UKU NDIYE YALAKWA, ANTHU AKUCHILIMBA BLANTYRE ZOMWE ACHITA🙌🙌🙌

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 13 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 583

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 2 місяці тому +9

    Mfiti zopemphera Chakwera ndi mbale wake Usi ndipo anthu inuyo Mulungu akuyendelereni mwapadera ( SKC FOREVER IN OUR HEARTS 💔)

  • @angellah-l8e
    @angellah-l8e 25 днів тому +1

    Powerful prayer,anazolowera sewero kwambiri

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 місяці тому +11

    Inu agaru yehova wake uti,kupusa ziwanda yehova wamoyo sakhala ndimbava akuba akumpha, mulungu azakulangani osapota zopusa ukule garu iwe chairman

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 2 місяці тому +16

    Awus mulibe nselu misimu yah andu 8 yinkukusatilani nkomaso awusseni amalawi ndege yinangwa bwanji osat samanyi munkunenaso mulungu ankuphasani matenda onyassa phamodsi ndi ashankwela mulungu anankuwonani 👌👌👌👌🙏

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 місяці тому +1

      @@esaMoha-dm4kj inu mulungu????

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 2 місяці тому

      @@esaMoha-dm4kj pelepa kuwecheta iseseni. Ambuje Mlungu akunde yakuti uchimbichimbi uyiche kwa mmwejo. Ajaliwe wakulungwa.

    • @BlessingsKatopola
      @BlessingsKatopola 2 місяці тому +1

      Mcp chipan chonunkha kwambiri 😢😢

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 місяці тому

      @@BlessingsKatopola chonunkhila ndichiti???

    • @JamesNgwaya-vz1ox
      @JamesNgwaya-vz1ox 2 місяці тому +1

      Kupha

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 місяці тому +52

    Kodi ngongole imasitha dziko poti mukufuna mwaonjezere anthu mamvuto musise katundu osati ngongole

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley 2 місяці тому +1

      Ndipo live atsitse katundu

    • @CatherineDesire
      @CatherineDesire 2 місяці тому +1

      Ngongole pa campaign aoneke abwino

    • @prettytambala5687
      @prettytambala5687 2 місяці тому +2

      God bless this thinking, ineso wad like why keeping poor malawians in a bandage yangongole mmalo mokaika mankhwala mzipatara, kutsitsa katundu, kuwaonjezera aziphuzitsi ma salaries kuti aliyese azifikira zinthu mosavuta. Izi zikungoperekaso mwayi kwa mbava za m,bomazo kuti ziziba ndalama in the name of kupereka ngongole kwa amalawi mxiiiii

    • @CatherineDesire
      @CatherineDesire 2 місяці тому

      @@JamesChiphwanya-m4v maona Ngati ndi thandidzo angobitsa Chichewa kodi NDI ngongore yangati ya fincca adzaole tidziwiya ,adzatenge timinda NDI tinyumba akalephera kubwedza

    • @Gautengstanzo
      @Gautengstanzo 2 місяці тому

      Zimayamba wez wez, sungapangile zinthu pakamodzi

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd 2 місяці тому +8

    Anthu siyani kaduka.. mulungu simunthu..
    Mulungu anaziwa kale kuti Usi azakhalapo vice president wa dziko la Malawi. Tivomereze chifunilo cha yehova pa dziko lathu la Malawi.

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 2 місяці тому +42

    Sewelo leni leni tikufelanji apapa pangosowa mulelemba

    • @LuundoJohnkabage
      @LuundoJohnkabage 2 місяці тому +2

      😂😂

    • @alicehananiya
      @alicehananiya 2 місяці тому +2

      Eya pakusowatso make sikono ndi winiko

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 2 місяці тому +2

      Dramatising politics .this guy is useless

    • @lucianogeoffrey4275
      @lucianogeoffrey4275 2 місяці тому

      Nde mwati ndinu a UTM? Muzivere chisoni bwana😢😢

    • @WitnessPhiri-zr9uf
      @WitnessPhiri-zr9uf 2 місяці тому

      Nde anthu mukuwona akakupasani ngongolezo mulemela mumene Zinthu zikudulilamu tsiku ndi tsiku ndalama ya ngongole siyingakupindulileni asise zinthu pandalama yanu yochepayo ikupindulilani 😢

  • @fumbomumba5016
    @fumbomumba5016 2 місяці тому +8

    Palibeletu Fundo apa koma A vp awa he's only proud kuti ndi vice president

    • @madakabichi2251
      @madakabichi2251 2 місяці тому +1

      Kape uyu

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba 2 місяці тому

      ​@@madakabichi2251kape umamudziwa koma 😂😂😂😂 mesa kape amakhala osauka ngat iweyo

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 2 місяці тому +3

    Amalawi tichenjere😢 kwambiri. Timva zinthu.lets think and work together.Tiwunikilane. and love each other ❤

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 місяці тому +15

    Mwamchitq bwino munthu wakupha ameneyo angampeleke chilima zoona

    • @Henry-vw2cz
      @Henry-vw2cz 2 місяці тому +1

      Midzimu yakwiya😂😂😂😂😂😂

  • @arthurkayuza
    @arthurkayuza 2 місяці тому +1

    Is that soccer player from chirimba?

  • @geokah78
    @geokah78 2 місяці тому

    We need a system that everyone fine support without being influenced by any political figure. Dr Usi reflect on this.

  • @RachelKamanga-vt3fp
    @RachelKamanga-vt3fp 2 місяці тому

    Ambuye akupaseni moyo wautali me utsi muzina loti musinthe malawi wathu
    Ufumu unasata Daved kuubus chifukwa choti mulungu sakuva zaanthu

  • @KizitoChikuni-dy9us
    @KizitoChikuni-dy9us 2 місяці тому +1

    Akuwa patipo anthuwo yogulisira kut tionere imeneyo? Zopoila

  • @trymhango1509
    @trymhango1509 2 місяці тому +2

    Abale mundiuzireko a vp nzeru alibe chifukwa iwo amayenera asanayambe kulankhura kunkhalakaye cohete ose pasonkhanowo popereka ulemu kwa skc ndikunena zimu wawo uutse mtentere kenako kuwapepesa a malawi zaifa ya chilima kwinako mkumakamba mbwerera zakezo

  • @Edson-sj8vn
    @Edson-sj8vn 2 місяці тому

    Kod m'mene zinthu zilili pansikapa osamba zosisa mitengo ya zinthu bwa? Paja mwakwera muntengo apansife mulibe nafe ntchito

  • @lameckmajiga5426
    @lameckmajiga5426 2 місяці тому +2

    Bwana micle usi athu amakukondani kwambili!! Koma pa game yomwe mukusewela ndichakwelayi athu akutulukani chifukwa azindikila kuti inu muli under M.C.P mukanakhala kuti mukutengapo gawo muma program ama candle 🕯 komanso kuchita zomwe anthu ena a UTM akuchita mukanayenda moyela kwambili komanso zikuwoneka kuti mukufuna kuzutsa chipani chanu cho odya zake alibe mulandu!!! Ife tikanakuvotelani chifukwa cha chilima koma mwaluza basi!!! Pepani bwana usi!!!

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому +6

    Mbuzi iyi ya MCP. Usi usanamize anthu ndiwe wa MCP. Wavala za MCP osati UTM. Ukunamiza ndani nyani iwe. Pamtumbo pako Usiku.

    • @ManganiStanley
      @ManganiStanley 2 місяці тому +1

      Galu kwambiri ndipo akundinyansa kwambiri

    • @omardyman8083
      @omardyman8083 2 місяці тому +1

      Osaiwalatu ndimazimbabwe awaa​@@ManganiStanley

  • @MikeTwaibu-i1h
    @MikeTwaibu-i1h 2 місяці тому +4

    Anthu owopa mulungu ngati abusa a chakwera

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 2 місяці тому +6

    Mizimu ya anthu 13 yayamba kuonesa unya nawo ayise kufupika ngt mchimba

  • @WillyChisale
    @WillyChisale 2 місяці тому +1

    Nde munayenda basi nkumawauza anthu zoti ndinkavala ma kabudula awiri ..zitithandiza chani ngt a Malawi

  • @ElizahMadi
    @ElizahMadi 2 місяці тому +1

    Uyudi ndi manganya srs ,masewero paliponse

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq 2 місяці тому +5

    Ngongole muyambe mwaona tikuyandikila mavoti 4 years munalikuti kuti muwapase ngongole mwabwera nthawi yochedwa inu mwapha chilima nde mukuona kumene ali chilima akusangalala muvutikapo apa panya panu ana anjoka inu

    • @GregoryMatambo
      @GregoryMatambo 2 місяці тому

      Ngongole ilibe nthawi , utha kutenga olo tsiku lovota

    • @prettytambala5687
      @prettytambala5687 2 місяці тому

      You can say this again, anthu tavutika all these years iwowa qnali pheee ,kumangokweza zinthu ndalama akusungira campaign? Rubbish

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq 2 місяці тому

      @@prettytambala5687 eti nde panopa akimalubwa zausilu aba ndalama za amalawi ena agwidwa nazo zana

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq 2 місяці тому

      @@GregoryMatambo khalani ndi umunthu inu nde ubwino wakuba ndalama ndi uti? Mesa kumangophelatu dziko chithyola anamupeza nazo zana president nkumati musiyeni azipita what doesn't mean you're rubbish

  • @ClezinaChimala
    @ClezinaChimala 17 днів тому

    Osamatenga amphawi kuwaika pa udindo amangofuna kuba kt athane ndi umphawi wawo

  • @LovenessShugar
    @LovenessShugar Місяць тому

    Ine ndikufuna Dr usi ife tikufuna thandizo lawo ngongole atipase

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd 2 місяці тому +4

    Ndiye kukuwa mwalemba pa munthu wa nkhanipo akuwa pati reporter wa bodza iwe

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba 2 місяці тому

      😂😂😂😂 😂😂😂 always cadet amatero mix mizimu yama albino

  • @YatoRoy-kt4lh
    @YatoRoy-kt4lh 2 місяці тому +4

    The guy has a good heart

  • @Sophiejphiri
    @Sophiejphiri 2 місяці тому

    Mau onveka bwino avp anthu my God bless u, ndili pambuyo panopa maka pankhani yangongoleyo, odya zake alibe mulandu

  • @martinndawala8125
    @martinndawala8125 2 місяці тому

    Kodi Bwanausi ndi Bwanaisa mpachibale?

  • @KanthuSankalah
    @KanthuSankalah 2 місяці тому +4

    Blantyre inachulukadi mbuzi,am from by city koma delali ndi la nkhumba basi

    • @GeraldChisamba
      @GeraldChisamba 2 місяці тому

      Munachuluka amoya 😂😂😂😂

  • @JenniferFyson
    @JenniferFyson 2 місяці тому +3

    Powerful prayer 🙏

  • @RatifMakiyi
    @RatifMakiyi Місяць тому

    Usi Khala serious ukulongosola zithu zisamveka kutundu wa malawi

  • @rhodrickmpumila1820
    @rhodrickmpumila1820 2 місяці тому +1

    Ndiye amuwowoza patipo tikusikatu mboli yako

  • @patesnkajenda4258
    @patesnkajenda4258 2 місяці тому +2

    Fundo palibe bwana ingodyelanitu basssssss😂😂😂😂😂😂

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 місяці тому +3

    *wayankhulapotu .. Koma ndege inagwa chifukwa chani bwana*??

  • @NancyNyirenda-v9o
    @NancyNyirenda-v9o 2 місяці тому +5

    Inuso ndinu a boza pena nanga akuwa pati apa chimutima cha nyawu icho

  • @JumaGadaff
    @JumaGadaff 2 місяці тому +6

    Mwayankhula bwana koma ndege inagwa bwanji boss 😂inuyo bwana ndinu opanda mnzelu mulungu akukantheni chisanathe chaka muyankha mulandu

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq 2 місяці тому

      Umayankhula bho heavy

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 місяці тому

      @@JumaGadaff kafuseni mulungu kuti ndege inagwa bwanji chifukwa ndamene amadziwa chilichose

    • @IanChidothe
      @IanChidothe 2 місяці тому

      Ndipo akudziwapo kanthu uyu

  • @ShepherdChisale
    @ShepherdChisale 2 місяці тому

    Musamatichotse feel nanu......penapake muzingodula pofunikila pokhapo.
    Ma Bandle akuvuta kale awa😢😢😢😢

  • @EmmanuelstoneyJere
    @EmmanuelstoneyJere 2 місяці тому +1

    Olo opepherayo akuona ngati akupanga sewero ndi manganya

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 2 місяці тому

    Zaka 4 zimenezi zinalikuti ?

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 місяці тому

    Zopepela zakozo osamantchula mulungu ukuwona ngati mulungu ndiwosewela naye

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 2 місяці тому +9

    Amalawi chonde osayelekeza kuvotela izi

  • @rasnocuss4183
    @rasnocuss4183 2 місяці тому

    Chirimba one love!!!!!🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤🎉 mwana wapaden Manganya

  • @mwaisulaimana
    @mwaisulaimana 2 місяці тому +2

    Koma this man, alindinzeru kwabasi. Amandisutha kwabasi

  • @WedsonZuzewatayamakina-rn8yp
    @WedsonZuzewatayamakina-rn8yp 2 місяці тому +4

    Ndiye mwati chani😂😂😂😂 ine sindinatolepo mfundo atah olo pang'ono

  • @alfredbamusi1093
    @alfredbamusi1093 2 місяці тому

    Ndi ntchito yabwino kuti akuzipanga available to the public anthu apempha ngongole kuti upange boost capital chomwe ndi chabwino koma zimafunika kuti ayambile kukonza moyo wa ma customer amene ali anthu ogwila ntchito m'boma ndinso ma labour onse azipasidwa ma salaries omwe atazipanga match kukwera kwa mitengo ya zinthu omwe ndi ma buyer ama businesses amene akuvuta kupita pa tsogolo

  • @AnockyDavidd
    @AnockyDavidd 2 місяці тому

    Seweloli kodi ndilapamajiga?

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 2 місяці тому +1

    Musanayambe kukamba zasewerozo mutatiyankhako kaye funso likumatisowesa mtendereri, Kodi ndege inayenda bwanji ku chikangawa? Zangongole zanuzo ifeyo ayi, munali kuti ndi chakwera wanuyo? Nkhani ndikusisa katundu, zinazo mukakambirane ku state house

    • @AbdulhameedWyson
      @AbdulhameedWyson 2 місяці тому

      Chisilu iwe

    • @DeliaKaduya
      @DeliaKaduya 2 місяці тому

      @@AbdulhameedWyson tangopita ukalandire nawo ngongoleyo munthu iwe

  • @LiyayaNyamula-j3b
    @LiyayaNyamula-j3b 2 місяці тому +1

    Fundo pa line katundu anali azanu anja inu ndi achimulilenji sakusiyan

  • @GIFTEDWARDCHIGUMULA
    @GIFTEDWARDCHIGUMULA 2 місяці тому

    MP wachinyamata and chi player mbambande🤜🤜🤜, msikawo akonzedi eee

  • @johnman4619
    @johnman4619 2 місяці тому

    Ndiumenewotu u .vice president.munkaufunauja mpaka kupherapu nzanu chilima tiyeni nawoni mulibe ngakhale thenthi lomwe

  • @lawrencekayona9247
    @lawrencekayona9247 2 місяці тому

    Ndinaonela atapanga comedy as a president of the republic of Malawi lelo izo

  • @randettaclaan
    @randettaclaan 2 місяці тому +4

    Kodi Dr. Micheal Usi ndiu wa DPP kapena wa UTM///////////////// Nanga slogun ya woyeee ndi ya UTM

  • @Gautengstanzo
    @Gautengstanzo 2 місяці тому

    Zimayamba wez wez am sure manganya akonza zinthu, very soon katundu atsikaso

  • @FrankMasamba-uk6mc
    @FrankMasamba-uk6mc 2 місяці тому +1

    Iweyo Usi ukamalankhula kumatchula dzina la chakwela , panyapako kwambir

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 2 місяці тому

      😂😂😂😂😂😂😂akutopetsadi bwanji ameneyu

  • @HarrisMathew-ve5ib
    @HarrisMathew-ve5ib 2 місяці тому +2

    Akuti kukhalatu ma Team ampira uku 😂 😂

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873 2 місяці тому +2

    A chairman wo akalamba😂😂😂

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 25 днів тому

    Palibe chanzelu ndamvapo apo ...manganya akupanga za chakwera mbuzi ya munthu

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx 2 місяці тому

    Am still feeling sorry for my country.
    We seem to be a cursed nation.
    Tikungoyang'anira 2025 mwina tizawona madakiso

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem 2 місяці тому

    Zamakabudula akowo anthu apindula nazo chani pomwe anthu akugona ndinjala. Dzuno pamenepo panali ena lelo ndiwe ndipo mawa ndi ena samala osatenga Malawi kusowa zochita.

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 місяці тому

    Pamene ukulankhurapo nzimu wa achilima ukukantha ñdkuuuza, km Malawi ndinu anthu omvesa chison kwambiri kd mcp ndi chipan chochitsatira anthu akupha

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l 2 місяці тому

    Iiiii ausi kuendatu kuposa malemu iiiii agwilizana zichani ndi chakwela aah Anthu-wa ndi amozi sure akuziwana

  • @earnestchapita2194
    @earnestchapita2194 2 місяці тому

    Nanga bwanji asilikari sadaseke maso popemphera bwanji

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 2 місяці тому

    Bambo asikono ife sitikufuna ngongole ai, coz ngongole yo ndiye mavuto oooopsa Kwa ana anthu. Koma pangani zoti zinthu zisike pansinka kuti aliyese athe kufikira mtengo wakatundu osiyana siyana emwe mtengo wake wachita kuopsa ngati muja uchitila mkango

  • @FrankHaruni
    @FrankHaruni 2 місяці тому

    Akuluwa alindifundo dxopusa kobasi adximuudxa Chakwela dxoti mulungu simuthu amasithadi kom osati kwaife ndiwe galu kobasi

  • @UsenLashid
    @UsenLashid 2 місяці тому +1

    Tengani ndalamazo or musazabweze Ayi ndi misonkho anu atuzuza thawi yayitali tengani zaulere

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn 2 місяці тому

    Zaziiiiiii zopanda mntchele masewelo

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 2 місяці тому

    It's so sad to see Malawian are still fooled by MCP.what a hell

  • @InnocentSteven-k3y
    @InnocentSteven-k3y 2 місяці тому

    Munthu ukamangitse okusakira mtchele

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 місяці тому

    Zomwe akulimbana nazo athu awa zaziiii, noe mukuyenera kutsitsa zithu mtego komaso mudziwe kt kugwa kwandarama yathu yakwacha mukuyenera kuganiza kwambili mukapanda kutelo zithu zizativuta mpakana kale

    • @JaneMhango-zl6pt
      @JaneMhango-zl6pt 2 місяці тому

      Kujaila kungongola ndiye mulephere kubweza ndalamazo.
      Dziko la malawi latha ili. Ma president ake ndi akuba onse.

  • @elbeys783
    @elbeys783 2 місяці тому

    Awaso nde ayi, athu akuvutika osamuuza za umphawi wanu muli ndalama osamatipusitsa

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 2 місяці тому

    Ndikuon ngat Anthu anu okuthandiziran sadakuthandizen
    Kungokhal ngat sewer sinthan okuthandiziranio

  • @TSAMBASOmex
    @TSAMBASOmex Місяць тому

    Powerful boss

  • @vincentkhunsanama584
    @vincentkhunsanama584 2 місяці тому

    Ngongole mumupatse munthu ogulitsa zitumbuwa mwati

  • @KestenMukhwapa-qp2gj
    @KestenMukhwapa-qp2gj 2 місяці тому

    Za ziii zeni zeni zopanda ndi Schererville womwe

  • @SagNuran
    @SagNuran 2 місяці тому

    Amalawi azanga Pena mukamalakhula muziganiza osamangokamba zithu zopanda umboni musiyeni usi ndi thawi Yake iyi yakwana

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 місяці тому

    Ndiyeno gulu lose ilo nkumayimba / nkuyankha anthu 5 , manyanzi bwanji usi pamenepo.
    Komanso ndi ana akuyakha usi

  • @umboneyusufu4499
    @umboneyusufu4499 2 місяці тому

    Aka manganya ngati adalephela mayeso awumphunzitsa nde lelo angatukule Malawi

  • @NenaniMwamadi
    @NenaniMwamadi 2 місяці тому +2

    Zasewerooo bas usiì

  • @LovenessLester
    @LovenessLester 2 місяці тому

    Ndrama yangongoleyo ipititseni Kuchimanga ndi feteleza kuti zitsike mtengo chooooooondeeeeee a VP

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 2 місяці тому

    Malawi 🇲🇼 dziko lovetsa chisoni kwabasi 😢😢😢😢

  • @JonesBenNgaiyaye
    @JonesBenNgaiyaye 2 місяці тому

    Cheptsani mapemphero otamanda munthu mmalo motanda Mulungu mwini zonse wa kumwamba chonde imvani chimenechi

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 2 місяці тому +1

    Tamangodyani ndalamazo bas,uku tikudikira report la kuchikangawa,koyenda ndege ma hours 3800, ngati imayenda wapansi

  • @SolomonMatola
    @SolomonMatola 2 місяці тому

    Mmalo moti asise zinthu ziko lonse aaa koma mr vc presdent mwaganiza bwanji poti ngongolezo ziziaonjezera mavuto mmalo mopita chisogole azibwedzanso zinthu mmene zakwereramo aaa

  • @Demndovie-x2v
    @Demndovie-x2v 2 місяці тому

    Pepani amalawi dziko ndiutsogoleliwathu ndi wa sewelo musiiletu kulakhula zopusa asogoleni mukuendela galimoto komanso mafuta ,zogulandi ndalama misokho a osauka manyazi mulibe mbuzi

  • @LucyTatianahChikwekwe
    @LucyTatianahChikwekwe 2 місяці тому

    Usi mu ma speech akewa mmmm chikondi chikupelewera bwenzi ali mu chisoni 🙏

  • @WilliamChirambo-cp5dl
    @WilliamChirambo-cp5dl 2 місяці тому

    Zamasiye ndizovuta muonekera ng'amba

  • @mustafakanfosi6916
    @mustafakanfosi6916 2 місяці тому

    Landirani ndalama zathu zimenezo. No need to pay back.

  • @KestenMukhwapa-qp2gj
    @KestenMukhwapa-qp2gj 2 місяці тому

    Ndangotaya nthawi yanga kumvesera zopusazo manganya munthu wankhaza uyu

  • @Tilipo-r4p
    @Tilipo-r4p 2 місяці тому

    Fundo ikuvuta pafunika azipita pa point first osati kudzifotokoza Za mmbuyo mwawo ....komanso kukamba Za chipani chawo or ofunika mulangizi adziwauza zokamba ku mtundu waanthu

  • @FrancisMazamba
    @FrancisMazamba 2 місяці тому

    Vmufiti lyi yinapeleka mzake

  • @priscan6389
    @priscan6389 2 місяці тому

    Nkhani ndiyoti osamacheza ndi Mulungu.

  • @MarthaJafali
    @MarthaJafali 2 місяці тому

    Anthu a ku Blantyre mulibe so nzeru mpaka mkumati woyela

  • @MexcoJepter-p5f
    @MexcoJepter-p5f 2 місяці тому

    Mudakakhala ena mukadamati tikutsika katundu amalawi akadamvako bwino koma zangongolezo ndikuwawonjezera umphawi

  • @RhodaBandah-sh1ir
    @RhodaBandah-sh1ir 2 місяці тому

    Ngongole sisitha zithu bwana ..mungowawonjezela mavuto
    Kasiseni zithu kuma shop full stop

  • @LuciusChitseko
    @LuciusChitseko 23 дні тому

    Aaaaaa zaziiii atikwanatu uyuu

  • @SamuelMthengo
    @SamuelMthengo 2 місяці тому

    Slogan imeneyi siya utm,ok asanditayitse nthawi.

  • @SylvesterMoyowinah
    @SylvesterMoyowinah 2 місяці тому

    Kodi muli pa campaign 😢😢 kodi

  • @JamesIngeni-ku3qj
    @JamesIngeni-ku3qj 2 місяці тому

    Ndipo ngongolezo 4 yrs ago zinali kut mungonena kut mukugawa ndalama zakapeni.

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt 2 місяці тому

    Mutsitse mitengo yakatundu osat ngongolezo .....kod ngongolezo atapindule ndangat ? .....pangan zot athu ovutika apindulenao osat zangongolezo