Man of God,, a chakwera akonzekela kupha nantindi Wina a nthu,to Eliminate them from contesting,, the list is known tell me which God is instructing him ??
People of God palibe chifukwa chotukwanira mtumiki wa Mulungu Ngsti akunama Mulungu yemweyo adziwa chochita naye koma ngati mzoona munganiza kuti Mulungu angatani nanu? Mirriam ndi Aaron atatsutsana nd Moses chinawagwera mnchiani Tisakhale ife mmalo a Mulungu Prophet work in God's office If he is not of God adzadziwika pangapite nthawi bwanjiiii Mfunseni Mulungu kodi a prophet athuwa mwawatumadi ndinu Mulungu? Stay blessed i God bless 🇲🇼
Dr Michael Usi. not Manganya. Dont be dull. There is no one called Manganya appointed Vice President. Manganya is a character in acting. Please. Learn to differentiate.
This is man is a prophet but he is orso been used anthufenso ndi anthu timakhara ndi zofoowoka zathu Akurankhura zina ndi nzeru za umunthu but he is a prophet
Nde macheza anu amulungu wo amakhala ocheza za ndale zokhazokha basi pena ndi zoseketsa bwanji zovuta zonse zikuchitika m'malawi kuli ma Freddy kunja zilala bwanji osalosera zimenezo ndi njira zoti zipeweke koma kumangosera za ndale zabodza izi
I am very disappointed in you,i have been following you all along,koma I have now realized that I have been following a very wrong person,God almighty should forgive you.
Lalikirani za Uthenga wa bwino kuti anthu akalowe kumwamba plz Nthawi zonse pulezidenti Aa koma kalalikire anthu atembenuke mtima amdziwe Yesu Nanga izi zikalowetsa anthu ku mwamba? Mwaxhedza ndi Mulungu inuyo aaa Mulungu amadana ndi bozaa
😂😂😂 Kutherana data abusa yimani pa mawu mulungu sioseweresatu mulungu sakukondwa mmene ana ake akuvutukira mziko la Malawi plz lalikirani chabe unthenga wa mulungu musalowe ku ndale musocheresa nazo uzimu ukuchokerani sitikuti mulibe yesu iyay mwina mulinaye koma gwirisani bwino ntchito uzimu wanu, anthu tikuvutika basi kukavoteraso ndithu ife tizisintha kaya every chisankho mpana tsiku lina wabwino azapezeke mulungu tu akukuonani apo
Kodi aneneli onyenga aja mmozi wake ndiiwe? Mulungu wake ukumtumikilayo ndi mulungu wa anthu akupha osati mulungu ndikumziwa ineyi ayi Koma muyaluka achimwene
Akuluakulu wina aliyense akhoza kulankhula ndimulungu ngakhale muli achichepele, koma ndukuzani kuti ntundu wa malawi uli okwiya kwambiri ngakhale mwana wazaka 10 panopa saliokondwa nda president kulibwanji inu akuluakulu odziwa chabwino ndichoipa? Posabera mavoti akuluwa sangawine ndukuzani am in there in Malawi but I can see how people crying tilindi nthawi yochepa kwambiri kuti president angathe kuwakhazikitsa ntima pansi amalawi because wapanga big mistake mumnthawi yothaitha.
Kuvota MWA Chilungamo a Chakwera sangawine never,, Koma Ali pa ma plan oti adzayendetse zitsankho MWA chinyengo,, ndipo ayamba kale kuchepesa chiwerengero cha anthu ozavota powamana ma ID makamaka anthu ochokera Ku mmwela ku mpoto ndi madela ena amene iwowo akudziwa Kuti palibe angawavotere,tell me this plan is also from your god
As President Chakwera has fulfilled the God set conditions, he will be caught between a hard surface and a rock. His opposing teams will try hard to provoke him so that he can breach or disobey God. The other thing is that he will have a tough time to raise people's trust in him
Koma zili ku Malawi, Ambuye imvani kulira kwa ana anu a Malawi ndipo tikudziwa kut palibe angabwere ndikusithilatu zinthu. Koma tichotsereni uneneri uwu usakhale owona cz dziko la Malawi lafika poola ndipo zikuonetselatu kut mwa awa utsogolere mulibe
Kuselelerako kosekelera yekha? Mulungu wa Israel amene adaononga pharaoh pa madzi nachitila chifundo ana a Israel atichitila ndipo tipemphera ngati wayankhula ali yehova yo amvaso kulira kwathu ngati tinachimwa atikhululukira
Ndidayamba kale kale kumutsatira a prophet wa . God uses Him to the fullest.He is powerful
Your Prophecies always come to pass. I've been following you, and you never miss.
Ineyo since 2014 ndidakhala ndikumutsatira , Zambiri zimachitika ndthu
@@justinchabwera5380 He's always on point
Amwsne , amwene, mavoti atati ayende mwachilingamo patati pasakhale zacinyengo ndimmene zilili zinthumu MCP singawine ayi
Prophet honest speaking forget about Chakwera to rule again this country come 2025,mark my words zinthu sizilibwino
You said inorder for Chakwera to rule he had to meet certain conditions then God will have mercy on him so what sin has he offended
Man of God,, a chakwera akonzekela kupha nantindi Wina a nthu,to Eliminate them from contesting,, the list is known tell me which God is instructing him ??
Zikuchedwesa izi ase zandalezi bola kutumikila mulungu ndi njila yabwino
I always follow you man of God
machende ako pamozi ndi chakwerawakoyo umuwuze zoti ndinamuchindila mkazi wake chakwerayo
Kkkkkkk kumuthila madzi Monica mumakwana bamboo a Nick
Koma guys pa tsiku la Ambuye , tsiku lomaliza anthu mudzakhumudwa kwambiri. Lapani please osamaseweretsa Mulungu
People of God palibe chifukwa chotukwanira mtumiki wa Mulungu
Ngsti akunama Mulungu yemweyo adziwa chochita naye koma ngati mzoona munganiza kuti Mulungu angatani nanu?
Mirriam ndi Aaron atatsutsana nd Moses chinawagwera mnchiani
Tisakhale ife mmalo a Mulungu
Prophet work in God's office
If he is not of God adzadziwika pangapite nthawi bwanjiiii
Mfunseni Mulungu kodi a prophet athuwa mwawatumadi ndinu Mulungu?
Stay blessed i God bless 🇲🇼
Prophet never work in the office of God, otherwise Not Yahweh
Dr Michael Usi. not Manganya. Dont be dull. There is no one called Manganya appointed Vice President. Manganya is a character in acting. Please. Learn to differentiate.
God bless chakwera and malawi
This is man is a prophet but he is orso been used anthufenso ndi anthu timakhara ndi zofoowoka zathu
Akurankhura zina ndi nzeru za umunthu but he is a prophet
Km ndiwe obowa 1hr tikudikira osangoyankhula bwanji? Kmanso Chakwera nzosathe kuwina, za ziiiii
Next time mudzapange record conversation with God 😢
Mneneri wa MULUNGU sakhala odulira mutu uzikatumikila makolo ako zim
Nde macheza anu amulungu wo amakhala ocheza za ndale zokhazokha basi pena ndi zoseketsa bwanji zovuta zonse zikuchitika m'malawi kuli ma Freddy kunja zilala bwanji osalosera zimenezo ndi njira zoti zipeweke koma kumangosera za ndale zabodza izi
Unati chilima azakhara pulezideti apano wasintha maganizo, tigwire chiti
My Question as well
Chakwera yemweyo
What can God do if multitudes of Malawians are crying because of the current leadership crisis? Will he force Dr Chakwera on people?
I am very disappointed in you,i have been following you all along,koma I have now realized that I have been following a very wrong person,God almighty should forgive you.
Kkk koma apa ndie uyaluka
Koma guys Kodi baibulo Mo ulimo ulaliki umenewoo Chikilisitu mwachisandusa kukhala pingo wa business komatu asamachula zina la mlungu pashabe muopeni mlungu musamupepuse pachabe ....koma mlungu really angayakhule ndiiweyo khani zimenezo koma ya kumapeto kwaziko uku kuli xithu eee😮😮😮😮😮
Great prophecy
Guys uyuyu simupulofiti akuziwana ndi chakwera chisiru cha munthu
Lalikirani za Uthenga wa bwino kuti anthu akalowe kumwamba plz
Nthawi zonse pulezidenti
Aa koma kalalikire anthu atembenuke mtima amdziwe Yesu
Nanga izi zikalowetsa anthu ku mwamba?
Mwaxhedza ndi Mulungu inuyo aaa Mulungu amadana ndi bozaa
How should I pray teach me prophet
Forsake
Ambuye mundithandize ine chifukwa maganizo anga sali maganizo anu komanso njira zanu siziri njira zanu. Pakuti monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, momwemo njira zanga siziri zazitali kupambana njira zanu, ndi maganizo anga kupambana maganizo anu, /Yesaya 55 v 8- 9
Ambuye mundithandize ine chifukwa maganizo anga sali maganizo anu komanso njira zanga siziri njira zanu. Pakuti monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, momwemo njira zanga siziri zazitari kupambana njira zanu, ndi maganizo anga sali opambana maganizo anu( yesaya 55:8 -9).
Hahaha!! unama mphwanga akugayra zingat kd? Prophet wodztamandra uyu akut ka 4n kanga ka ma million kķkķ.
Aise ndiwe chitsilu usamangwilise tchito dzina lamulungu god panish you be careful mulungu siosewela naye ameneaja ndintunda wina
Kkkkk sorry by starting my comment with a laughter style
Mumasewera ndi Mulungu bwana Prophet?
Kkkkkkkkkkkkkk
A Chakwera akowo akudyetsa ma banzi angati za usatana etiiii
🎉Achakwera akuonesa ulamuliro wankanza akabwereraso tizavitika zed
Unwino ndiwakut zokhulupilira azibusa ma prophet tinaleka amalawi coz of chakwera wakoyo nde usamatiuzenso zamkutu kumakokomeza yet akutizunza munthu ameneyu
We are waiting for it to be fulfilled
😅😅😅 koma macheza anu ndi Mulungu ngoseketsa, mpakaso mumasewerera pamodzi
😅😅
Never think about that appeasement we are also people of God. Kodi mulungu Angalore kuti anthu ake azakhala akulira mpaka liti
Pena pake amazandionekela ngat wa sewelo bwanjii
Zopusa basiiiii prophet waboza uyuuu isaaaaa
God help Malawians zinthu sizili bwino kuzayimaso mmm Ambuye chitanipo kanthu
Kucheza ndi Mulungu??? 😢. Kumbukilani Mneneri Elijah ndi Ahab pa phiri la Caramel.
Chakwela chake kulibe 2025 and watikwana kwambiri,zosekelererazo asekeketu panopa next yr nomore kuseka bt kuzakhala kukirano
Ameneyo ndi Mlungu wakodi otsati waliese olenga zonse ,mlungu ofumuka chonchi
Banzi limene akupasa chakweraro umenyedwa naro uli pakautumiki kakoko, shatap prophet wakuba iwe, palibe munthu omuona mulungu maso ndi maso, ndiye iwe ndindan
Anthu azazuzuke Ambuye tikomekebi mtima asawineso
😂😂😂😂 Malawi is sweetest country❤
Iwe ndikape adah aaa u prophet wake uti zasataniki chan kkk chakwera akuluza adah
Spirite of pride wil make u poor forever
Nenani uthengawo zomatiuza za 4n or studio zilibe ntchito iyaaaaa
Ati phon yamamilion koma dzikooli likutha ili
You once said Patricia Kaliati will be the vise president😂😂😂😂😂
Akupasa ndalama Kodi ukungoti kukambilana ndi Mulungu ungayankhulane ndi Mulungu wayamba fodya amkayankhulana ndi Mulungu anali mose mulibe mphatso
😂😂😂 Kutherana data abusa yimani pa mawu mulungu sioseweresatu mulungu sakukondwa mmene ana ake akuvutukira mziko la Malawi plz lalikirani chabe unthenga wa mulungu musalowe ku ndale musocheresa nazo uzimu ukuchokerani sitikuti mulibe yesu iyay mwina mulinaye koma gwirisani bwino ntchito uzimu wanu, anthu tikuvutika basi kukavoteraso ndithu ife tizisintha kaya every chisankho mpana tsiku lina wabwino azapezeke mulungu tu akukuonani apo
Chakwera 2030
Man of God ndimamvesela km achakwelawo asiyad kumanga wanthu?
It's too late koma
Kodi aneneli onyenga aja mmozi wake ndiiwe?
Mulungu wake ukumtumikilayo ndi mulungu wa anthu akupha osati mulungu ndikumziwa ineyi ayi
Koma muyaluka achimwene
What if akazalephela?
2- Mapemphelo unenawo ndioti amachitika every year, so Chakwela wapangitsa liti mapemphero!?????
tiyeni tidikire 2025 election osati mutinamize chifukwa aliyense adzawineyo adzatilamula bas wina afune asafune
Akuluakulu wina aliyense akhoza kulankhula ndimulungu ngakhale muli achichepele, koma ndukuzani kuti ntundu wa malawi uli okwiya kwambiri ngakhale mwana wazaka 10 panopa saliokondwa nda president kulibwanji inu akuluakulu odziwa chabwino ndichoipa? Posabera mavoti akuluwa sangawine ndukuzani am in there in Malawi but I can see how people crying tilindi nthawi yochepa kwambiri kuti president angathe kuwakhazikitsa ntima pansi amalawi because wapanga big mistake mumnthawi yothaitha.
Unalandira ndalama zingati iwe kkkkk kuchita kuwonekeratu kuti Wadya ndalama kkkkkk Wa bodza iwe M, Busa Wa bodza iwe aaah wanama
Mwagwanayo, akudyesani pangono ndalama zakubazi..😮 kucheza ndi Mr Chakwera not a man of above, trust me.
Mulungu olenga kumwamba ndithu adzionetsele yekha pankhani imenei cos Mulungu sagogo athu oti tizimuseweletsa chonchi ndithu katsala kanthawi pang'ono kut tidzapange regrate Mulungu wamphamvu zonse odziwa kutsegula maso anthu atitsegule arhuwa ndithu nthawi yatha.
Muthu wakunyanja uzipanga zako umamuziwa mulungu iwe mbuzi zobwelela kumalonda n
Hahaha!! unama mphwanga akugayra zingat kd?
Koma nanga poti anthu ovota onse mdziko lamalawi lino adakali okwiya ndiye nzotheka president olamulayu kuwina opanda voti? Tandiuzani aprophet mumdzina layesu mosanyoza ndikufusa mowopa mulungu.
Mbuziyo singamvere coz anamwa kale magazi😂
man of God ndakhala ndikulondola za ulosi wanu ayi ndimkhala ndi chinkhululupiliro man of God.
Chadwell wa chani mene dziko lavutikilamo angoba bwanji osanena kuti ndiokupha za ziiii
Unayamba Bodza wadya ndalama kapena bwinotu mutha ngati agalatiya ndi nzako chakwerayo zi tsiru za anthu.
i hope ndiwe wa ndale osati mutumiki wamulungu chitsiluuiweeee usamatiputsitsepo shupit
Hahaha!! unama mphwanga akugayra zingat kd? Prophet wodztamandra uyu akut ka 4n kanga ka ma million kķkķ. 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mulungu wake ndye mgwabodza
Kuvota MWA Chilungamo a Chakwera sangawine never,, Koma Ali pa ma plan oti adzayendetse zitsankho MWA chinyengo,, ndipo ayamba kale kuchepesa chiwerengero cha anthu ozavota powamana ma ID makamaka anthu ochokera Ku mmwela ku mpoto ndi madela ena amene iwowo akudziwa Kuti palibe angawavotere,tell me this plan is also from your god
As President Chakwera has fulfilled the God set conditions, he will be caught between a hard surface and a rock. His opposing teams will try hard to provoke him so that he can breach or disobey God.
The other thing is that he will have a tough time to raise people's trust in him
Mwadya zingati man of God 😂😂
Koma zili ku Malawi, Ambuye imvani kulira kwa ana anu a Malawi ndipo tikudziwa kut palibe angabwere ndikusithilatu zinthu. Koma tichotsereni uneneri uwu usakhale owona cz dziko la Malawi lafika poola ndipo zikuonetselatu kut mwa awa utsogolere mulibe
Kuselelerako kosekelera yekha? Mulungu wa Israel amene adaononga pharaoh pa madzi nachitila chifundo ana a Israel atichitila ndipo tipemphera ngati wayankhula ali yehova yo amvaso kulira kwathu ngati tinachimwa atikhululukira
The 3 conditions are pure logic..
Speak Man of God malawians are crying.
Iwe Mbudzi sukudziwa chomwe ukuchita aneneri onyenga Inu akunsi kwa Nyanja akupatsa ndlama iwe galu
Onyenga asatana awa apansi panyanja okhaokha akudziwana ndani angavotere chikhesa magazi
Iwe ndiwamisara eti anakupasa chani garu nzakoyo
Iweyo si mtumiki wamulungu koma umatumikira satana ndikuudze izi mulungu sangalole kt anthu ake adzingolira chifukwa ca mbusa uyu cakwera yemwe sakudziwa kuyendetsa. Dziko ndiyeno adzaonetsa ukulu wake tiyeni amalawi tidzipephera
Iwe mneneri iwe funso ndiroti akaberanso kapena mukawasankhanso ndinuyo ma prophet chifukwa ifee tisaname mu la Yesu Christ sitikuwafuna oloo pang'ono ndipo ambuye ngati sakumva kuli kwa anthu Chakwera akuyener kuwina komanso a prophet musamakonde ndalama koma kufunira zabwino anthu amdziko lanu osati kumanama momwe mukuchitiramu
Amen
that 'ka phone ka tima million tingapo' was it necessar...?
Mkwabwino kutumikila Mulungu,ndipo usatchule dzina lamulungu pachabe
Aaaaaa Zowona zimenezi koma? Mulungu wake uti? Mulungu sangalore kuti anthu adzingodzunzika anthu ambiri sakumufuna chakwera, nde akadzawinanso sadzapitiliza zomwe zikuchitikazi?
So zizakhala bwanji kt chaka Chino chisanathe basi iwe ndi chakwelayo mwamwalira zizakhala bwanji ??
Ndikuona ngati mutamanena kuti m'mene ndimapemphera osakhala kunena kuti m'mene ndimacheza ndi Mulungu,
We just lost a true statesman vp,, people are not happy wit Chakwela leaders. If you're true to your calling advice to step aside
Koma a prophet Mpaka Ka fon kanga Ka ti ma million tingapo kkkkk mmmm koma yeeeeh
Liyabunya ndiwe wa fake unanena kt chilima 2025 awina masankho chosecho pano kulibe aaaaa liyabunya,komaso Kodi nowa anali chidakwa kapena mtumiki?
Ukungofuna ndlama from chakwera iwe
May the Lord forgive you,If Jesus came to join politics ndiye kuti ntchito yake sakadakwanitsa!!
Komaso apapa pa line yakeyi akumusatile olo ten sakukwana onse akumususa sono zawinila kuti poti ovota ndife
Ndiye mwati kusewera ndi Mulungu? Okay!!!!
Uchisiru kuwubweresa poyela pasana Pako ngati ndimisala wasalaku uvula ndiwe galu kwabasi
Musanamizile Mulungu wa yakobo kuti akuuzani izi ayi. Koma ndi milungu ya pansi pa madzi
Mmmmm nde pano chasintha ndi chani? Palibe po chikuyenda apa, bolanonso enawo
Nkhani ndi ndalama apa,only God knows.
Never,never never Gos cannot allow chakwera kuzuza anthu again