Kkkkk ili siboma koma chilango cha amalawi AAAA KOMA NDIMAKAKAMILABE KUTI 2025 MUDZIPILIDZA KUTIDZUDZA AMALAWI iiiii KOMA MULUNGU AMVE KULILA KWA AMALAWI AMBILI NDINTHU TIKUFA NDI MCP IYI
MCP why Why,?...Foundation ya economy yakuvutani vomerezani ..People they trust you kuti mwina Boma muyendetsa bwino Corruption yanyanya... ...Signal of Economy is sinking little by little. Bagamoyo 🤣 🤣 🤣
Boma lawakanika awa inu
We don't have a president in MALAWI 🇲🇼...
Kodi kumakawi kuli boma lolamulila ?
Kapena ndifunsechonchi ,
Kodi kumakawiko kuli president wamkazi kapena wamwamuna ? Kapena president wamwalila ?
She is right ✅️ saziwa kuyendesa mulimose
Kod anthuwa cholinga chomwe tinawayikira pampando akuchiziwa ?????????
Kwacha imagwa madela onse mmalawi muno kupatula kulilongwe kwa achewa 😂
Kkkkkkkkkk
Iwe ndigalu kwambiri
President wamalawi anamwalira
,😂😂😂😂ndipo onafa😂
Akuchita manyazi kuti azinena zawakanika chimene akudziwa iwo ndi kukwera ndege kumapita ku mayiko akunja kumakakwera njinga uchitsiru weni-weni
Ndizoona azitiuza kumene chifukwa zikumatibalalitsa zedi
That's quite true
Kom akutilakwira anthuwa mmmm
Musamat pempho ay mudzingoying'alura bas ineyo sindikudziwa kut anthu awawa mitu yawo imagwira ntchito coz zangofikat potikwana ndisaname
Zilikotu 😂😂😂😂.
Wina akuti Boma ndilomweli 😂😂😂😂😂
Machende ake ameneyo
😂😂😂😂😂😂Wazimvera yekha aliko@@HamanjaManyela
😂😂😂😂😂😂
That's hectic indeed my dear, this government is useless, panopa akuyendetsa dziko ngati kubanja kwawo so alibe nthawi youza anthu kuti zinthu zili chomchi pakali pano,
Koma MCP guys mmmmmm
Poor leader😢😢
Kale ife sitinkadziwa kuti kwacha imagwa koma pano mwezi ulionse akuti kwacha yagwa Eeee koma MCP ayi zikomo ndi Chikangawa
Boma linali kale mama😅
Bomalinalikale nthawiimeneyo osatilelo Masanjeenieni
Ukunena zoona ccta koma boma ili lavesa ife amalawi kuwawa ndipo amalawi tikuwawopa chami atsogoleri amenewa ife tinawaika pamupando malipiro awo akuchoka kwa ife y akutivutata? Kodi tilibe anthu woti angakwanise kutitsogolera
Ndi mbunzi izi chikangawa
Kwacha pano ndi chizude
Kkkkk ili siboma koma chilango cha amalawi AAAA KOMA NDIMAKAKAMILABE KUTI 2025 MUDZIPILIDZA KUTIDZUDZA AMALAWI iiiii KOMA MULUNGU AMVE KULILA KWA AMALAWI AMBILI NDINTHU TIKUFA NDI MCP IYI
We have a president, but not a leader. Eni ake a dziko la malawi ndi a IMF ndi World Bank.
Owe usataye thawi box 2 idasamukira ku state house
Mbudzi za MCP ndisaname afika pa. 0%
MCP why Why,?...Foundation ya economy yakuvutani vomerezani ..People they trust you kuti mwina Boma muyendetsa bwino Corruption yanyanya... ...Signal of Economy is sinking little by little. Bagamoyo 🤣 🤣 🤣
Koma nditsoka lalikulu kwambiri kuti anthu azingokudandaula tsiku nditsiku ndipo sungapeze mtendere
Tinauzidwa kuti katundu akwera pa 1 September ndi kampani yomwe imandìgulitsa katundu.
Mesa boma limakana kuti kwacha yagwa 😅😅😅😅
Ku central kulibe kwacha kugwatu,,boma ndilomweri akumatero,,,akumva kukoma
Kumalawi kwacha imagwa every 2 weeks mudziwe zimenezi
Chakwera wapa Malawi,
Kumalawi tilibe mtsogoleri panopa mtsogoleri anali uja anapheradalayi alipowa ndiokupha kuba ndikuononga kuteleko awa ndiokwanilitsa malemba malomokhala achakwera pachuma chadziko ndiachagwa,sangathe kuyendetsa dziko awa mmanja mwawo mulimagazi
MCP yanu imeneyo😂😂😂😂😂😂
Anasiya kunena pano kd Boma ili chiletsotu
Kwacha ndilibe nayo mawu
Komabe UTM izingojiyira azao owowo osalamulirako
Why malawi
Kwacha Madela ena imagwa mwezi NDI mwezi koma pano anasiya kunena .
KU Lilongwe siyingagwe kwacha poti anthu ambiri ali ndi makani
Hule iwe azikuuza ngat ndiwe ndani uli ndi mphanvu ziti
Chisilu ndi iweyo galu
Hule nda amako
Masende bhoko
Galu ndi iweyo mbuzi ya minthu
Koma nanu ndedachisilu bwaji buzi yamuthu ndithu