KUSANTHULA QUR'AN NDI BIBLE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 лют 2025

КОМЕНТАРІ • 22

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 8 місяців тому +2

    following from South Africa 🇿🇦 🇲🇼 🤲🤲🤲🙏🙏🙏

  • @trustDaud-gu6ke
    @trustDaud-gu6ke 8 місяців тому

    Great all the way from South Africa I love the program that's me Trouble Dawood

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery 8 місяців тому

    Ine ndaseka 😅😅😅 mishek akuti chithata ndicosadula maro mochiphwasula kkkk

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 8 місяців тому

    Palibe Muthu akapulumuka chifukwa zatchito zake osati kusambitsidwa kapena kupita osavala ayi akupulumuka chifukwa zatchito zimene amapanga kkk😂😂😂😂

  • @AlfredMakuwira
    @AlfredMakuwira 8 місяців тому +2

    A misheck mumakwana azanuwo akut kusambisa maliro ndichiyero kkkkkk km kusadziwa ndikifa komwe

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 8 місяців тому

    Kkkkkk koma inu musaname athu posambitsa malilo kumakhala gulu mesa amasambitsa athu amene auzidwa koma amiseki mumakwana inuyo sakudxiwa kuti malilo amasambitsila chiyani amisheki mwadziwitsa

  • @temwanyirenda7123
    @temwanyirenda7123 8 місяців тому

    Shiekh is full of cloudy personal minded ideas than evidence based. Komaso picking up only one verse without understanding😢
    Big up Mr misheck zikumveka

  • @UthumanMallo
    @UthumanMallo Місяць тому

    Amiseki mukunama ukundikupotosa chimbembezo ingobwelera kushisilamu mukapusile

  • @YusuffuDaud-cs7yu
    @YusuffuDaud-cs7yu 8 місяців тому

    Program imeneyi ili bwino please please ipasen nthawi yambili

  • @adamusaidih8570
    @adamusaidih8570 8 місяців тому

    😂😂😂😂km ndaseka inuso mumawelenga hadifi cholingachanu km

  • @Omwale
    @Omwale 8 місяців тому +1

    NZUNGU: tieni tiapatse zipembedzo, pakhale chisilamu ndi chikhilisitu azitsutsana komaso azikhala busy ndizimenezi ife titenge golide wawo... Oooh zipembedzo sizikukwana, tieni tiwapatse dimokalase, azivota kusankha mtsogoleri wadziko, kwinaku akumenyana ndipo ife tiwalamulire. Mmmmmm dimokalase ili apo, bwanji azikwatilana amuna kapena akazi okha-okha tiitchule ufulu wachibadwidwe (human rights), chiwerengero chao chichepe. Tsopano tionjezere kuteteza chilengedwe (climate change policy), asamalime zakudya zambiri azigula kwaife. ndiponjala ikawavuta tizikagawa chakudya uku tikutenga miyala yamtengo wapatali. Sadzakhala ndimphavu yotiletsa chifukwa adzatigwadira kamba kachakudya.
    RELIGION>>DEMOKALASE>>LGBTQ>>HUMAN RIGHTS>>CLIMATE CHANGE

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 8 місяців тому

    Auzeni pano silamu adatha kkkkk asilamu akale samamwa mowa pano ose akumwa mowa kulibe chisilamu kkkkkkk

  • @trustDaud-gu6ke
    @trustDaud-gu6ke 7 місяців тому

    Mishek ndi wachamba anawona kuti iyeyo munthu akufinyidwa alongosole tamufusani

  • @LondonSimwera
    @LondonSimwera 22 дні тому

    Ipitilile program imeneyi thawi koma

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy 8 місяців тому

    Program imeneyi mumaipatsa nthawi yochepa

  • @AlfredMakuwira
    @AlfredMakuwira 8 місяців тому

    Ndimanva kukoma kwambili ndi program imeneyi abusa mumaitimilira mumasathura moveka bwino kwabas

  • @trustDaud-gu6ke
    @trustDaud-gu6ke 7 місяців тому

    Khristuyo ndiolephela Basi olo atatani palibe chomwe amaziwa

  • @MaulidiAtibu
    @MaulidiAtibu 8 місяців тому

    Achikunja nonse amichek akukuyimililani

  • @MaulidiAtibu
    @MaulidiAtibu 8 місяців тому

    Amichek ndi achikunja ayenela kulongosola zachikunja

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 8 місяців тому

    Kkkkkk koma inu musaname athu posambitsa malilo kumakhala gulu mesa amasambitsa athu amene auzidwa koma amiseki mumakwana inuyo sakudxiwa kuti malilo amasambitsila chiyani amisheki mwadziwitsa

  • @YusuffuDaud-cs7yu
    @YusuffuDaud-cs7yu 8 місяців тому

    Program imeneyi ili bwino please please ipasen nthawi yambili

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 8 місяців тому

    Kkkkkk koma inu musaname athu posambitsa malilo kumakhala gulu mesa amasambitsa athu amene auzidwa koma amiseki mumakwana inuyo sakudxiwa kuti malilo amasambitsila chiyani amisheki mwadziwitsa