Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
For us who don't understand your language, please try to be writing some translations down. But the content looks good. Moto unandi🔥
Welcome brother 2024 mumakwana ndithu
😂😂😂😂😂 komatu mandota chakachi wachiyamba ndikuchimva kuwawa
Tinakusowatu mandota timakhala ndingawa kut kuluyu zikut bwanji kapena akita amfa😅😅😅😅
I'm a comedian and I wish to be followed by you ❤️
😂😂😂😂😂 koma chemandota iyaaaa iweyo basi ndidolo....musadure ngini ya mbasada😂
😂😂😂 usamaliya ndiomwe wakuphweteketsa😅
Welcome again mandota❤
❤❤❤❤welcome back she mandota
Muntu wankuluuuu.... 😮😮😮😮 Msanga wanga
Mpakana kukawaikila aneba Madi kubafa😅
Lifidiyo lilinyc 🔥 , koma sound sinapangwe record bwino.
Koma che mandota asaaa umatiwaza mawu okha ndiomwe akundisekesa iyaaa mawu ngati akuchoka mu botolo la coke
Welcome back Big Man.Wadzatu ndi Moto 😂😂😂😂😂Keep it up Che Mandota
Anasowatu mkuluyu
Moto unandi 🔥🔥🔥
2024 nde mwabweratu fah🎉
Mwapeza nyumba yabwinotu pano Che
Siwiyaso adule bazi😅😅😅😂😂😂😂
Mandota iweyo unabwela kudzakhala umakwana ngat la 40 😂😂
Nkhani ndi kankanjoko sikafuna kukhala strength 😂😂😂😂mandota please 😅😅❤
🤣🤣🤣🤣ati nde zipepesani kkkk mandota welcome back again 2024
Taonani taonani zilikotu ziliko😂😂😂😂😂
❤❤❤❤❤musazafe inuyo mumatiimilira is
Welcome my brother che mandota kachikena
ndota udulidwa gadafitu kenako iwe 😂😂😂😂😂😂😂. Kodi wasintha ka chikofiya you number on ndox nde ndikunyamulizeni neba 😂😂😂😂😂😂
Sono mukamapepetsa ndikhala ngt ine olakwa kkkkkkkk , kom Mandota
Comedian #1 the whole of this Malawi
Mandota iweyo umakwana
Koma mwini nkaziyo akanakhala kakhani kukanavuta😂😂😂 komabe naeso wabwela bho
Akatundu pangolin katundu ja boma😂😂😂
Lichipewa lanyuwani 2024
Thanks!
Wachiyao wangalusa brother 😂
Wagula ka chisoti kena ase Mendota 😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkk mandota umativesa kukoma🤣🤣🤣🤣🤣
Ndimakunyadilani brother ❤🎉❤❤❤
Eeeh eeh akut kuyivelaaa😂😂😂😂 futo niuzamaliyaa che mandota bola amapuma Bax 😂😂
Actor omangofa daily bwanji kkkkk
Sopano inu mwasitha Ka chikofiya 🙌🙌🙌🤣🤣🤣
Mmene ankokelamo ndi eliyo zikufana 🤣🤣🤣🤣
Takulandira kachikena ase 😍😍
Koma mandota pano mukumachedwa kutulusa Ife timakusowani bwanji
Aneba mupaka kuchipinda 😂😂😂😂 madota number one
😂😂😂😂...koma munadyad, kapena mwafera uchisamaliya omwwewo...
Ati ndi ma rumours 😂
Thanks
Thanks for gifting us
Umatha ndiye w1
Akita wafa 🤣😂 umakwan @Mandota
Kkkk @Mandota apa nde waku Ana ndi barracks tu
Ati "muntu wankuluuu!!"😂😂😂
😂😂😂😂😂😂Actor amafa dailytu kkkkkkkk we always proud of you
Umukonde neba inde koma mpaka apapa
Mwachiyamba chakachi
Chemwali wa😂😂😂😊 kankhan
Welcome back big
Umakwana doro ndota
U always making my day
😂😂😂ati akadulatu😂 much love mandota ❤
Neba wachibwana😂
2024 imeneyo mandota 😂😂😂😂
Wawo chemandota chachiwatu apikene Ohioo
Ndota squad 💥
Iweyo ndi dolo❤❤❤
Nice chemandota ❤
Good video
People who doesn't understand our language try to translate for them. Che Nandota kip it so bro
Iwe usatela mmanja mwa andu anyway umakwana
Mwasitha ka muzuli kaja😅
Munasowatu iweyo🤪🤪
😂😂😂 I don't want peace
Always i'm so happy with mandota
Neba Kkkkk wangwiro
Umakwana aixe Dolo iwe
Akita omafa every episode 😂😂😂😂😅😅
Umakwana mandota 😂😂😂😂😂😂
Chemandota koma kachisoti munasintha
😂😂😂😂😂😂 umakwana Mandota
Muphe neba😂😂😂
It was so delicious like food🤣🤣🤣🤣🤣 dulani
Bitoni koma katundu mulu😂😂😂😂😂
Zabwino kwambili ndinu nsangalasi
Udzathera mmanja neba che Mandota 😂😂😅
Nice
Iweyo ndi fadahhh
Koma vasala inuyo nde kaya😂😂
Uli bho akita
Welcome 😊
🤣🤣🤣🤣 lnu nde mumafela zaziiii 😅😮
Koma mandota umatha 😂😂😂😂😂😂😂
Ufa kangati
Acita awa amadyatu😂😂
Akita sangawineko kod 😂
😂😂😂 mandota tsopano
Imafunika kankhani iyiyi😂😂
Sumaonesedwa iwe
Matsitha kasuli
❤
Waza mandota
Neba🔥
Mumakwana biggy

Welcome back Big Man.
Wadzatu ndi Moto 😂😂😂😂😂
Keep it up Che Mandota