He was a blessed man, the problem which Africans have,we need people who think slow. Among the group of 10 members, we could have found zero or one genius person like the late SKC. may his soul rest in peace.
Ndinchoncho ndithu utsogoleli wamaso phenya ndichomwe tikufuna Ife amalawi posayang'qnq komwe ukuchokela or Mthundu and Chilakhulo I like you Mr Chilima that is why you have to be a president form may 2019
Popeleka ma comment muzidziwa kuti izizi anakambirana 2019 komabpa nkhani ya utsogoleri wabwino nde mtunda wake nde ndi umenewu basi Malawi okomela tonse kom poti maganizo ndi osiyana ena mumafunitsitsa Gogo lochita kugwirizana kutsika pa nsanja akhale president ena akufuna ena ngati wamtundu wawo zomwe tikuchedwetsa nazo Malawi kutukuka chosecho Atsogoleri anzeru tili nawo mdziko muno monga Atupele Muluzi,Enock Chihana, Kondwani namkhumwa,Dr Chilima ndi ena ofunira dziko lathu zabwino koma kukakamira ali panowa ndekuti dzikoli sitikulifunira zabwino his the good person koma amapanga zinganizo mochedwa ngati Gogo and zovuta kusiyanitsa Gogo munthalika ndi awawa sizikusiyana kwekweni lets liour county Malawians posakha munthu oopeka komaso wa maso mphenya ufunira zabwino dziko lake ngati Atsogoleri ndatchula aja zamitundu zatichedwetsa a Malawi

Munthu wamkulu kulakhula modekha
Timawakonda wakuluwa
Wish him all the best
Zoonad ❤
was a powerful speach
My vote.
Rip abiyeni only God knows
Ndinchoncho ndithu utsogoleli wamaso phenya ndichomwe tikufuna Ife amalawi posayang'qnq komwe ukuchokela or Mthundu and Chilakhulo I like you Mr Chilima that is why you have to be a president form may 2019
Mawa limafikatu ino ndi 2023😂😂😂😂
Bola chilima emweyo.😮😅😊🎉❤
A biyeni munapitadi zoona😭
Popeleka ma comment muzidziwa kuti izizi anakambirana 2019 komabpa nkhani ya utsogoleri wabwino nde mtunda wake nde ndi umenewu basi Malawi okomela tonse kom poti maganizo ndi osiyana ena mumafunitsitsa Gogo lochita kugwirizana kutsika pa nsanja akhale president ena akufuna ena ngati wamtundu wawo zomwe tikuchedwetsa nazo Malawi kutukuka chosecho Atsogoleri anzeru tili nawo mdziko muno monga Atupele Muluzi,Enock Chihana, Kondwani namkhumwa,Dr Chilima ndi ena ofunira dziko lathu zabwino koma kukakamira ali panowa ndekuti dzikoli sitikulifunira zabwino his the good person koma amapanga zinganizo mochedwa ngati Gogo and zovuta kusiyanitsa Gogo munthalika ndi awawa sizikusiyana kwekweni lets liour county Malawians posakha munthu oopeka komaso wa maso mphenya ufunira zabwino dziko lake ngati Atsogoleri ndatchula aja zamitundu zatichedwetsa a Malawi
😢
Simungawine ai,,,bro Malawi ya kuwerenga chilima serious
Koma ifa ndiyopweteka
Olo chilimayo atenga boma ndiye angapa tchani
AWA NDI akatundu ATATI akhale president akhoza kukozapo zinazake koma
Ai sangaime us president, uyu ndimbava azikhara us vice pa chinthu
Siizi mazilephela
Bodza lako lawakonda amalawi.!!😮
Boma iloooooooo 2019
Ayimeso mulungu atsogolele
Mumakonda kucheza ndi chilima ekha bwanji muzichezaso ndi achina muthalika makamaka muthalikayo tikufuna mutacheza nayeko pompano plz
Koma imfa iwe mmmmmmm
Bwelani ku dpp mkulu
Chilima agwilizane ndi nankhumwa atenga bomali
Kkkkkkkkkkkk chilima chilima chilima kkkkkkk president of Malawi ukahara iwe kkkkkk
Chilima boma looo
Ya masomphenya abwino
Chilma mbuzi yamunthu
Chilima udari ngati shasha ku dpp kuja,,,,,bro sorry mcp sungamake wachepa komaso just kudikira ndende bro,,,,,udaziputa za ma big