BON KALINDO WANG'ALULA LERO ZA A SULEMAN __7 January 2025

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 7 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 38

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 17 годин тому

    Ndipo iweyo the dc unanenapo....kuti .....azigo wamanga .....Anthu...amene akuwaziwa.....kuti...awawa timvutisana..nawo....azigowamanga...eeeish.....Boni kalindo...iweyo ndi Team yako yonse❤

  • @Anney-w1j
    @Anney-w1j 15 годин тому

    Kufa kufa olo mutimange sitingakuvoteleni inu achikangawa 😢😢 the DC musazafe mumatiimilila ❤❤❤

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 6 годин тому +1

    Iwe anabelo john tembo tsikulizafika uzalira pazomwe ukuchita

  • @CatherineMsaya
    @CatherineMsaya 16 годин тому

    The DC ❤❤❤❤

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 7 годин тому

    Iye akupanga zandale osati artist wabodza wangobisaliramo

  • @HopecinoChalira
    @HopecinoChalira 17 годин тому

    Kalindo ndi gwaza wakumalire kkkk

  • @FelixAkileni-m6f
    @FelixAkileni-m6f 18 годин тому

    Mdima ungakule bwaj kunja kumacha bac mulungu ali nayo thawi sangalore kt amalawi azingolira tsku lina tzayimba nyimbo

  • @ChristopherMwamasi
    @ChristopherMwamasi 16 годин тому

    More fire A DC

  • @YasperZulu
    @YasperZulu День тому +1

    Dc bon kalindo ❤❤❤

  • @AnnieZiba
    @AnnieZiba День тому +1

    Abishop anawakanika nkona akudelera Andale

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 21 годину тому

    Bon Kalindo kuyankhula kwanu kuli kolimbikitsa amalawi potsata chilungamo.Retirement age yaopsa mdziko la Malawi and radio station zotchukazi zafa posanena zakupsa.

  • @IsaacChitaya
    @IsaacChitaya 17 годин тому

    we don't have leader here in Malawi ,palibe chimene boma limapanga

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl День тому

    The dc born kalindo ❤❤❤❤❤

  • @VIOLETKENNEDY-co3tq
    @VIOLETKENNEDY-co3tq День тому

    ❤❤❤❤❤❤ I like you munabwera abwana

  • @Mosa-b6g
    @Mosa-b6g День тому

    More fire ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @MussaSeleman-k8v
    @MussaSeleman-k8v 23 години тому

    Koma guys mcp zomwe ikupanga ndisabwino koma 😢😢 please bon kalindo tiyimilileni

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 День тому +1

    Tikamati Boma ndilomweli Kodi mukuona ngati tingoyankhula?
    Chakwera wadutsa kale…16th September is just a formality 😅

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 7 годин тому

    Ife tadiya kumusaporter born kalindo amene akumusapoter Ndi anzako a DPP omwe akukupasa ndalama kuti axiipisa anthu axipani zina zosusa artist sukhala Ku mbali ya zipani koma mbali ya aMalawi akuzuzika zaziwika kuti akutuma Ndi DPP tamuyulukira

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa День тому +2

    Am waiting someone to be the first to comment

  • @CharleyAllan-p8f
    @CharleyAllan-p8f День тому

    Bon Kalindo kwatsula kuti akubatu mwalemekeza kwambiri ine ndikuti achuluka akupha

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl День тому

    Joni boys simagawa maswiti sitilola za manyi ife timayenda wofa ifa

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 7 годин тому

    Iweyo sungathe kuwagera aMalawi sungati Dpp ndiysbwino pomwe ukuziwa kuti Ku mzuzu anthu ochuluka anawomberedwa bwanji sukuwafera mabanja anaferedwa pama Demo wangobisalira Ku artist KO aMalawi siana Oti uziwanamiza

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 19 годин тому

    Bwenzi pano agaluwa kulibe, kkkkk

  • @BwanaGD
    @BwanaGD День тому

    Ndipo zoona ndawonapo ine munthu akamagonja ndewu amachulutsa zochita kuluma kukanda kugenda umagodziwa kuti uyu ndagonjetsa bas chakwera akugotitayutsa nthawi uyu ndimakape azakewa

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o День тому

    Komatu zomanganamanganazi tsiku lina wina azawafera ku police komweko. Pamenepo mpamene azaziwe kuti Kuchenjera kwina kumakhala kupusa ooho. Nkhani ya Chilima sinaziziletu, akuputanso zina?

  • @ChristopherKachepa-n4x
    @ChristopherKachepa-n4x День тому

    Iwe chakwera tula pasi udindo wako

  • @LIMBANIALISON
    @LIMBANIALISON День тому

    ❤❤❤u

  • @BlemaMasache-y5b
    @BlemaMasache-y5b 23 години тому

  • @JusticeNyirenda-y9e
    @JusticeNyirenda-y9e День тому

    ❤❤❤

  • @MorrisOwenSeleman
    @MorrisOwenSeleman День тому

    They are decampagne themselves, advisers where are you?

  • @ChikondiKatungwe
    @ChikondiKatungwe 23 години тому

    Zamphanvu

  • @YasperZulu
    @YasperZulu День тому

    Good speech ❤❤❤ 13:20

  • @YasperZulu
    @YasperZulu День тому

    Good speech ❤❤❤

  • @NdaonaMsowoya
    @NdaonaMsowoya День тому

    Ife kuno zopusa mayazi ndipo tikoza kumusowesa chakwla mumamutamayo kanthawi kochepa

  • @YasperZulu
    @YasperZulu День тому +1

    Good speech ❤❤❤