2025 Kuvuta nkhondo yi ikhala Jane Ansah vs Annabel Mtalimanja

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 138

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 2 місяці тому +13

    Mwana wa John tembo ndiwa mcp kumene chakwera akufuna kubera mavote koma kuzamvuta simasewera

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 2 місяці тому +7

    APM my vote

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 2 місяці тому +8

    Zisankho it will be just a formality....gule kwao already

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 2 місяці тому +1

      Kkkkk pitala walephera even kupanga hold convention kudzalankhula komaliza chifukwa chokalamba ndie angayendetse dziko

    • @MarthaPhiri-q8m
      @MarthaPhiri-q8m 2 місяці тому

      ​@@damianokachingwe3531aaaaaa inu munali ndi cholinga chofuna kumuchera pobwerera mwagwa nayo achimwene amene uja si mwana anakuwerenga kare kuti kuli mbora nde mumafuna mumuchite mbora ng, ooo

    • @damianokachingwe3531
      @damianokachingwe3531 2 місяці тому

      @@MarthaPhiri-q8m kkkkk km iwe waganiza bwanji ndani angataye nthawi imeneyo pa mdala amene uja,don't force matters please munthu sangalankhule for 2hrs choima ndibodza limenero vomerezan chilengedwe

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 місяці тому +8

    APM uja osazaphwekesa

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 2 місяці тому +7

    *A Boni Kalindo akuphika zotibweletsela asowatu 🎉🎉🎉🎉*

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 місяці тому +2

    MCP idaononga mbiri pa 10 june nde vuto.. and sakubweresa report mpaka pano

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 місяці тому +1

    Apm my vote

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 2 місяці тому

    Mistake yomwe amalawife achita maka aku opposion ndikuvomereza kuti ayese machine pamenepo ndi pomwe game yagonera mcp mphamvu zawo zili pamenepa cz monga kalindo ananena njirayo ndi imodzi yozabela next season

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 місяці тому +3

    Exactly bro

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 2 місяці тому +1

    Ndimmene tikuvela kuwawa amalawi ambirfe singalore chakwera apitilize apapa nde bola tifele chilungamo

    • @blessingsmimu5236
      @blessingsmimu5236 2 місяці тому +1

      😂😂😂sakusamalaso zochosa moyo wamunthu

  • @AdamMntonintshi
    @AdamMntonintshi 2 місяці тому

    Apm my vote 🗳 ❤️

  • @RitaBan-t7c
    @RitaBan-t7c 2 місяці тому

    Adzawina ndi Dpp chifukwa iyenda ndi UDF,ndi Aford,UTM ndiye azaluza bwa

  • @SurprisedDarts-di6fs
    @SurprisedDarts-di6fs 2 місяці тому +1

    APM VOTE

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 2 місяці тому +1

    Dats true,aend a thief to catch a thief(ziliko)

  • @OssmanAbubaker-k9w
    @OssmanAbubaker-k9w 2 місяці тому

    Zoonadi brother simukunama apatu MCP singawine ngakhale atabera motani

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 місяці тому +9

    APA panunkha kkk tambala tamugwira pakhosi

  • @BladesBullets-pu5uw
    @BladesBullets-pu5uw 2 місяці тому +1

    Chakwera adaziipitsira posamutsa ma office omwe amabweretsa mwayi wandalama kwa ochita malonda matauni a Zomba ndi Blantaya nkuwasamutsira ku Lilongwe. Komwe kuli kupha chigawo chakummwera. Choncho muchigawochi adzangopeza mavoti ambuli zo

  • @ChawandaBanda
    @ChawandaBanda 2 місяці тому +1

    Musaganize kuti mungadzachotse MCP ndi mademo ngati itawina! Zimenezo iwalani chimene muchite ndikupanga kampeni kuti mudzawine basi

    • @MandalaChaona
      @MandalaChaona 2 місяці тому +2

      👹🔨⛏️⚒️👹 Chikangawa Party 😂😂😂Devil at work

  • @SamLongwe-y9b
    @SamLongwe-y9b 2 місяці тому

    Iweso ndiwa dpp mcp sinaluzepo amayibera ili fans

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 2 місяці тому +3

    Tipex Thief Jane Ansa. Mtalimanja ndi machine Jane Ansa tipex Ansa wachepa

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell 2 місяці тому +2

    Dpp ndiyowina kale

    • @MjombaMjuba
      @MjombaMjuba 2 місяці тому

      Taa, ng'ooo mudzakhumudwa

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 2 місяці тому +2

    Zitsankho zogwiritsa ntchito akazi kubera mavoti no use of voting.

  • @kha6068
    @kha6068 2 місяці тому

    You are just imagining things tachoka iwe

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 2 місяці тому +1

    Mulungu ndiwadongosolo mwina wapanga dala kuti ikhale 50.50

  • @PreciousHenderson-qc1hq
    @PreciousHenderson-qc1hq 2 місяці тому

    APM My vote🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @PetersKondana
    @PetersKondana 2 місяці тому

    Pointless, straight wine for APM

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 2 місяці тому +4

    Kuchokera pamene ndinamva kuti boma lamukhulukira Boni Kalindo milandu yache sakuonekanso,nkutheka pamwamba pa kukhululuka anapatsidwa ma millions ngati Chibanzi ,koma ndingadandaule bwanji chifukwa ndiyekhayo akuyankhulira amalawi tonse

    • @ReginaMulipa
      @ReginaMulipa 2 місяці тому

      Sanapasidwe kathu iye uja samapanga za nyerotu akuti amadwala mupange search watulusa odio lero wapepesaso kuti amadwara alipo ndithu

    • @HarrentBanda
      @HarrentBanda 2 місяці тому

      Mhmmm ukunama aise amene ndi The DC

  • @jackmambo2638
    @jackmambo2638 2 місяці тому +4

    DPP is a system mwavomelazano😂😂

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 місяці тому

    Koma iweyo sindmapanga comment koma lero wandisangalatsatu keep it up bro ukuesetsa ntchito

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika 2 місяці тому

    Mwana wa John tembo asamale azaona nyenkhwe

  • @blessingssaiti
    @blessingssaiti 2 місяці тому +1

    Tizayenda kumene ASE MCP atayivotere ndan komaso inu khan imeneyo isiyeni zimenezo mumuphesa munthu

  • @harrispheleni2205
    @harrispheleni2205 2 місяці тому

    Ndiwe galu ufuna kupereka perception yofoila

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 2 місяці тому

    Akazangoyelekeza kubela anne mtalimanja wawoyo azaonongesa ziko azawona cnanga ana atenga mwana wa tembo kuti azabele zisakho akhawula awonaso sitizalola tikuziwa kuti chikangawa ndi woluza luza kale ameneyo or atamati ku votako mawa chikangawayo sangawine ka 😂😂😂😂

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px 2 місяці тому

    Ka Jane ansah nikandaniso kameneka kayidziwa MCP kuti sikugawa kamba idzawina iyeyo akuwona and adzavomekeza kt MCP wawina

    • @thomaswyson-e2q
      @thomaswyson-e2q 2 місяці тому

      Atiazvote ndiye ndiabamboako ndiamayiako kuphatikiza akazako anaako kumanso nkhukuzakwanu zonse olonso osazaiwala agalu ndiamphaka omwe kut ambwiyakoo azawine

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 місяці тому

    Ife chimanga tikuchisinja mutondo

  • @ChitsanzoMizere-tz7ye
    @ChitsanzoMizere-tz7ye 2 місяці тому +4

    Kkkkkkkkk amwene koma mumaganiza apapa nde kunkhala drama sure and mwachiziwikire Jane asah azankhale monitor kkkk

    • @Ahlubyt
      @Ahlubyt 2 місяці тому +1

      😂😂😂 Azakhaledi monitor 😂😂

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 2 місяці тому

      Adzakhar bwanj monitor ali phungu ? DPP inazolowela kubela kma MCP ndi 70+1

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 2 місяці тому

    Big up brother man!!

  • @RodneyMwapasa
    @RodneyMwapasa 2 місяці тому +1

    Pamenepa yalakwa kkkkkk

  • @GraciousKhonje-k8f
    @GraciousKhonje-k8f 2 місяці тому +1

    U are intelligent man

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt 2 місяці тому +3

    Send a thief to catch a thief 😂😂😂😂

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 місяці тому +1

    Kodi muli ndimaloto oti Mr chikangawa azawina ??

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому +1

    Ada awawa ndazelu chimene amandisangala ine akabwela khani satenga mbali enawa mmalo angoponya khani koma kuyikokomeza kuchita kunetsa kuti iwowo Ali mbali ya DPP

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 2 місяці тому

    Dpp 2025 woyeee

  • @EdenNgulube
    @EdenNgulube 2 місяці тому

    MCP PAYOKHA SINGATENGE BOMA MA DEMO AZAKHALA OCHEPA KOMA NKHONDO BASI

  • @daviechibwana3137
    @daviechibwana3137 2 місяці тому

    Ine sindingavotere munthu oti Mano mkamwa anatha nkhalamba ine ai 😂😂😂😂😂😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      @@daviechibwana3137 Boss mukuyankhula bwanji akumenyanitu anthu😂

  • @PeterChalechale-pz2bp
    @PeterChalechale-pz2bp 2 місяці тому +1

    Mukapanda kusamala kukhala civil war Malawi be ready for any attack

    • @MjombaMjuba
      @MjombaMjuba 2 місяці тому

      Zamkutu, mumayidziwa inu nkhondo, agang'anthi

  • @aminikondwani9361
    @aminikondwani9361 2 місяці тому +1

    Ndipo kudzavuta 😢😢

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 2 місяці тому +1

    Dpp ilowa awo kwao kwatha

  • @learnermuyaya-en9xi
    @learnermuyaya-en9xi 2 місяці тому

    Kkkkk, ndipo live apa ndi game ya mbava zokhazokha

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy 2 місяці тому +1

    ❤❤❤❤

  • @KaliyapaSeeter
    @KaliyapaSeeter 2 місяці тому +2

    Koma ine akulu awa nde amandisangalasa❤❤

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 місяці тому

    Kuzavuta kumwela Koko

  • @NedGft
    @NedGft 2 місяці тому

    Mcp sinawinepo zisankho

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl 2 місяці тому +1

    Kungobera kuzanunga linya

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 2 місяці тому

    Kumpoto tili pheee kudya zammathumba mwathu

  • @HendryChiwezo
    @HendryChiwezo 2 місяці тому

    Kutathauza kuti 2019 Jane adabela chisakho kuti pitala awine basi nowonso adzabela

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 2 місяці тому

    Tamugwila pa khosi tambala

  • @SandfordBanda-gk2dp
    @SandfordBanda-gk2dp 2 місяці тому

    Pajatu ndi 50+1 musayiware

  • @KhadijaMsosa-d7z
    @KhadijaMsosa-d7z 2 місяці тому +1

    Koma bro😂😂😂😂

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 2 місяці тому

    Mumakwana Pali mwambi amati mwana mbuu make mbuu

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 місяці тому

    Kodi DC anapita kut kwangoti zii

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh 2 місяці тому

    Kungowina chakwera kudzachela tidzamatcha mpka kuchikangawa

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 2 місяці тому +1

    Kuzavuta

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 місяці тому

    ndipo kuzakhala kuomberana tizavotaso kawili

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 2 місяці тому +2

    Amayendana pansi palibe kubela zisankho kkkkkkkk chaka Cha mawa kuli zinthu za nyo

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 місяці тому +1

    Kkkk a send thief to catch a thief😂😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      😂😂😂😂😂 Eeeeeetu azagwirana ufiti

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 2 місяці тому

    Kkkkkkkkkk nkhaniyo ndiyowona kuvutad

  • @Edwinsanga-zh4yv
    @Edwinsanga-zh4yv 2 місяці тому

    DPP bomaaaaaaaa 😅😅😅😅

  • @MoreenSemu
    @MoreenSemu 2 місяці тому

    Jen asah wachani

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 2 місяці тому

    Kugwetsa boma sizamasewera

  • @FrankChanza-l3g
    @FrankChanza-l3g 2 місяці тому

    Iwe tikamati ndiwe chisilu wawonatu kape wa mcp iwe galu

    • @Ahlubyt
      @Ahlubyt 2 місяці тому

      @@FrankChanza-l3g Anthunu nde simukumunvetsatu munthu yu ena akumunena kuti wa Mcp ena akuti wa Dpp😂 video yi mukuionera bwanji kodi sanaimire mbali iliyose tu uyu apa

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 2 місяці тому

    Azakhaula

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 місяці тому

    Ndipo 2025 kuvuta koopsa ..😂😂

  • @RobertCosmas-bo1uo
    @RobertCosmas-bo1uo 2 місяці тому +1

    Kkkkkk umakwana iwe wabwera

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 2 місяці тому +1

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @StevenDastan-b9u
    @StevenDastan-b9u 2 місяці тому

    Kkkkk koma ndiye

  • @Ertyvhk
    @Ertyvhk 2 місяці тому

    Akulu mukufuna mukambe chani sizikumvekatu

  • @Shamsdeenchikwakwa
    @Shamsdeenchikwakwa 2 місяці тому

    😂😂Kuzachema

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 2 місяці тому +1

    Paja winiko ananenatu kuti 2025 kuli zinthu 😂😂😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      😂😂😂 Atijigira madzi akuti mmidzimimu 2025

  • @GanizaniMagalasi-i1y
    @GanizaniMagalasi-i1y 2 місяці тому

    Iweyo ndichitsiru kwambiri ase sukudziwqnso chimwe ukuyqnkhula

    • @Ahlubyt
      @Ahlubyt 2 місяці тому

      Aaaaa iweyo nde namache... Chikangawa

  • @DouglasDazuKamwendo
    @DouglasDazuKamwendo 2 місяці тому

    Uzikhala serious poyankhula

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 2 місяці тому +3

    MCP zinawavuta chifukwa cha anthu anafa ku Chikangawa. Anthu tilibe mayankho

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      This is true Mayankho mpaka pano sanabwere

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 2 місяці тому +4

    Bolani asamupheso Jeni Ansa yo a MCP

    • @Ahlubyt
      @Ahlubyt 2 місяці тому +1

      Athadi kumusowetsatu 😂😂 asamale kwambiri

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      😂😂😂

  • @SalimZambia
    @SalimZambia 2 місяці тому

    Aise zamademo usakaike mwinanso nkhondo

  • @Jibsan-t2f
    @Jibsan-t2f 2 місяці тому +1

    Mn pangani nzero ina.imemeyo simunaganize bho inuyo

    • @Ahlubyt
      @Ahlubyt 2 місяці тому

      Ngati iyeyo akupanga nzeru? Mesa akuuzan za zomwe zizachitike kapena ndinu a Malawi Chikangress party 😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      Okay ndanva inusl mupeze comment ina ya nzeru iyiyi mulibemo zeru yayi😂

  • @Ahlubyt
    @Ahlubyt 2 місяці тому +1

    😂😂😂😂
    Apapa agwirana umbavadi 😂😂😂😂😂😂

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 2 місяці тому

      Ai Macson mbendela anabela zisankho, jane ansah anabelas ai palibe kusintha boma apa

  • @fahadhasan2222
    @fahadhasan2222 2 місяці тому +1

    50+1 m,bale

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 2 місяці тому

    Kodi uli mbali ya mcp olo zita vuta ulendo basi

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      Ai baba 😂 nkhani ili apa ndiya Zisankho osati wa Mcp or not 😂

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 2 місяці тому

    Thieves and evil.

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 2 місяці тому +1

    Apaaa MCP yagwidwa basi ma plan awo atha basi😂😂😂😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 місяці тому

      😂Iwo anzao anawathothola ndi Mademo nao ayembekezere zomwezo 😂

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 2 місяці тому

      @@MalawianCamera 🤣🤣🤣🤣Ndipo Adha apapa kulinkhondo koopsa Zedi azalira a MCP 🤣🤣🤣🤣🤣 wapanga dala Jane Ansah Kuti azizati lakutipo tionenso nanga apaaa bwanji?🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому +1

    Dr Lz 2025 boma kale

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 місяці тому +3

      Ukulota ase kuchokera 1984 Mcp sitingawine payokha ma bwana anuwo akutiimbila phone kuti apa zavuta nde inu mukuti chani apa ena ayamba kale kugula nyumba kuno kudzakhala ena atumiza kale family yawo sitingawine ase

    • @ThokoMsonkho-hy4uc
      @ThokoMsonkho-hy4uc 2 місяці тому +1

      Chakwera sangawine zisankho 2025 pokhapokha adzabere.
      Koma akadzangobera zidzaziwika bcoz ambiri samamufuna, tidzaonera zobwibwi

    • @spargomw
      @spargomw 2 місяці тому +1

      Maloto achumba😂😂😂😂😂

    • @paulkalizangoma5904
      @paulkalizangoma5904 2 місяці тому +1

      Day dreamer lwe!

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 місяці тому

      @@ThokoMsonkho-hy4uc komaso kubelako zivuta Jane Ansah maso alipompo paja nayeso ndi dolo kkkkkkkuchematu

  • @Laurent-h9u
    @Laurent-h9u 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂

  • @ElizaKumwenda
    @ElizaKumwenda 2 місяці тому +1

    APM my vote