😅😅😅😅😊 Koma ndoxy iweyo ndi khani zina 😅😅😅 ndaseka mpaka mimba kupweteka.... Besides that i get good advice and it's true that some people are pretending to be deaf yet they are able to hear... Nde naweso ndoxy aise ukukulaso mtima kufuna kuyambitsa ndewuu kkkk😮😮😮😮😮 Ma maili ali pamavuto ndithuuu 😅😅😅😅 Ndimakunyadiran guys keep up
Whenever I feel low and depressed,I watch your comedy and booooooom my day brightens up,more love and respect for you bwana Che Mandota from Zambia 🇿🇲 Inu mumakwana basi
Love this one.....mtaunimu aaa zaonjeza. Kuvuta kusiyanitsa kuti ovutika weniweni akufuna chithandizo ndi UTI. Keep up the good work!
😂😂😂😂😂😂😂Atiii ndimalankhula chilungamo kuti andipase yonse, Mesa madam amanena kuti mungondipasa yonse😂😂😂
Che mandota😂😂😂this is the best video you have ever made.... I can't stop laughing 😂😂😂😂😂
Mwana wakwathu umayitha ndipo ku malawi sindikuwona actor amene angapikitsane nawe....... Mandita squad
Creativity at its best... This is great👌👌🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Chilungamo chiyende ngati mazi. 20 pin igwe basi. Kkkkk
Osokonesa ndi olembayo🤪
Iwe man ukonze macamera yakoyo simawoneka bhoo sithuzi izo
I like kankhani's seriousness 😂😂😂
Mandota waonjeza km kankhani akupha apa ndiye wapsya mtima waona mene achosera cholembedwacho
Wachiyao pure ❤ still watching
Chemandota love you simatikhumudwitsa 🤣🤣🤣
Hahaha mpaka kuyamba kubweza moto kkkk chemandota😅😅
Continue Mr I like
Izi ndi zoona ,zikumavuta town kt uzindikile ovutika en en
Kkkkkkkkkkk,akt akulu osamakala ndi moyo wokhomerera ai,udadza iweyo!
Nice video
Mayooo osayankhura wagwida kaamba ka ndalama, ndalama ndi satana walayi
Sumakhumudwitsa mwene
Good work, mbazada ndoxy,, akangani! Musampase ndimpasa 😂😂
NdImafunisisa top yojambul mandota ndiNGAIPEZE BWANJ GUYS
Timagulitsa......Timvane uku....0999374695 WhatsApp
Mmakwana guys.koma aKankhani lero ndinakumana ndiwina Wake ofanana ndiinu alimujez yaPolice ulemu wanu
Ndi yemweyo
Eeh koma ndasekaaa😂😂😂
Ichichi mutu wake sugwira ndithuudi
😂😂😂
Mandota comedy nonse ndiakatakwe pitilizani kuphunzitsa moto kuti buuuu!!!!!!! Alesi nonse samalani yambani kufuna maganyu kuopa kuyaluka
Tiwonere zmenezo ,,, umatha iwe Mandota
Very fine
ase mandota kudekhatu kwakuvuta pamenepa
Osalankhula osamva wamva ndipo walankhula 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chemandota ineyo ndipatse number ya kankhani ndimuone kena kake nkulu uyuy amandiwaza kwambili
Mchosa ma stress pa Malawi nde mandota after pa Izeck and Jacob
Kkkkkkkkkkk mundu wankhulu mandota
Ine ndilibe nanu mau Che Mandoa your are the best
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣. Mandota ase
Koma ma mayili ndiye awonda2
Ndotaxy suzatheka basi😂😂😂😂😂😂
Mbambande comedy very edecative
Good one
Mandota kuno amudulira mpamba😂😂😂Koma ma Maili ati ukadya konkotu .
Kkkk kma eee ache kupeza Yonjera after a wife kukukanilan kudy panden
You never disappoint mandota😂🔥
😂😂😂koma guys😂good work guys keep it up
Mumakwana my brother
You said, "this talent from home Machinga"?🤣😂😂😂 Iwe ndi dolo bas🙌🙌🙌
Umakwana che mandota ukutivesa kukoma
Kuphunzitsa 😊
Kushemangamba umatha weo my limodelo
😀😀😀 mandota iwe ndi 1 umakwana 🙏🙏🤣
GOAT
Kkkkkkkkkk koma guys kumangamba ndilibe Nako mawu
Sorry boss km atleast mwapezako yandiwo much love you guys
Iweyo ndinuu bigiri man
Uopyedza Munthu otandiza mandota wapepela
So munauza kuti alembe osaona iiiii kkkkkkkkkkkkkk km I love 😍 u
Che mandota I loves u😂😂😂
😅😅😅😅😊 Koma ndoxy iweyo ndi khani zina 😅😅😅 ndaseka mpaka mimba kupweteka....
Besides that i get good advice and it's true that some people are pretending to be deaf yet they are able to hear...
Nde naweso ndoxy aise ukukulaso mtima kufuna kuyambitsa ndewuu kkkk😮😮😮😮😮
Ma maili ali pamavuto ndithuuu 😅😅😅😅
Ndimakunyadiran guys keep up
Koma mandota ma dilu iiiiii 😂😂😂😂
Zowonad anthu opephawa akuonjeza ulemu wanu chemandota
this one was GOATed 😀😀😀😀😀
🔥🔥🔥🔥Mandota ine pambuyo pako😂
Ahhh😂😂😂Umakwana iweo aseh
hahaha mavuto awawa ngowaputa
ndakomoka ndikuseka
Kkkkkkk koma guys muchenjere bwino ❣️❣️❣️
🤣🤣🤣🤣🤣wanena wanena axe Dolla apeleke bas
Anakoza km iweyo✊✊✊
😂😂😂😂Koma Mandota ase
Mandota umakwana 😂😂😂
😆😆😆😆😂🤣🤣 mission impossible
Talented
Kkkkkk kma yaah Kuva 20pin kuyakhula a Chee kkk kma mumatiyimilira
😂😂abwana kufuna kuwabera anthu
😂🤣😂 wow
Ilibwino
🎉🎉🎉🎉🎉🎉
M'malo modenkha nawo amandota😂😂😂😂😂
Zina ndi mwamuna eeh Koma awa
Akita wafa apa😂😂😂
Nice
Zili boo
Iweyo ndi ndoxy di🤣🤣🤣🤣
ayamba kufupika macomerd mandota
Mumakwana brother mandota
Whenever I feel low and depressed,I watch your comedy and booooooom my day brightens up,more love and respect for you bwana Che Mandota from Zambia 🇿🇲
Inu mumakwana basi
😂😂😂😂 bro sipanayende😂😂😂😂
Kwabasi 😂😂
Kkkkkkkkk koma maluzi amenewa
Mandota koma 😂😂😂
Akuti ana andimvera kuti sindikuchita kalikonse kkkkkkk koma
Che Mandota ur the best
Akita wafvwa😂😂😂😂😂😂😂udzatipha iwe😂😂😂
Ndipo live 🔥🔥
Koma chemandota nkhani sizimakutherani kkkkkk, deaf and dumb😊
😂😂😂😂😂 Mandota
😂😂😂😂😂 kma mandota 😅😅😅
Mudzionjezelako thawi ambasada
Ili bho heavy kkkkkkkkkkkkkkkkk
Koma nde ndaseka🤣🤣🤣
Kkkkkkkkk mandota nd 1👐😂😂😂
Big up bro nice one
Umatha heavy
Ndoxy ndi dolo 😂😂😂🔥🔥
Che mandota timangolandira bas😂😂😂😂
😂😂😂😂 kkkkk kma iweyo adah
Koma mandotaaaaa 😂😂😂😂😂😂
Big up mandota😂😂😂😂