The problem of this proticians kuba awa kugowina bac amakhala asitha zochita kukhutisa mimba zawo amakhala abwino chochi ali ku opposition ayikeni muwone muzalira inu
Kod bwanji mr aford amamvanana ndi lamaposa aford ukusiwa chani UDF kapena dpp utm kom inu maso atu alipamenepo usigoleri wabwino 1adadi 2 UDF 3aford 4utm bas mulungu akudalisene ini
Quite fantastic 👏👏👏 remarks of the great Leader We are tired of IMF ngongole mpaka 16 trillion 3 trillion for killing Chilima President 4 trillion Mkaku 1 trillion Kunkuya 1 trillion Chimwendu 1 trillion Catherine hazi 2 trillion Kamajekete 1 trillion General phira 1 trillion Namagetsi wa polis 1 trillion Mkada wa za chuma 1 trillion
The presidents speech was fine. But missed to expend on national security, food security and economic trajectories. Please engage ur team to do more research on the issues that you highlighted. They are really true. So that a Malawi amvetse as we delve into the polical compain rallies. Thanx.
Koma pa speech yanu Mr chihana point sindiku imva,Auzen ma plan anu ,wosangonyoza,Mcp imanena chonchi nayoso imanyoza pitara,kugenda pitara pano ndiiwo
Aford and opposition parties unite for the benefit of all Malawians dziko laola ili palibe chakwera akupanga mavuto kwa mavuto
Cheap politics
Absolute truth 😢
SKC forever in our hearts
A very good and powerfully speech. Viva Chihana
Eish I didn't no that Chihana has got wise words like this, wish you all the best keep the fire 🔥 burning
Chilima will never be forgotten
How could we? 😢😢
Wow!!!! I love this speech , very powerful speech indeed
Massive Combination! CHAKWERA BWERA KUNO UDZAONE WEKHA.
Kip resting well VP (BIYEN?) we shall not have someone else like you. FAKE ALIANCE TOOK YOU AWAY FROM US😭😭
palibepo apa powerful speech,kungochemelera zili zonse,a malawi kutengeka basi.
Anali momo ndipo akanakhali kuti Ali ndi unduna momobe mpaka pano bwezi zinsenzi zikukambidwa tsono?
Andalewa pliz amalawi,Mukazitengera udyo mukuliononga dzikoli
Amalawi ambiriwa ndopepela. Amapanga zisankho zowapweteka iwo omwewo. Adasankha MCP adali omwewatu lero ndi izi
Akuwononga dziko ndi chakwera osati ife
Imagine kupha anthu osalakwa eish!!!! Rest in peace chilima and the other comrades
Ndifuna ndilembe bunkhu lokhuzana ndi za kuchikangawa😢😢
Plz
Lembadi bale
Biyeni still in my mind forever😢😢😢
Ine ndiye izi ndazikonda heavy🎉🎉
Good for thinking about our late brothers who fought for our beautiful democracy
The problem of this proticians kuba awa kugowina bac amakhala asitha zochita kukhutisa mimba zawo amakhala abwino chochi ali ku opposition ayikeni muwone muzalira inu
Exactly
Kod bwanji mr aford amamvanana ndi lamaposa aford ukusiwa chani UDF kapena dpp utm kom inu maso atu alipamenepo usigoleri wabwino 1adadi 2 UDF 3aford 4utm bas mulungu akudalisene ini
Skc for ever , abwino sakhalitsa
Power like android Chihana gud speech
Eastbank congratulation pomugagada chikangawa ndi miyala yona wazungulila mutu azingendedwa choncho galu wachabechabe chikangawa
Ndipo ine ndiye zandikomera, well done sena tribe 😂😂😂😂😂
Mwana wa Simbi ya moto,, courageous like his late father
Quite fantastic
👏👏👏 remarks of the great Leader
We are tired of IMF ngongole mpaka 16 trillion
3 trillion for killing Chilima
President 4 trillion
Mkaku 1 trillion
Kunkuya 1 trillion
Chimwendu 1 trillion
Catherine hazi 2 trillion
Kamajekete 1 trillion
General phira 1 trillion
Namagetsi wa polis 1 trillion
Mkada wa za chuma 1 trillion
DPP. UDF... AFORD..... BOMA!!!!!!!.
Zaziiii, a Malawi kupusa,
Wa MCP muno ay
@@HawardKalipandeandale musanamizike nawo. Anthuwa sakukondani
Powerful massage ❤
🎉tidzakuwonani nanu mukusitha mawanga ndani sakudziwani anthu andale inu mukufuna kutipusitsa basi
Good said 👍 Mr Chihana
Powerful speech koma mukati mwalitenga bomali mwayankhulaapazi mukazichita bwana pule?
Tidzakuvoteranitu chifukwa cha mawu anuwa
Please pangani alliance ndi zipani zonse mwatchula kuti mwina Malawi yingapulumuke, Chakwera ndi boma lake la MCP atikwana.
Wishful thinking
The type of president we need in Malawi
40 year in politics change nothing negative negative negative ...
The presidents speech was fine. But missed to expend on national security, food security and economic trajectories. Please engage ur team to do more research on the issues that you highlighted. They are really true. So that a Malawi amvetse as we delve into the polical compain rallies. Thanx.
Anthu awa sanasithe ai kma chilima 😢😢
Mzimu wa chilima uwuse mumtendere
That's true and exactly boss keep move on
"Zikufunika munthu oganiza bhooo" end of quote.
Leader of opposition angaithe bwanawa
Pena ndimadzaona ngati mutu wa chihana sumayenda bwino.....
Awa akulimbana ndi Alliance zakale tikufuna mfundo zomanga ziko ife osati kulozana chala apa
I'm afraid that sungazione kumene uliko. It's not your fault 😢
funny how they hated DPP AND now they want to partner...😂😂😂😂
What is the meaning of Kapuku?
I love this dude
Is the kind of mbewa
Koma pa speech yanu Mr chihana point sindiku imva,Auzen ma plan anu ,wosangonyoza,Mcp imanena chonchi nayoso imanyoza pitara,kugenda pitara pano ndiiwo
Am watching from rumphi vinyolonyondo
Ndale zachikale izi zomangonena zifooko za anzanu. Tanenani zimenene muzachite tikakuvoterani
Rest in eternal peace Dr Chilima🙏🏽
❤dpp woye katiwezgerenipo ufumu wanthu wakwa chikulamayembe mcp boma la nkhaza kwambiro
Ndil boma lankhaza kwambiri
kupanda zelu inu
Good speech 👏👏❤❤
Beautiful 😊
Apa chikangawa wautali bac muumodzi muli mphamvu
Wandiwaza pa dzina loti Kapuku hahahahah😂 Chihanga wakhadzulatu apa
Chikatero cha MCP chilipakona chufuna chizinyoza
Anthu andale panyopanu sure, anthu osakhulupilika inu mbuzi
😂😂😂😂😂
Tizingokhalira kupepha basi 😢😢😢
Gud speech
Nice wordz mr
So nice
Good speech 👏
Bola mupange mgwirizano ndikusainirani tisakaone ngat za chikangawa ndi mzake
Good speech chihana
Hahahaha anakuuzani ndiye munkadikira amwalire kuti mutinamizepo 😂😂😂😂
Rip SKC
Manifesto ya aford ilipo koma?
Vilombo vayamba kunjenjemela
Powerful
Malawi titamuyesa uyu mwina
Tisamayese zinthu nkana tikulakwitsa,onsewa akutinamidzapo....ndale za ku 🇲🇼 ndizokolezera ziwawa....ndi angati amene akhala akupangidwa chipongwe....PeterBakili ....zinawawoneka...ndeno mumafuna alanule ankhondo awaphe anthu ake kenako muziti president wapha anthu ngati Bingu
Combination yabwino kwabasi
Nvuto anthunu mmabwera ndmawu okoma chochi koma kungolowa mmboma iiiiiiiiiiiii kaya zolankhulaz zmankhara zapita kuti kaya aaaa
Very stupid decision making ever....you guys costed him his life.....he never consulted his party members
Empty speech. Just pointing weaknesses in the current state. No tangible indication of what he & his party will do after getting unto government.
Collable iyiyi ya APM Chihana plus UTM mmmmm ndaikonda kwambr
The words kapuku😅😅😅😅😅😅
Kkkkkkkkk koma uyoooo kkkkk khope ngati gulukunyinda
Uthenga wabwino suchitisa manyazi polakhula
Ichi sichiopa yoooo
Azimayi kuvina basi 😂
I see Chakufwa
Let's vote for FORD
Zoonadi Brother zikumveka
Inock chihana chifukwa chopanda nzelu azathesa chipani cheche chipani cha AFFORD chilibe mphavu chifukwa chosowa msogoleli akanasankha msogoleli wina mwina chingathe kupitabe pasogolo chifukwa inock nde mbuzi yeniyeni
Dc wat tiona zinthu chaka chamawa
Which iz going into government
Ndiye simunatitu kusamvako muchitanso mistake ina sure
Zomwe akukamba awazi akuchedwa ife tikufunamfundo lekani kulimbana ndiwathu zigulitseni nokha ife tikufuna ma plan anu
Ngati abombo achihana afelelamo apanda upule ndiye awa angakhale zaziii zopanda mchele
Ndina achitsiru inu munali m'boma ndiye kuganiza kwa bho kwabwera relo simunali president mukupitaso kokaberekedwaso zaukape bas
Zomwe amanena bingu izi
Manifesto a mu alliance yanu ndi CHILIMA CHIKANGAWA,
.... aaah 🚮 shame!
Zabodza izi masiku onsewa bwanji sunkanena zimenezi mnzakoyo alimoyo,imfa yanzanu mukupangila company
Nanutu mukumachulusa kulankhurira aaaa zoremba zomwezo zokwana Ka
koma azimayi achipani mmmm mumakwana mulungu azikudalitsani kkkkkkkk
Awa ndiachisiru bwanji? Atumizileni message yangayo kuti ndiachisiru, akusangalala ndizomwe zachitika kuchikwawa iwo akazatibulidwa kwina azikati MCP yawachita chipongwe
Munthu odziwa ndale sanyoza anzake,pikisanani pa fundo
Kunalibe ku mcp izi uku kwatsangasa
I hated MCP
Dzifotokozani fundo zoti anthu zizawathandize osati kumangonyoza azanu komaso malilo asakhale choti muzichitila kampeni muzikamba zoti muzalitukula bwanji dzikoli osati uje ndi oyipa inuyo ndi abwino muli ndi mavuto anuso kozani anuwo
Kkkkkk koma abale ndiye awa omwe kkkkkkk
Kapuku wina kkkkkk
Osaopa osafooka osalola
Waphodatu nanga nyautete
Koma chaka cha mawa kuli zinthu dzimitu dzadxikuludzikulu dzigugumuka ndithu
Kodi kumangonena za zipani za anzanu ndiye mfundo zozalowera nazo muboma?