Che mandota I like the way u have acted this episode.... Waphunzitsa anthu ambiri kuti mu limbe azikhala ochenjera even if munthu sunapiteko ku limbe ukhala ukudziwa kuti kuli okuba .... Komanso anthu omwe amachita mchitidwe obela anzawo atengelapo phunziro kuti akupangazo siku lina azaona polekera ..coz zinthu zikuvuta aliyense nde solution isamakhale kubelana keep it up u deserve masso award
www.maso-awards.live/category/best-comedian
Zatheka
You got my vote 💪 continue being a blessing to others
Umakwana mandota
U are the Tru Talented G .... We konda you to the Max...
Tafota zateka che mandota
Che mandota is the best comedian in malawi who is with me
I'm with you
As a matter of fact 😂
Most definitely 😂😂😂😂
Umatha ase ulemu wako
We are together
Iweyo mumata mazo awad tatenga nditutu mwaona ,mwaona❤❤❤
Wow that's great on our way okatengaso award yathu loweruka lino❤️🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
0:23
Our own doctor che mandota, keep the fire burning.olo patient amanva bwino
Chemandota is better than DStv 😂
Kodi mumalemera ma KG angati Chemendota😂😂😂😂😂😂
Chifukwatu anthuwa amangokunyamulani2😂😂😂😂😂😂
Tili pambuyo Pako mandota,my best comedian in Malawi,umakwana
Thanks brother
Owina wina kale bafo
I'm a comedian and I wish to be followed by you ❤️
Che mandota I like the way u have acted this episode.... Waphunzitsa anthu ambiri kuti mu limbe azikhala ochenjera even if munthu sunapiteko ku limbe ukhala ukudziwa kuti kuli okuba .... Komanso anthu omwe amachita mchitidwe obela anzawo atengelapo phunziro kuti akupangazo siku lina azaona polekera ..coz zinthu zikuvuta aliyense nde solution isamakhale kubelana keep it up u deserve masso award
Mu limbe amwene eeee
Mandota iwe ndi 1 maso award mwatenga basi😂😂
Indeed limbe sisunga kape anandilizapo ine
Zowona zokha zokha, ine mu Limbe momo anandibera 50 thousand njira yake yomweyo.
Talirapo ambiri mu limbe,18k yanga inapita, inspired 🇲🇼 pa top ndi che Mandota umaphu zitsa ase koma sechedwa kufaaa kkkkkkk
😢😮😮😮
Yes this video is very educative do more of this type Bro more fire, umatha
😂😂😂😂 napangidwapo ndili mwana ku chilomoni BT, 🤣🤣🤣
This comedy is massive 🔥👏
Brilliant 👏
Mumatimvetsa kukoma, go ahead
😂😂😂😂😂 ndibwere kodi kkkkk n yothawira mbasada.....umakwana king of comedian
❤️❤️❤️ iwe mandota kkkkkk kuti kweeeee......
Yaaaaa umathadi mr watching from Durban South Africa ❤
Yophunzitsa kwambiri,kuno ku Zimbabwe timakondwera
Kkkkk sopano mologeni alikt apa zikukuonekera wekha nzanga
Iwe pa dolo unadutsa pano ndiwe dololo 😂😂
Akita omangofa daily 😂😂🙌🙌.. umakwana🎉
Akitatu wake daily maliro...koma adah awawa nkhani Zina amatha comedy 🤣 😆 😄 😂 😀
🎉
Kkkkkkkkkkk Palipose mbasada sizimuthera bwino
Our way to take MASO award again motsatiznana 😂😂😂😂😂😂😂 munthu wamkulu walila jumbo ya bulaki muli ma pepala
Bola musatiphuzitse kubaaaa asaaaaaaa ndiwe dolo
Hahaha osatiphunzitsa kubatu koma 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂 muyao osamba
Mandata umakwana ethi kkkk kubera poison akuwona 😂naye mologere ndiye kungotawa wozanena 😂😂😂mandota my vote 🎉🎉🎉🎉
Machine opangira machine azake
Big man mudzathera mmanja mwa anthu Inu adzangokuyatsan kkkkkkkkk❤❤❤❤❤ iweyo ndi mbambande taphunzra zaku limbe
Kkķkkkķ🤣🤣🤣🤣🤣🤣 anandipangapo izi mavenda kundigulisa chitenje chimodzi mtengo waziwiri kukazindikira ndafika kunyumba 😁
Kod award tikatenga litro kodi
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma ndaseka iih inuyo ndi one as a matter of fact
Tiyeni tikatengeso awars ija Saturday
Comedian obhebha 🔥🔥
Achiyaofe mmatiyimilila big up mandox
As a matter of fact kuthawa kumeneko hahahah😅
Umakwan chemandot😅😅❤❤❤❤
Che Mandota ndi dolo ndipo Limbe akuiziwadi bho. 😄😄
Chemandota zatiphunzitsa kwambiri zikomo kwambiri
Sho
Mbazada 😂😂 deserve award
Doro kwambiri ❤
Ndiye sumavuta kunyamulatu kkkkkkkkkk
Iweo ndi dolo Ndoxy❤
True story
Inuyo ndi one mwene
Azichenjera pa town pamenepo
Mandota waonjeza
limbe eee anakonzad 😂😁
Akulu akulu apatu akita wafa!!! Kkkkkkkk km yaaaaaa wiki yamawaso mudzafe kkkkkkkk ndiye ufa kangt panotu epsode iliyonse ukungofa, mumakwana mandota anakupatsani moyo wautali okufa mkumadzukaso pakangotha wk imodxi
Che mandota wayamba kubwela anthu 😂😂😂
Moni apereka kale kkkkk aze matalà ofu fakiti
Mumakwana malume 😅😅😅😅
Mu limbe anganga
Such talented
Ine kuba angakhale ndaniso kuposa inuyo
😂😂😂😂😂😂 Mologeni wathawa yekha
mupange pa muthu oti dziko lavuta
Fire
Kkkkkkk koma che mandota kkk sazatheka
Ulibbb elias mozambiqui
Leicester city😮😮👏👏
Mbazada! Iyiyi ndi mazitapizi mwaona!!🤩
😅😅😅 machine
Chemandita amalemela 11kg tu😂😂😂😂
Mumakwana anyamata
Ndine sam from BG adala mumakwana inu kkkkk
😂😂😂umakwana chemandota ndi crew yako
kubwera ndi thumba lapathako,koma popita sukhala nalo thumbalo
As matter of fact zi azibambo okha okha
Mmmm inenso ndinabeledwa ndi kukaoda zitenje mandota umaitha aise
Odi ndiyambe ku commenter 😅😅😅
Mumakwana inuyo chemandota
A ward tikutenga iyi✊✊
Day maker😅😅 keep it up
Limbe anakonza
Kkkkk apapa wafa basi
Musatiphuxisetu kuba bro
Mandota nd doro!!!
Someone to tell me how did he exchange 😂😂😂
School days
Award ndi ya Doctor 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Mumatha wakulu mutivetsa ukoma
Limbe ndiyachabe heavyy😂😂
Watenga kale awadi ase osadanda
11:47
Kkkk km iweyo ase umakwana tu kkk
Kkkk bwana mandota udolo mlope nambo apa umasire😂😂😂
akulu akulu, apa nde akita wafa
No matter fact kkkk kuyiwonera patali kkkkkkk Koma wathawa
Iweyo udzathera mmanja mwa anthu
Mu Limbe mulibe dolo
Ndipo palibeso mandota😂😂❤
Mumativetsa kukoma