Thanks man of God and God bless you for everything kulungule ngintando yake siyamuthanda ujesu inzisuku zonke malibongwe igameni le nkosi ya sezulini amen
Thanks man of God but lets also pray hard for Chakwera's protection because in the spirit i see him sorounded with enemies and right now are very busy planning to frustrate him more...May God intervene
Though am not your fan, but the last part of has a point. We really need to have national day of prayer for our country. We really need Yehova at this time
Anga fiyile bwanji adzawayeletsa Ngati matalala tiyeni timudetse chakwera Koma mulungu alinaye cholinga akanakhala wina chakwera Ku tcheu anthu akanafa ambili Koma sanatero to save people akudziwa kufunikira Kwa anthu
You are a worse sinner than Chakwera,yet you want him to be punished? Because you are full of anger and malice which is sin,so who is sinning here btwn you and Chakwera?
Malawi be wise.,..Kodi ma prophecy bwanji akubwera after accident not B4 accident. Chomwe ndimaziwa true prophecy izibwera before events not after izo timati zaboza. Don't take advantage pa ma situations adziko save God with honest heart....muzakolora....why don't prophecies to chilima before kumuwudza zomwe mukuwona and why now. Osawanamiza Malawi....
Palibe odziwa Koma kudziwa kuchokera kwawina sitingadziwe tonse ai never in life every where you go white black people we need to share to know something
Ndimaganizo chabe popeza enaso akuunikila zomwezo osati kuti Mulungu wakuuzani ayi I know you pastors or ine ndikhoza kuwawunikilanso a president kuti asnkhe Ku utm and it's obvious
What mistake you saw man of God in the world of spirit?I need to understand that because you have already shown us that your a man of God who doesn't want to hide or keep anything secret
I'm following you a lot these days but is this prophecy coming through the iPad or what why are you reading it from your iPad..... maybe is just your massage to Malawi
You are one of fake prophets if I may say coz God cannot contradict himself,last time you said Chilima will stand on ballot paper,so you were just fabricating? Other thing you lack spiritual maturity on how to deliver your so called false prophecy
Thanks man of God and God bless you for everything kulungule ngintando yake siyamuthanda ujesu inzisuku zonke malibongwe igameni le nkosi ya sezulini amen
Muwapitire konko Achakwerawo mukawauze kuti akavesese akanyozere wokha Man of God
Thank you man of God
Thank you man of God, 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Thanks man of God but lets also pray hard for Chakwera's protection because in the spirit i see him sorounded with enemies and right now are very busy planning to frustrate him more...May God intervene
Though am not your fan, but the last part of has a point. We really need to have national day of prayer for our country. We really need Yehova at this time
Indeed Israel was saved by the word of a prophet.amen
May God Bless you more man of God
Zoona izi Chakwera anasanduka satana anasiya ntchito ya Mulungu ndiye zitonzo sizingamuthere komanso dziko ngati Malawi mavuto sangathe chifukwa otsogolera wadzadzidwa ndi ziwanda
And David and Solomon did as well
Thanks Amen
If you says like this truth man of god people they will love you also god he will protect you everywhere you're 🙏
Man of God ndamvera prophecy ndiye ndili ndi funso kuti popeza zinthunzi ndizofunikira kwambiri simungathe kupeza mwayi wokumana nawo a President? kuwafotokozera mwina achite kukana wokha
Ma prophet abodza why not coming earlier to the country that skc should not board aplane
Ma attention seeker awa.
Ambuye atikhululukire a Malawi pa zomwe Tinachimwa tikugoja pa maso pano
God bless you , I wish to meet you
A very good idea man of God.
Ndiolotse mkakutafune😢
Amen man of God
Amen man of GOD
Iwant chakwera to be in trouble, why why why because he chilima, MAHSRIP 😭💔💔 humble person
Anga fiyile bwanji adzawayeletsa Ngati matalala tiyeni timudetse chakwera Koma mulungu alinaye cholinga akanakhala wina chakwera Ku tcheu anthu akanafa ambili Koma sanatero to save people akudziwa kufunikira Kwa anthu
You are a worse sinner than Chakwera,yet you want him to be punished? Because you are full of anger and malice which is sin,so who is sinning here btwn you and Chakwera?
God for give us
It is my prayer too
Ndikukumbukira prophesy yanu munati SKC achite sisankho mwachangu chotuluka mugwirizano before it is too late, he had chance to become a president.
So touching Prophet
Palibe mneneri mu bible anatenga mbali ndi dziko ayi ndale ndi za dziko . Bwanji osatiuza mau osati za ndale.
Malawi be wise.,..Kodi ma prophecy bwanji akubwera after accident not B4 accident. Chomwe ndimaziwa true prophecy izibwera before events not after izo timati zaboza. Don't take advantage pa ma situations adziko save God with honest heart....muzakolora....why don't prophecies to chilima before kumuwudza zomwe mukuwona and why now. Osawanamiza Malawi....
Amen
Vuto lake ma prophecy akumakhala opeka coz ambiri mu kunyika kwambiri ankolo...I think mukugwilotsa ntchito momwe zinthu zikuyendela.
I was thinking the same
Tachimwa ngati dziko / achakwera achimwa ngati mtsogoleri wadziko? Man of god ndithandizeni kumvetsetsa.
Mwachimwa nokha Ife sitinachimwe nawo, nde machimo anuwo musaphatikize Ku dziko.
Osakawaiza kiseli bwanji in private. Ma prophecy opeka awa, and why are you telling it to the public? You want publicity right?
Na iyi apha ishiii
Wapha ndani nanu inu are that ignorant?
Nanunso kkkkk anzanu abvomereza Inu mukufunsabw kuti wapha ndani
Kkkkkkkkk! Phumatu osadikila kuti ndimvele kumapetoko eti , apa ndinangoziwilatu kuti ndanyula 😂 ! Koma akunena nkuluzi ndi zachiziwikile akuenela kutero bsi so zitengela kuti chakwelayo amaganiza bwanji bsi
The prophecy could have come before events unfolded. Too late to save Jerusalem from fire!
Zamasiku otsiliza inu
Dziko limayendera malamulo osati zofunaza munthu, ngati malamulo akuti vp achokerer ku UTM chakwera apanga zimenezo , komaso ngati ayi asankhaso yekha ,but liyabunya asanamizire mulungu ayi, liyabunya ndi wa DPP ndipo komaso akamati dzikolachimwa,akutanthauza chani, bwanji sanawauze amutharika mmene ankasaka alubino ngati mbuzi,iyi ndi imfa yangozi tidikire ofufuza osati wina aoneke ngati mneneri ayi, 2020 liyabunya adalosera kuti ngakhale chisankho chlkubwerezedwa DPP iwina,koma sinatibulidwe otengeka ndi uneneri zitengekani shalom
Exactly but MCP failed to deliver
Ndimakuvetselani mwachidwi aprophet pitilizani kutiwogolela ngati mkotheka ndineneleni ine
I dont trust prorphet i
Only trust my true God ❤️ God is one i dont trust a fake people Who dreaming Beer ntonjani kabanga cattle lite
True
Komatu mulungu tisamuseweretse kudzera ku ndare please please 🙏🙏🙏🙏
Alise ndiwoziwakale osanamapo yapa
Palibe odziwa Koma kudziwa kuchokera kwawina sitingadziwe tonse ai never in life every where you go white black people we need to share to know something
This is true
kkkkkk🤣🤣🤣🤣🤣🤣 kodi uprophet wayinu ochokela kwandani? ndiwandale etii
Odala amamva chizuzulo
Mr prophet why don't you come straight to the main point of prophecy's what's God shows you,but you go far around
Mukufuna Kuti apheso Wina wa UTM eti
Pena ati ma prophet amagwiritsa ntchito calino, chovala pankono. Izi not from heaven
Oowo ukudziwa eti masiku otsiliza
Anthu tazindikiratu masiku anu kuti amagwiri ntchito kalaino
Keep prophesying
Koma zinazi kungoverapo basi
paja tu zako ukumuuzayo amayakhulaso ndi mulungu nde akuuza iweyo bwanji osamuuza direct busa zakoyo
Ndimaganizo chabe popeza enaso akuunikila zomwezo osati kuti Mulungu wakuuzani ayi I know you pastors or ine ndikhoza kuwawunikilanso a president kuti asnkhe Ku utm and it's obvious
That's a very big mistake again using utm
You seem UTM
Za masiku otsiliza ma prophet adzagwilitsa ntchito kalaino mmmmmm
Monga dziko tachimwa , wachimwa yekha ka😂
😂😂😂😂😂
Speak direct
What mistake you saw man of God in the world of spirit?I need to understand that because you have already shown us that your a man of God who doesn't want to hide or keep anything secret
Uneneri kapena maganizo anu?
Well articulated Prophet
Prophets of the last days,some of them are real and some of them are false.
I'm following you a lot these days but is this prophecy coming through the iPad or what why are you reading it from your iPad..... maybe is just your massage to Malawi
False prophets!!!
Inu prophecy osadikira anthu anenekaye maganizo awo.this is obvious.

Lies
Amen