila mu chiyawo ndichan zikungotanthauza kt Oro mutawina upere ndekuti zonse muzazipanga kudzela nchiyawo ,,,,,,,zosankhanazo ndizomwe tikuukanazo ,

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 12 годин тому +2

    Momwe mwatelemu ndiye kuti chipani Cha UDF chatha ndipo muyembekezele kuluza or ma Mp ambili sumawapeza anthu a UDF tiyeni tiyendele limodzi tipite mu zipani Zina monga DPP afford ndi UTM bs zinazo zitayeni ndi achina UDF awowo

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 10 годин тому +2

    Naweso Ayisha mambomo bwanji ukuyankhula mchiyao mwakomo ukufuna ife sitinve nawo kelekete kelekete chiyao chakocho kumapete ukumalizira chichiwe koma naweso😂😂😂😂

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z 8 годин тому

      Eti ine palibe chimene ndamvapo 🤷🤷🤷🤷🤷

  • @RukayaIssah-h7t
    @RukayaIssah-h7t 8 годин тому +2

    Pena zikundidabwitsa kuti bwanji atupele ndi bambo ake ali duuuuu osalakhula chilichonse since ngozi ija chichitikireni

    • @charlesmbewe4001
      @charlesmbewe4001 6 годин тому

      Bakili muluzi sangayankhule kanthu chifukwa paja amuchotsera mulandu uja ndiye wadya banzi akakhala Atupele anatha amene uja akuwaseweretsa amalawi

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 14 годин тому +1

    Azimwale andalama awa cholakhulira chiyao ngat chipanicho chayao bwanji

  • @SandraBanda-hd1li
    @SandraBanda-hd1li 9 годин тому

    Aisha.., wagulitsa . ndi. Lilian. Patelo.... asakupusitseni..... akulu akulu.... tidzaliratu. Patsogolo

  • @MoyendaLucas
    @MoyendaLucas 11 годин тому

    panjanso atupere ndimchewa ndichifukwa akufuna kupanga alayasi ndi mchewa mzacheyo tizaona 2025

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 14 годин тому

    Amuluzi dpp yawazuza mokwana komaso inawachita chipongwe moti Atupele chonde ganizani mofasa dpp imafunafuna kuti ikuthesereni chipani

  • @OmexMainala
    @OmexMainala 13 годин тому

    Zopusazokhazokhabas zikuineselatu kut mulimbaliya mcp kaliwen muzazivotela nokha

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 14 годин тому

    Nambo achakulungwa manyilile the invitations ungwi nambo yawogoya ,Aisha Mambo sampano tupikene nsampano tupochele uthengawo wanuwo ,😅😊 nsampano tindende ULI Aisha ??

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 13 годин тому

    Tiye nazo kuchenjera kumeneko kutha aise Malawi anadzuka pano 150million udzalira mchiyawo uone nonsense

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 11 годин тому

    Kodi comrade ntanyiwa nkhamiyi wayinva pena amabakera atupere ndi Achair nanga apa akuti bwanji ?uyuyu wasambamo mmanjatu akuti achair ndi atupere akuziwa bhobho za kuyitanidwa kwa MCP shame on you people for UDF.we will not trust you anymore chifukwa penapache ndinu ang'oma yaganda iya

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 13 годин тому

    ndakuvetsa zachiziwikire anthu amenewo adapha nawo Shani, ndakuva sister, anthu oti adawaphera akuziwa kathu tidangoyiwala that guy is evil remember matafale

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 9 годин тому

    Chokan makadeti mukufuna kumagwilitsa tchito athu ngat audf chosecho makadeti

  • @MusaWilliam-t8n
    @MusaWilliam-t8n 10 годин тому

    Ife ngati masapota a UDF dzamanyi ayi ngati wadjandalama ndidzako ife tikhodza kukugendani

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 10 годин тому

    UDF TU NKHANIYI SIIKULIMBIKIRA. NKHANIYITU YACHOKERA KU DPP NDI AMENE AKUYANKHULA PA SOCIAL MEDIA.DPP NDIYE MDANI WANKULU WA MCP CHIFUKWA ANAPITIKITSA MBOMA ASANAMALIZE KUBA.

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 13 годин тому

    Km zowatenga anthu ngt opusa sidxabwino udziwe sudzavota wekha ovota ndi anthu ndye mukanakhal kuti mumaona mavuto aanthu sibwezi mukupanga zopusa zanuzo mai

  • @AminaMpulula
    @AminaMpulula 13 годин тому

    Iwe aisha iwe ndichitsilu kwambiri iwe garu kwambiri wadya ndalama ya mcl wekha ndiye iwe ukumutenga mmalawi kukhala chitsilu chaiwe hule wachabe chabe zonse zimene ukupanga ukuyesa anthu sakuziwa samala ufa posachedwa garu iwe ukuyankhula chiyao bwanji chipanichi ndi cha nthundu wina uli onse samala phwanga ndakuchenjeza chaka chino ndi chomaliza kukhala kupaliyamenti kukakhals pakhomo kapena kumanda be careful

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 13 годин тому

    Ndi chisiru kumene iweyo ngt sukudziwa udziwe lerol ndwe opepera wamva osanena zoona kwauza anthu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 14 годин тому

    Atcheya and his so called son ndi athu osakhala bwino ma betrayer,atupele si mtsogoleri ndanena ndanena period

  • @AzencoNjirima
    @AzencoNjirima 11 годин тому

    kod simungamayankhule chichewa kupangila enafa?

  • @EthelOsman
    @EthelOsman 10 годин тому

    Ifeno timva chani simungayankhule chichewa aaaa

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 13 годин тому

    AISHA MAMBO NDIWE KANYIMBI KUNYASA KUCHIKAMWA KONUNKHAKO

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano 6 годин тому

    Vito lanu mukukonda ndalama mudya Za satanic

  • @EllahChikwatu
    @EllahChikwatu 10 годин тому

    A tupere nd mamuyesa ngat nd oganiza bho

  • @RaheemMogoya
    @RaheemMogoya 14 годин тому

    Inu athu akutulukan ndivuto zainu akumipando

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 12 годин тому

    Ndiyeno pangani cas asabwere mcp bas

  • @FrankRabson-q6j
    @FrankRabson-q6j 14 годин тому

    Ndiye potenafe sitivachiyawo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 11 годин тому

    Kagendeni amene wa MCP aliyense.

  • @AtupeleChitenje
    @AtupeleChitenje 12 годин тому

    Mulibe zeru achina kholokolo

  • @chikalabuba9045
    @chikalabuba9045 13 годин тому

    lwe aisha ndiwe ngalu nditu

  • @MariaNyamwera
    @MariaNyamwera 14 годин тому

    Nde ife tikumva zimenezi aaa

  • @MussaRafael-d4q
    @MussaRafael-d4q 8 годин тому

    Salani ndi udf yanuyo

  • @CharlesNamanjo-l2b
    @CharlesNamanjo-l2b 9 годин тому

    Ndiwe galu kwabas

  • @JoyceMiles-f5b
    @JoyceMiles-f5b 10 годин тому

    Mwapanga zibwanatu

  • @MouliceChikapa
    @MouliceChikapa 9 годин тому

    Tulan pans udindo

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 11 годин тому

    Kwavuta UDF yatha

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 9 годин тому

    UDF yatha basi

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 14 годин тому

    More 🔥 Aisha Mambo

  • @SayidiMisessa-x6y
    @SayidiMisessa-x6y 8 годин тому

    Uyu si Aisha Mambo ayiii bozairi

  • @CharlesNamanjo-l2b
    @CharlesNamanjo-l2b 9 годин тому

    Hule iwe

  • @LuwisKaigwaze-gr6cg
    @LuwisKaigwaze-gr6cg 15 годин тому

    Nde uthengau ukupita kwa ayao basi?

    • @mollymasangano473
      @mollymasangano473 15 годин тому

      Ayi si ayao wokha ayakhulanso chichewa athathauzila

  • @KelvinSymonmatope
    @KelvinSymonmatope 9 годин тому

    Ndiye kuti bakili anapanga nawo chiwembu chopha shanil ndipo zinamisangalatsa kwambiri