Ine ndili kutali but I love brother kalindo ndiye ndingoti may Allah almighty be with him munyengo zowawitsa ngati izi koma pa mtendele mulungu ndi wadzatheka bwanji mulungu akumenyelani nkhondo ameen 🙏🙏🙏
Patrícia ng'oma Hule anagona ndi amuna Ten kamodzi ku Cape Town Hule,hule chihule atinso amanunkha musazanyenge ali ndi Edzi, komanso a MCP onse panyero pamawo ndiri konkuno ku Cape Town
Mulungu Muthandize A bon kalindo munthu okoma mtima omva chisoni ndi amalawi ndikanakondwa Ndikadakhala pafupi ndipite nawo kukamvera milandu imeneyo kuchoka kuno kuthyolo thekerani
Mulungu Ali kumbali yanu ,tikupepherelani ,ife mulungu wathu ndiwoteteza ndiwokhulupilika
But amtanyiwa ndava mwatchulamo our vice president Ben Longwe anadyaso nawo zovundazo?
Patricia ndi hule, anali kuno Ku Dunoon Capetown, ma video ake Lololo ovula azipanga zake zija
Mulingo umene ukumuyezela nzako mulungu adzakuezele omwewo always god with u
Zivute zitani ife amalawi tili pambuyo palipompo komaso winiko kkkk more fire akalindo akukulepherani kkkkk awonetseni yanu ija kkkkk
God is watching, their throne is given to another one. But for now you must persevere
Bon kalindoyo kalero anali wachipani chanji lero muli bzy ndizimenezo zachamba
Gwaladi yemweyo ukamati ndikanyuwani osaziwa anzako atopanaye
God is watching indeed
Kma Mcp yatikwana ndi nyasi zomwe zikuchitikazi
Ayaluse zenizeni asamajaile
Ine ndili kutali but I love brother kalindo ndiye ndingoti may Allah almighty be with him munyengo zowawitsa ngati izi koma pa mtendele mulungu ndi wadzatheka bwanji mulungu akumenyelani nkhondo ameen 🙏🙏🙏
Arest the guy he's full of himself
Ben Longwe mukumutchulayu naye anachita naye mmayiyu
Ineso ndadabwa koma osati angomutchula coz nayeso ananenapo kut amuyalusa mayiyu n ihope ndiye watumiza mayina a amunawa ibelieve
Zafikapachipongwetsopano nangandizokhazokhazi enawatundima empty vessels osapusanawo noiseyo yawonjeza
Koma iwe Mtanyiwa
Kalindo suliwekha
Kaya kumeneko Mtanyiwa
Bon kalindu Mulungu aku samalile
Ambiri amachemeleramunthukungofunakumukankhilakoipa komaalibenaye film
Ubino ndiot mukuziwa kit iyi ndi m c p
Koma ayaluka mayiyu eeeeeee
Eeeeeeeeeeeeeeeeee eeeeeeeeeeeeeeeeee eeeeeeeeeeeeeeeeee eeeeeeeeeeeeeeeeee eeeeeeeeeeeeeeeeee eeeeeeeeeeeeeeeeee ine ndikafila koko ndikuti ndikafila koko ndikuti ndikafila koko ndikuti ndikafila koko eeeeeeeeeeeeeeeeee zabwana zopusa sitifuna zopusa ayi sitisiya kupanga mademo sitisiya tinakapanga mademo sitisiya mukusiya kumanga athu oba ndalama zambili pono mukufuna kumuzuza bon eriyasi kalindo ndipo koma mukunana ine ndikafila koko ndikuti ndikafila koko ndikuti ndikafila koko dziko mwalisikoneza nokha ife koma sizithekha Moti tikundikila manday mukunama mwachepa tionetsana manday
I said ine ikalilisa ngoma imaphulika
Tapezan zina zochita sizomatithela ma bundle ndi nkhn zopusaxi ayi
MCP kukhalila kumanga anthu aaa yatikwana😢
Mulungu simuthu
Hehehe Ascent kuchita kudziwikiratu😂😂
Patrícia ng'oma Hule anagona ndi amuna Ten kamodzi ku Cape Town Hule,hule chihule atinso amanunkha musazanyenge ali ndi Edzi, komanso a MCP onse panyero pamawo ndiri konkuno ku Cape Town
Talita kum it's Hebrew word meaning mtsikana dzuka
A Hebrew man (me) has translated
Ulemu wanu
Nosense
Ma program anuwa akutivuta kumvera bwanji
Why again after bello out?
Komano malawi mcp yapezelela malawiyo
Mwakhuta kachaso Kodi mukuputila dala lero mufuna anthu asiye kukapanga maganyu azikamvetsela milandu chamba
Ngt sizikukukhuza osatulukako bwanji alipo akupanikiza kt usegule radio imeneyi
Ntanyuwa iweyo ndimbambande
Ungofunapo ndalama inu kukupatsani 2,000000 mungasokoselenso pa waiyelesi inu tikulephela kugona chifukwa Cha inu
Iwe osatseka radio yakoyo bwanji
Mmmmmm komatu mmmmm onsewooo
Mcp was evil n would be evil
aaaaaaaaa Kagwele uko iwe wangindithela bandulo yanga, zanziiiiiiii!!!!!!!!!
Talithakumi dzuka bwela kuno Mai patrisha muzifele mtolo🤣🤣🤣🤣🤣
Azimvele chisoni ameneyi ndipo apha anthu ambili
Tili pambuyo pa kalindo
Mwatimvesa kukoma
Big up Limpopo fm kkkkk akut ose nyinbo yake ndi kwathu sipadziko 😂😂 💪💪💪🔥🔥🔥
bon kalindo ❤️❤️❤️
Collen zamba not zanga zanga chikhosi,chikhosi is a man
Àlomwe boza kwambili
Tiyambise nkhondo amalawi okaoka RIp mcp
Zoona big man auze umakwana
😂😂😂😂
Asowa olimbana nawo amenewo zawavuta basi anthu amagazi mmaja
Basi, program ndi program, zimenezi 😢
Kamuzu banda mzimu wake uzuzike modetsa nkhawa
Kenako tizangomva ziiiiiii ngat Timothy Mtambo
Fundo zili umu zosagwira
Kkkķkk zoona Achoke Chakwala
Shameful party 🐓🐓🦂😢😢
Vp wa malawi first ationetse njira
Mtanyiwa thx nkhanga zaona
Pathako panu alhomwe
Wants nayo mbale
Limpopo 🤸🤸🤸😅😅🤸🤸
If you loved and miss Kamuzu Banda give a thumb up as l was born free❤ Kamuzu and Rip.
Tikhamukila konko
Mndyangu
Mukadabwelatu koma osamangosokosa apa
Kudzataniso nanu aaaaa malawi wakeuyu
Kodi achitsiru awa amachulukitsa bodza bwanji
Chitsilu ndi iweo
@@MisheckKanyenda-vx4yv pambolo pako iwe
Big up Limpopo FM along side comrade Mtanyiwa, proud of you 🔥🔥🔥🔥