Chimene Chinapha a Chilima Cheni Cheni | Malawi Latest Prophecy

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 29 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 291

  • @AlexNjanje
    @AlexNjanje 3 місяці тому +5

    Go deeper Man of God ndipo ifee tikufuna kumva zoooona zeni zeni zokhudza imfa ya a Vice athu omwe timawakonda koposa ndipo musachite mantha ndibwino kufera chilungamo monga momwe anachitira Mwana wake obadwa ekhaa mkutiferanso chifukwa chazochimwa zathu choonadi sichiwawa Man of God may be with you all the time

  • @AndrewPhiri-y2d
    @AndrewPhiri-y2d 2 місяці тому

    Zamveka. It's our prayer zichitike fast

  • @JamesMartins-tf8qr
    @JamesMartins-tf8qr 3 місяці тому

    Mawu amalenga Mr preacher man tikunena nkhani yamugwirizo chakwera anganene bwanji kuti ndidzaimanso pamene Pali mgwirizano walowetsa nyangayo ndi chakwerayo

  • @VeronicaMatiki
    @VeronicaMatiki 2 місяці тому

    If the president is not involved ndiye kuti Bomamo a pulewo sadziwa za matsengazo

  • @stanlychibwato-xr2uv
    @stanlychibwato-xr2uv 2 місяці тому

    yes tikumvetsela

  • @bettiemgamphula6275
    @bettiemgamphula6275 3 місяці тому

    Where can i meet you Man of God

  • @EnockBwaila
    @EnockBwaila 3 місяці тому

    Mkulu ukuchulutsaso macheza penapake zinazo ukambabe kaaaaaa tiye nazo macheza ayi aaaaa

  • @RonicSouza-sk5ux
    @RonicSouza-sk5ux 3 місяці тому +1

    Owoh

  • @DilaGerald
    @DilaGerald 3 місяці тому

    Munakawakakamiza a Saulos kuti aonane Nanu pa nthawi iyo .

  • @rhodamsiska
    @rhodamsiska 3 місяці тому

    Akuti tu mgwirizano

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 місяці тому

    chakwera ukuzeke kukuthira unyolo

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 3 місяці тому

    Koma tsiku lina tchulani mayinawo mitima ikuwawa

  • @alickmathias2097
    @alickmathias2097 3 місяці тому

    You true Ms of God 100% true

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 3 місяці тому

    Nkaka kupelekera ma pepala maso akuluo munthu oyipa!!

  • @francisntonya171
    @francisntonya171 3 місяці тому

    Kmbe mkovuta aztumik a mulungu kulemekezedwa, so mmmmhu

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 3 місяці тому +1

    Wabodza iwe

  • @FalistaNjeri
    @FalistaNjeri 2 місяці тому

    Machende ako busa onyenga

  • @anniezovu2620
    @anniezovu2620 2 місяці тому

    Amalawi titan kut tikozenso tsogolo la malawi

  • @Memorykamanga-qb7eo
    @Memorykamanga-qb7eo 3 місяці тому

    𝐇̰𝐨̰𝐰̰ 𝐦̰𝐚̰𝐧̰𝐲̰ 𝐡̰𝐚̰𝐯̰𝐞̰ 𝐦̰𝐚̰𝐝̰𝐞̰ 𝐢̰𝐭̰ 𝐭̰𝐨̰ 𝐇̰𝐞̰𝐚̰𝐯̰𝐞̰𝐧̰ ❓

  • @PeterChirwa-vy1gc
    @PeterChirwa-vy1gc 3 місяці тому

    Why don't you expose those witches please

  • @ChristinaMasache
    @ChristinaMasache 3 місяці тому

    Mukumveka

  • @ReginaMangwiza
    @ReginaMangwiza 3 місяці тому +8

    Ulendo wina mudzakambeko mwachangu mukuchedwa poyankhula zikomo😊

  • @steinmuhuwa
    @steinmuhuwa 3 місяці тому

    Mukumveka

  • @BlessingsMwale-k4s
    @BlessingsMwale-k4s 3 місяці тому +10

    The good thing the wicked will not live osalangika..
    Mfiti zo ziona..
    Koditu kunali Hamani anakumbira dzenje Mordecai..
    Zinatha bwanji?
    I have never doubted my God..
    Mfiti nayo idzafanso ngati galu..
    Rahab anafa bwanji?
    Nanga Jezebel?
    Ma misa ose aja God won't keep quiet...

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 місяці тому +8

    Zowinazo aii man of God sitikufuna ifee abela mavoti kuti awine bcs ife ovotafe sitikufuna aii

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 2 місяці тому +1

    Koma this time around,tapemphera pemphelolo tikumva kuwawa Za imfa ya Chilima ndi anthu enawo,plz plz

  • @KelvinBandah-h9p
    @KelvinBandah-h9p 3 місяці тому +4

    Kodi MULUNGU akungoyang'ana za a Chakwera okha nanga a Malawi ambiri akuvutikawa bwanji Mulungu sakùwaona. A Chakwera amphinja a Malawi ambiri.

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley 2 місяці тому

      Ndipo ndikudavwatu mwina mulungu wake wina koma yemweyi aaa maloto a chumba

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley 2 місяці тому

      auzen man of God asamapange zibwana

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley 2 місяці тому

      zandisangalasa mwawauza chilungamo aziziwa mulungu choyamba

    • @MikeMwale-bw1xw
      @MikeMwale-bw1xw 2 місяці тому

      Ndipo aumbwita utsogoleri sadzaunaso,chifukwa ngakhale zitati sakutengapo gawo pa Nkhanza ndi uchigawengawu koma ndekuti pa utsogoleri sakukwana Ali week kwambiri.

  • @MackdBanda
    @MackdBanda 3 місяці тому +6

    Chakwera sangawineso muthu oipa amene uja alibe uzimu

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому +1

    Ndye fertilizer tizizagura 200,000 asaaa tatopa naye ndye analipanga kale affect ameneyu

  • @chimwendogift9676
    @chimwendogift9676 3 місяці тому +3

    Nkaka muja ankayankhulira pa times muja akuti ndale sizomwe timaona nsanasanazi

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela 2 місяці тому +1

    Ufumu wawo wayezedwa ndipo zawonesa kuti walephera anthu a MCP

  • @FellisterChinthona-uv4rg
    @FellisterChinthona-uv4rg 2 місяці тому +1

    Mulungu. Simunthu.mulungu atithandize..koma chakwela sitikunfunaso.ayi

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому +1

    Eya tikupempha mulungu tikufuna amve kulira kwathu oipayo aziwike tisanavote plz ambuye

  • @peterphiri7119
    @peterphiri7119 3 місяці тому +6

    Prophet, I love your ministry and the passion you have for this nation.
    Before chakwera became president you sought an audience with him and he became president. I wanted to plead with you to seek an audience with him again this time and tell him the condition that will assist him become president in 2025. Thank and continue doing God's work. I pray for you and the president as well.

    • @limbikanil.i.mmtewa7595
      @limbikanil.i.mmtewa7595 3 місяці тому

      Never again...forget that people are angry dont be deceived

    • @PaulMvuma
      @PaulMvuma 3 місяці тому

      I know chakwera is innocent in this matter

    • @limbikanil.i.mmtewa7595
      @limbikanil.i.mmtewa7595 3 місяці тому +2

      @@PaulMvuma he might be innocent yes but he is to blame... he knows all the affairs run on the ground

    • @moureenish
      @moureenish 3 місяці тому

  • @williamalisson266
    @williamalisson266 3 місяці тому +6

    Tikufuna za Chilima osati za enawo

  • @AaronMsewezi
    @AaronMsewezi 3 місяці тому +2

    Your message it is reminding me of last week, when I've been thinking about this tragedy of plane crach , there are some clips from different platforms, showing the speech made by another minister, and it has been bothering me so much , because what he said it was not good at all , today if people they point at him as one of the witches who have made the plane crach he must not be angry, the speech itself shows that they had something against the VP, that is why we have to be very careful how we speak, words have got power to create, the tongue has got a power of life and death, so God will expose these people , they are so wicked

  • @AgnessKavalo
    @AgnessKavalo 3 місяці тому +2

    😂😂😂😂 koma abusa awawa koma za yesu izizi or maganizo chabe komatu musatengepo msambi pa imfa ya chilima mwixx

  • @KondwaniMbalu
    @KondwaniMbalu 3 місяці тому +6

    Maganizo amenewo ndi aiweyo osati Jehovah atate Mulungu wamphamvu zonse, zonama zakozo ayi

    • @IgnatiousFote
      @IgnatiousFote 3 місяці тому +1

      prophet abodza awa asakunamizeni

    • @HamanjaManyela
      @HamanjaManyela 2 місяці тому

      Waboza ndiweyo kod you think mu win agalu inu

  • @alickmathias2097
    @alickmathias2097 3 місяці тому +3

    Prophet no one is after you people are evil don't believe them God could show you that

  • @florencegondwe2607
    @florencegondwe2607 3 місяці тому +2

    I understand you said it's all about ufiti wa mutonse alliance...And chakwera is also a president of tonse alliance..it means he is with them too...Coz he is also in tonse alliance

  • @DilaGerald
    @DilaGerald 3 місяці тому +9

    Thank you very much man of God, let God expose the Se m'fitizi, plz let it happen, we thank you very much man of God

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому +1

    Tasatadi ndithu akanamvera bwenzi tili naye

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому +1

    Koma asazawinsenso eeishh boma latipweteka ili

  • @martinsalimo3209
    @martinsalimo3209 3 місяці тому +5

    Go deeper man of God

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому +1

    Koma ufunu uwu utheretu basi sitikuufuna

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 3 місяці тому +1

    Alliance yathapo apa

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni1621 3 місяці тому +2

    Ndipo muzilankhuladi mu chichewa man of God. Mulungu ndiye aziwa zose tizipemphera zolimba

  • @justinmendere
    @justinmendere 3 місяці тому +1

    So ngati inu munthu wa mulungu kodi sizikanatheka kupemphera kuti ufiti umenewo upangike cancel

  • @MorganLucious-ny8nl
    @MorganLucious-ny8nl 3 місяці тому +1

    Dakhala dikukusatirani bwino kwambirii dipo mumayankhula zoona zokha zokha

  • @limbikanil.i.mmtewa7595
    @limbikanil.i.mmtewa7595 3 місяці тому +3

    i agree with you man of God, anthuwa ndi afiti opemphera

  • @clementmahoka6287
    @clementmahoka6287 3 місяці тому

    But Man of God why do you always put conditions when predicting future for someone? don't make us think kuti mukusaka pozathawira ngati sizichitika as predicted? Just tell us the next president bas. Chala cha Mulungu chikaloza chimakhala chaloza bas. God can never be conditioned. Mulungu akuziwa kale next president, so as a man of God just tell us kuti next president ndiwakuti bas

  • @Wisdomjames95Mughogho
    @Wisdomjames95Mughogho 3 місяці тому +3

    Tiuzen zeni zeni tatopa kumvesera Ali chete chete

  • @Bonaventure1965
    @Bonaventure1965 2 місяці тому

    Malawians are the wisest people the whole world. They know everything on earth. They elect the best people. Soon after election, they desparage and parade the very leader they elect as the worst leader they have elected. One wonders what these wisest Malawian people want. Therefore one would comfortably say Malawians don't know what, who and how they really want their leaders to be.
    A good elected leader will bring into the country the best development. Malawians will close their eyes to those and never talk or even mention about those good things. Rather, they will say he is the worst leader, making one wonder even more whether Malawians know what is good and bad. Malawians will praise the worst leader who has done totally nothing for the country as the best leader.
    Where to Malawians? Malawians anthu omvetsa chisoni kwambiri.

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 3 місяці тому +1

    Aneneli wonyenga 😂😂😂..... Awadi ndi masiku wosiliza kape iwe

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 3 місяці тому +1

    Baibulo linanena kuti kuzabwela aneneli onyenga mozi mwaiwo ndiwe ndiwe onyenga

  • @francisntonya171
    @francisntonya171 3 місяці тому +1

    Bwanj mupemphere kut dpp ilowenso m'boma??

  • @alickmathias2097
    @alickmathias2097 3 місяці тому +2

    Prophet help clean the record of president please man of God

  • @sibongilekolisi4144
    @sibongilekolisi4144 3 місяці тому +1

    Tell us the future of Dr Michael Biziwick usi

  • @patrickkishombe3755
    @patrickkishombe3755 3 місяці тому

    uyu ndiwabodza uyu, there is nothing true from him ,i do'nt judge but on this one man there is nothing.

  • @HarryChindiwo
    @HarryChindiwo 3 місяці тому +2

    Iweyo zimene ukunenazo sizochokela kwa mulungu...... Mwayamba akunamiza wanthu.... Iwe ndiye sakumanga bwanji

    • @BexSaidi-so8lw
      @BexSaidi-so8lw 3 місяці тому

      Go deeper man of God..let the spirit of God continue to use you..ndi kuona kucedwa kut Mulungu aulule za ufuti athakatiwa

  • @nancynyirenda6774
    @nancynyirenda6774 2 місяці тому

    Aliyese matsiku ano ndi senior prophet 😅Nanga a Tsalanje aja mumati azawina u president bwanji?

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 місяці тому

    ZOTI CHAKWERA ANGAWINENSO INEYO NDIKUKUTSITSA OLO ULI PROPHET NDI BODZA LENI LENI UKUYANKHULAZO

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому

    Ufumu unachotsedwa kale tingodikira 2025 basi mwalamulo

  • @emmanuelsulani3959
    @emmanuelsulani3959 Місяць тому

    Nanga mtsogoleriyu mwamuuza zoti asamachitezi directly?

  • @charlesmbewe4001
    @charlesmbewe4001 2 місяці тому

    Kkkkkkk you make me laugh mr prophet kupanda mgwiridzano uja maka maka malemu chilima akanaona?

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому

    Fake profit chakwera sikumufuna we are tired with nonse goverment

  • @MadalitsoChinkhonyo
    @MadalitsoChinkhonyo 2 місяці тому

    Iwe udzakavote ndiweyo ndizako ukukambazazo imeneyo sikhani wathawatha basi

  • @SamuelLiphava-p4u
    @SamuelLiphava-p4u 3 місяці тому +1

    Chakwera must go,by any way

  • @WilliamMasula-cb1mg
    @WilliamMasula-cb1mg 3 місяці тому +1

    Mukuchulutsa zoyankhulatu mtsogoleri kkkkk

  • @KennyThindwa
    @KennyThindwa 2 місяці тому

    Dzina la Ambuye ndi loyera a ndale eish ndi ochepa okonda choonadi.

  • @ChiluBengoh-js2ky
    @ChiluBengoh-js2ky Місяць тому

    Kkkkkk za formal communication ndi kamajeketeyo?

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 2 місяці тому

    Abwanna shangu please it's because of times

  • @feranjifeza6802
    @feranjifeza6802 3 місяці тому

    Mukutathauza kuti modzi wa athu omwe anakwera nawo ndege anali mfiti?

  • @TambulaniPNyirenda
    @TambulaniPNyirenda 3 місяці тому +1

    Koma mmmmm zosayenda tapwekeka kwambiri ife SKC ndimamukonda kwambiri

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e 3 місяці тому +1

    You are now really talking man of God I am with you

  • @EvansNaphazi
    @EvansNaphazi 3 місяці тому +1

    Zozawinazo nde ukunama mmene ziko likuvutikilamu zikabwela apa mkumat azalowenso aaaaaah akudyesa banz

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому

    Pena mumaduka koma apa mukumveka koma munaduka kwama minutes angopo apa tikumva

  • @TamalaSoko-vg5wq
    @TamalaSoko-vg5wq 3 місяці тому +1

    Penatu zikundivekeradi bwino mukunena zoona zimuwawo use ndi mtendele ndipo zozi zwa zichitike pa ifa iyi😭😭😭😭😭

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 2 місяці тому

    Pa chakwerapo musathawepo no fear naye ndi mfiti

  • @jollychadzuka
    @jollychadzuka 3 місяці тому

    Do you mean you are a prophet or a fundraiser?

  • @leviefeston7626
    @leviefeston7626 3 місяці тому +1

    Chakwela sitikumufunaso achoke amene

  • @gloriaKasambala
    @gloriaKasambala 3 місяці тому +1

    God bless you
    I like your spiritual maturity
    Mwalankhula mwa nzeru kwabasi

  • @GeorgeManda-dj1zc
    @GeorgeManda-dj1zc 2 місяці тому

    Kodi a president athuwa samadziwapo zochitikazo

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu 2 місяці тому

    Amen and amen

  • @mrgrace4161
    @mrgrace4161 3 місяці тому +1

    Iweo ase musiye mulungu apange mwachifunilo cha ana ake and mulungu amanva kulila kwa ana ake

  • @AliceBotha-o4h
    @AliceBotha-o4h 2 місяці тому

    Nanga mfitizo sizitiphera mtsogoleri wathu

  • @ayisekiahamaduahamadu
    @ayisekiahamaduahamadu 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Busa oname wakupasa ndalama singati shakwela

  • @NeneKimu
    @NeneKimu 3 місяці тому +1

    Amwene tikudikila mutiwuze za ifa ya chilima osati zanuzo

  • @EmilyBanjachikwatula
    @EmilyBanjachikwatula 3 місяці тому +1

    Ndipo man of god anthu amenewa awonekele pa mbalambanda amudziwe mulungu kuti ndi mwini zonse

  • @FranklimNowa
    @FranklimNowa 3 місяці тому +1

    Abwana tipemphe kuti muzingopita pa uthenga wanu womwe mwabweresa osatenga nthawi ndima pause ambiri pofuna kutisungira data yathu.

    • @Sabina-hw4js
      @Sabina-hw4js 2 місяці тому

      Amen.

    • @Sabina-hw4js
      @Sabina-hw4js 2 місяці тому

      What about anthu awo amene akusaka saka ma activist?

    • @Sabina-hw4js
      @Sabina-hw4js 2 місяці тому

      Nanga chilungamo chili pati man of God

  • @WilsonBandawe-uu9jo
    @WilsonBandawe-uu9jo 3 місяці тому +1

    Kodi a pre wo amatha kupanga chiganizo paokha

  • @NicholusKampezeni
    @NicholusKampezeni 3 місяці тому

    Nyimbo ya ndani iyi plz

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 2 місяці тому

    dzikuveka kwambiri a prophet.

  • @giftmingo9293
    @giftmingo9293 3 місяці тому

    All in all Mulungu azakhalabe Mulungu. Ngati Chakwera anapha SKC Mulungu alipo ndipo tsiku ndi limodzi ukulu wake uzaoneka. Koma tsoka ngati tikungotengera chidani pandale nkufuna kuipitsa dzina la Dr Chakwera, Mulungu tsiku lina adzaonetsa mkwiyo wake nkupukuta misonzi yosalakwa ya Dr LMC. Mulungu sanagone.

  • @HarrentBanda
    @HarrentBanda 2 місяці тому

    Palibe za u polofeti apa pezani zochita baba

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 3 місяці тому +1

    Prophet ometa mmbali serious? Aaaa

  • @Crossley-e6g
    @Crossley-e6g 2 місяці тому

    ADJIBA

  • @ayisekiahamaduahamadu
    @ayisekiahamaduahamadu 2 місяці тому

    Iwe wabosa gona palibe ukunena wabosa iwe

  • @anniezovu2620
    @anniezovu2620 2 місяці тому

    Tukumva

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 3 місяці тому

    Mubweranso liti timve zambili