Zomvesa chisoni kwambiri

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 15

  • @ThreeBrothers-ww2zh
    @ThreeBrothers-ww2zh 3 години тому +1

    Palibe cha mnzeru apa

  • @KennedyKManda
    @KennedyKManda 4 години тому +1

    Amene am amagenda anali anyamata akwasundwe apite akagwile.

  • @ThomasJohn-d9r
    @ThomasJohn-d9r 4 години тому +1

    Ma Report awa opusa kwambiri

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 3 години тому +1

    Report lenileni liziwika tikawachotsa Pampando Sept 2025

  • @AdamRobert-u9v
    @AdamRobert-u9v 20 хвилин тому

    inuyi ameneyo ayi zikomo

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 3 години тому

    Kodi vp Sanavale jekete pokwera ndege kupita ku Maliro?

  • @AlexanderTraffick
    @AlexanderTraffick Годину тому

    Kodi yemwe akajambura ku Airport uja namanong,onedzana aja alikuti

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 4 години тому

    Chipatso choyendetsa ndege kuchita expire 😅😅😅

    • @AdamRobert-u9v
      @AdamRobert-u9v 18 хвилин тому

      inenso kudabwa tu mwina sitizisata kuti zithanso kupanga expire then nkupangisa ngozi

  • @ireentaombe
    @ireentaombe 3 години тому

    Koma yaa 😢

  • @BlueTicksound-ow4fq
    @BlueTicksound-ow4fq 6 годин тому +1

    Ndege ya boma zosezi mukuyakhura ndi zaboza simunapeze zifukwa zitatu kungwesa chithu chimozi ayi mukanafotokoza chithu chimozi bola, Malawi ndife anthu opusa kwambiri ngati ndege inalibe vuto black box inapita kuti? And ndege sinanyamuke mwa emergency zitheka bwanji kt oyendesa osawaziwisa za nyengo?

  • @InessRenard
    @InessRenard 7 годин тому +1

    Koma zolakhulazo muzilakhula ngati omwe adamwalira achibale awo adakali
    Moyo ma report anu onukhawo

  • @LottiAffati
    @LottiAffati 7 годин тому

    koma kumalawi kuno tinaputsadi ndipo tili kutali tidakali upusabe

  • @PeterChaponda
    @PeterChaponda 7 годин тому

    Nde amalola bwanji muthu oti alibe chiphaso kumayendetsa ndege?