Ras Chikomeni Chirwa

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 42

  • @africulturetv6498
    @africulturetv6498 2 роки тому +8

    Chikhomeni is very bright than Chakwela and chilima
    Vuto anthu anzeru Koma osaphunzila amakhala ngati amisala
    People confuses him chifukwa he is a RAS but he is great

  • @skyperlizz7193
    @skyperlizz7193 2 роки тому +2

    This man is so wise
    Chikomen is great historian ever seen

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 5 місяців тому +1

    That Man is very intelligent mwana wa nyakayange

  • @jessienkhoma2492
    @jessienkhoma2492 2 роки тому +3

    Rasta satchena isiyeni nsapato yo akudziwa chimene akuchita inuyo tangonvelani uthengawo

  • @giftulemu9470
    @giftulemu9470 2 роки тому

    I can see chikomeni he is a great mn ndipo mutu wake umalingalira . Akulakhura chilungamo chokhachikha🤜🤜

  • @alliemussah2998
    @alliemussah2998 2 роки тому

    Koma zoona zokambaza zake muthuyo muli nzeru ndithu ndipo zoti amasuta chambazo zikhale poterepo ambiri tikuziwa kufunika kwachamba n y azungu amachikhomerera ndiposo we now kut malamulo amenewo okhuza chamba ndi opangiridwa for sure *FREE UP GANJA*

    • @aishahabdullah3660
      @aishahabdullah3660 2 роки тому

      Tizavotela inu achikomeni 2025 yi mwina zizakhala better

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Рік тому

    He was talking sense though only that black people don't listen to the fellow blacks

  • @assimamatola7791
    @assimamatola7791 2 роки тому

    President chikomeni chilwa 2025 to lure the country

  • @louisbonongwe4864
    @louisbonongwe4864 2 роки тому +1

    The guy has sharp mind

  • @princemartin3750
    @princemartin3750 2 роки тому

    Ras chikomeni is gonna be a best president ever before

  • @aishatawakali9017
    @aishatawakali9017 2 роки тому +2

    Who is here in 2022?

  • @eliahchidenga6015
    @eliahchidenga6015 2 роки тому +2

    Chikomeni looks smart In mind

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Рік тому

    Chifukwa chachani mwqpanga zoom sapato yake?anthu antundu ngati umeneu ndamene amakhala anzeru makamaka ma Rasta

  • @grevasiokajiwa931
    @grevasiokajiwa931 2 роки тому

    This guy is right

  • @alickhassan181
    @alickhassan181 2 роки тому

    Ndeinuyo mujambula sapato

  • @lawrencepatson6388
    @lawrencepatson6388 2 роки тому

    Koma Nsapato ya Apuleyo ai 2025 M'bomaaa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌

  • @sailimwale2806
    @sailimwale2806 2 роки тому +1

    But i don't understand why you did zoom your camera on his shoes; i feel it is out of place; but maybe as Zodiak you had reasons enough.

    • @Benty_Pro
      @Benty_Pro 2 роки тому

      It Doesn't make sense at all

  • @africulturetv6498
    @africulturetv6498 2 роки тому

    RAS chikhomeni go a brain than those we thought there are good

  • @amosmaseko1825
    @amosmaseko1825 3 роки тому +3

    Chojambulira nsapato ndi chani

  • @madalitsomakawa9708
    @madalitsomakawa9708 5 років тому +1

    great interview
    all the best Rasta

  • @d_vrdlovec8724
    @d_vrdlovec8724 5 років тому

    thanks for bringing this to us

  • @pattaika3507
    @pattaika3507 2 роки тому

    After 3 yrs lero zachitikadi mmalo mopanga chitukuko alibuzy ndicampaign yet progress iliyonse as nation development palibe

  • @erickondowe8781
    @erickondowe8781 2 роки тому +1

    Koma the dude is wise ndithu 😀

  • @graciouslokoma7431
    @graciouslokoma7431 2 роки тому +1

    nice video🥳

  • @doctormutano5717
    @doctormutano5717 2 роки тому

    haaaaaaaaaa Apule a 2025 nsapato yakeyoo.kkkkkkkkkkkkkkkkkkk ayi zikomoooo

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 6 місяців тому

    Mchazerutu🎉😂

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 2 роки тому

    Munthu wachikomeni uganiza boh mwaumuthu bro

  • @tonnybersonmwawa3908
    @tonnybersonmwawa3908 2 роки тому

    kkkkkk koma iwe ase kaya ndi Fodyaaa ukumudya mowonjeza
    choncho ukhale president kudwaalaaa chani.
    tabangosutani, masewela eet. malawiyi kuti azidzangofuka fodya yekha yekha2

    • @bigga1093
      @bigga1093 2 роки тому

      Very stupid comment u sound like ur brain washed he's actually got a very good point if u listen and Overstand kuzolowelera kulamulidwa ndi ma foreigners

  • @frankkamunde4575
    @frankkamunde4575 2 роки тому

    wakumana naye waganja raster man sagonjetsdwa koma amagonjetsa

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 2 роки тому +1

    Kodi mulikuti chakwera akuononga zinthu

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 2 роки тому

    Kkkk woyase nyabhingi

  • @ibrahimjacksons7545
    @ibrahimjacksons7545 2 роки тому

    🙏🙏🙏🙏

  • @_mindview_7707
    @_mindview_7707 2 роки тому

    Ku Malawi nkobheba