NKHANI IJA YAFIKA MPAKA KU NSOKHANO WA DPP __15 December 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 39

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 4 години тому +2

    💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙 odii uko! Aini ndilande afika mu gheto APM 2025 boma!

  • @Nechealkeet
    @Nechealkeet 3 години тому

    Watching live from Capetown, RSA.

  • @GeoffreyMarko-v3s
    @GeoffreyMarko-v3s 5 годин тому +1

    💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💗💙💗💗💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙. APM 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MemoryZiyaya
    @MemoryZiyaya 4 години тому +1

    💙🧢💙boma ilooo mughetto!!

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 4 години тому +1

    Rerpot la mcp imene ija

  • @Dinalamakanjira
    @Dinalamakanjira Годину тому

    Ngakhare Ku Ameleka avomera kuti akuwina Ku Malawi chaka chamawa ndi Peter Muthalika katundu omànga ndi mawaya

  • @stanfordchiwaulah8837
    @stanfordchiwaulah8837 49 хвилин тому

    💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @CyprianoSandalamu
    @CyprianoSandalamu 3 години тому +1

    Kanamizanani komweko peter sadzalowa m'boma vomerezani kuti mudawinapo ndipo simudzalamulaso .

    • @JosephyMwambe
      @JosephyMwambe Годину тому

      Ngat asazalowe m,boma atalowe ndimachende akowo nang'ongowamakonso

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 37 хвилин тому

    Mukamatitu dpp singaloweso m'boma dziwani kuti munamizana ngati mukuganiza kuti mcp ingawineso payokha,,,ndilitilo mcp idawinako payokha,,,,zipani zikaphatikizana zizawina 50%+1 mukamati boma ndilomweli muzidziwa kuti kuli 50%+1 yomwe palibe chipani chingawine pachokha ku malawi,,,mcp ipange mgwilizano ndi chipani chinaso ithaso kuzawina or dpp siyingawine payokha,,,,pano ikulamula kamba kazipani zochuluka zomwe zinapanga mgwilizano kugwetsa dpp,,,,
    Osamayiwalatuyi,,ndiye pano chomwe mcp ingaluzile palibe chipani chomwe chingalole kupanga mgwilizano ndi mcp basi chifukwa siyingapeze 50%+1 payokha

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 4 години тому

    APM is on the way stetar Haus again 2025

  • @MedsonNkhoma-s2d
    @MedsonNkhoma-s2d 2 години тому

    Mukunama inu, mudatizuza kale simungabwerereso mu boma. Bola mudzavomereze zotsatila za chisamkho

    • @AlihIbrahim-s7v
      @AlihIbrahim-s7v 30 хвилин тому

      Eyadi koma bolani anthu amadya,,,,mu history ya malawi tadziwa pano kuti Anthu amadya chitedze,,,,kwathukuno ku Dedza mwina vote izapezeka ya mcp koma ndakayika,,,,Anthu kuno akusiyanitsa ndi boma la dpp,,,anthu amakwanitsa kugula matumba awiri omwe ali ovutika koma lelo akulephela kupeza yathumba or limodzi,,,palibeso zovotela kuti ndiwa central region aliyese akuvutika,,,,ndiye mukamati mcp iwinaso okay it's fine,,,koma muzizitsata kuti kuli 50%+1 azanuwo apanga mgwilizano kuti adzapeze 50%+1 pomwe enanu ndizovuta kuti mupezaso opanganaye mgwilizano ndipomwe zingakuvutileni,,,

  • @MedsonNkhoma-s2d
    @MedsonNkhoma-s2d 2 години тому

    Guys tien tisamanam8zane, dpp sidzalamulilaso. Olamkhula kazilankhulan ma bodza anuwo. Pokha pokha , peter, Nankhumwa, Joice Banda, Kabambe ndi ena apange mgwilizano.Apo biii simudzawinaso

    • @AlihIbrahim-s7v
      @AlihIbrahim-s7v 43 хвилини тому

      Tizipitilizasotu kuti mcp siyingawine payokha,,,,ndipo sidawinepo payokha kuchokela kalekale,,,osamanamizana kuti boma ndilomweli,,,,azawina munjila yanji,,,palibe chipani chingawine pachokhayi ku malawi aliyese akudziwa,,,,dpp ikapangaphatikizana ndi zipani zina idzapeza 50%+1

  • @InnocentWisiki
    @InnocentWisiki 3 години тому

    Kkkkk kwamvuta kundilande

  • @JosmanMw-di5vl
    @JosmanMw-di5vl 4 години тому

    Dpp my vote tikubwelera m boma 2025

    • @MedsonNkhoma-s2d
      @MedsonNkhoma-s2d 2 години тому

      Kulibe kubwereraso ankolo, dpp idatuluka idatuluka basi

    • @JosmanMw-di5vl
      @JosmanMw-di5vl Годину тому

      @MedsonNkhoma-s2d umeneyo nde uchisiruyo

    • @JosmanMw-di5vl
      @JosmanMw-di5vl Годину тому

      @MedsonNkhoma-s2d ifeyo inshallah 2025 tikulowa m,boma 💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @YohaneJohn-n3l
    @YohaneJohn-n3l 5 годин тому +1

    Report lonama

    • @MaingaKam
      @MaingaKam 4 години тому

      DPP ndiyakuba ndiyakupha ndiyonama mavutowosewa munabweretsa ndinu

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 4 години тому

      ​@@MaingaKammesa Inu polowa m'boma mmati mukukakoza zinthu ngt azanuo anaononga Inu ndiziti zomwe mwazikoza?? Bread alipabwanji pano, chimanga, fertilizer mwakoza zimenez pokweza mitengo??

    • @RaheemNgoma-pk1ev
      @RaheemNgoma-pk1ev 3 години тому

      Inuso ndi achitsilu et ngat linaononga inu mulekelanji kukoza? Anyau ​@@MaingaKam

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 4 години тому

    Mphuchu

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 5 годин тому +2

    DPP si ya chilungamo

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 4 години тому

      DPP kwake ndi kupha,kuba ndi kuwononga sakusiyana ndi makhalidwe a satana

    • @symoldicky
      @symoldicky 4 години тому

      Nde ndi ati achilungamo ? Pot mcp ndi tonse Alliance ndi awa atigwilitsa chiphwisi ndi manja feteleza mmalo mwa 4000 ndi 100.000 kudya katatu kuja kulibe . mafuta kusowa zinthu kukwera

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 4 години тому

      @symoldicky sizingatheke zimenezo mayiko omwe amapanga fetereza ndi awo alipo nkhondo kungoti chilima samadziwa za mtsogolo koma kulankhula ngati kuti nyengo inali mmanja mwake anotu ndi masiku otsiliza ngati mwayiwala zanu zimenezo chilichonse mukuchiwona ziposanso pamenepa andale kwawo ndi kulankhula ndi ochepa akapulumuke DPP mulungu anayichotsa ameneso amuyike chaka cha mawa mumuwona koma zinthu sizisintha because nthawi yatheratu

    • @phindiswatshibo7101
      @phindiswatshibo7101 4 години тому

      ​@@symoldickyaise asakutaise nthawi ameneyo palibe amakhala 100.%koma mcp ndiyakupha komaso akuonesa kuti ndi wachichepere akufuse agogo Ake akamuuza za mcp Dpp woyeeeeeee basi💙💙💙💙💙💙💙

    • @FelixAndafu
      @FelixAndafu 4 години тому

      Nde utani ? Usamuka