The DC aaa aganidza dzokhala ngati bakili muluzi TV tsonotu dzonena zake timadziziwa ndimayetsa amati wabodzo lelo nde akanena iwowo nde anthu adzikhulupila komadi chitseko chapani dzedi a MCP
Dzulo ndanena kuti uyuyu si wa bakili muluzi, page iyiyi si yake chifukwa wa bakili muluzi sanganene zimene zija ai, DC ndi zache weni×2 wa bakili muluzi tv nduyu akunenanso kuti si wa bakili muluzi anthu ndi propaganda ndipo ndizoona chifukwa iwowo amalankhulana dairy ndipo awuzana kuti siye koma anyamata a mcp inenso ndinadziwa kuti ndi propaganda koma ojiya amenewo apezeka chifukwa naenso wa BM tv anafa kwambiri. Mcp kudzangobela mavoti ndidzakhala nawo mmodzi oyambitsa dziwawa mmalawi muno chifukwa ndikudziwa kuti sidzawina nde wina adzanene kuti cikangawa wawina kunena kwa DC kudzacitika zoti cikangawa sanadziwone cibadwileni yelekezani muone.
Mwana woooooPsyaaaaaaa kwambiri... The DC..God bless u
Let's Malawian give chance mnyamata mzathu Denis Mahata. The political philosophy
He is telling the truth, Malawian people are suffering. I assume they are the worst in SADC
The DC🎉🎉🎉
The DC Boooon Kalindo president wa aphawi Malawi 🔥🔥🔥🥳🥳🥳🥳🎉🥳🎉❤❤❤❤
Thanks u bon kalindo
Kuziko lamalawi ngati kuli muthu Ozawa Maputo acanthu ndi bon kalindo bas
Chakwera must gracefully step down he has failed the people of Malawi
Anthu akubaa a MC P .
Mutha kwakumbutsaso
Nkhani ya resignation ljah. Kutheka aniwara
The DC 🔥🔥
More fire
Azoooonad mr kalindo
Thank mr born kalindo
MCP olo itapanga chani ife sitikuivotela yatinyasa kwambili
The DC Mr president for poor people l like u
Very true Mr Kalindo
Pa ground sipalibwino chilichonse Chakwera magaye.
Kumawakwapula kumene The DC osawanyengerera😂😂😂
Mr born kalindo ,awa mukut avitumbiko Mwenda akupanga izi chifukwa chot zisankho zayandikir ,paka 4yrs yapitayo ankapanga chat,
😂😂😂😂😂😂😂 chalakwe zamvuta kwambiri ndipo the DC mulungu azikutetezani kwambiri ifeyo sitikhara chete pokha pokha APM alowe boma basi 1 samueli 16:1:10 yesaya 54:17
DC we love yu
Ipanseni moto 🔥🔥🔥
The DC umatha
Ummmmmmmmmmmmm page ya Bakili TV sinapangidwe hack
UTM ndiyakubad Chilima sanali wabwino olo pang'ono. Zonsezi ndi zoonad
Atupele Muluzi my Vote
osaopa the Dc 🔥🔥
🙏🙏🙏🙏
The Dc 🎉🎉🎉🎉
Unasowa kalindo ndatchera khutu kt ndinvesere zomwe wanyamuka ❤❤❤❤
Bakili muluzi TV hacked guys
Kalindo mukumenya nkhondo kwa osaukafe..No more mcp in 2025
The DC ❤
❤
Kodi a DC UTM simuitchula bwanji?
Tiziti aimuuidziwa😂😢😅
Chakwera is the worst president Malawi has seen. Munakwera stikani
DC zowona
Tinakusowanidi bige masiku a menewa bola apa mtima wakhazikika,ofunika anduna azaumoyo ayendere kuno kunancholi Blantyre,chipatala chakwa komka chomwe anachitsekula kumene chija madotolo akumabwera mochedwa kuntchito npaka 9 o'clock asanabwere anthu kumalandira thandizo mochedwa ayi sizowona,zikumatiwawa ngati ifeyo amasikini,sizowona mutiyankhulire bwana DC kwa anduna azaumoyowo nkhaniyi
Mwana wowopsa kwambiri
Kuno Kulilongwe kwawo kwachakwera tikumaphikila mafuta odzola akomba. Mafuta ophikila olo amukakondomu adhula.
Ndipo ku Tanzania nkotukukaditu
Ine ndiye ndili pa mbuyo pa Denis mahata
The DC ndinadabwa kwa two days kut simukutulusa odio takunyadiran kuti mwatifikilaso the DC mulungu akuonjezelen mphavu kwambiri
The DC aaa aganidza dzokhala ngati bakili muluzi TV tsonotu dzonena zake timadziziwa ndimayetsa amati wabodzo lelo nde akanena iwowo nde anthu adzikhulupila komadi chitseko chapani dzedi a MCP
Za chimangazo olo kubalaka anthu akupulumukira ku andiamo kumene anthu akugula chimanga chamankhwala choyenera kuti chikazalidwe Malawi waola uyu ambuye atithandize
Kodi umasintha chiyani ukamatele bwaji iwe.ossakoza😅😅😅😅😅😅😅😅
Ulemuwako the DC
Yah ine ndi mzika ya kwa manjeko ndipo izo zikuchitika chimanga cha mbeu chapent ya green ndichomwe chikusukidwa kupangidea nsima zilikuno Kwa manje
Ijayi si bakili muluzi TV. Fake tinayiona kale
kaye boma la nsanje athu akuvutika kwambir chakudya kulibe anthu akusowa pogona Malawi dziko lomvetsa chisoni
Tiyankhuleni boss
Inetu ndimadziwa kut imene ija sibakili muluzi tv ayi koma alibe mtendere
Ndi bakili muluzi tv
❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
tiyeni tingomuza Kut achoke Mesa tikuva kuwawa ndifeyo
Chakwera masiku ako ndiowerengeka
Ife timaziwa kuti wa bakili sanganyonze UTM
Ine ndimadziwaso
@@ElizabethMulindesikunyoza koma chilungamo 🎉🎉😂
❤❤❤❤
Dzulo ndanena kuti uyuyu si wa bakili muluzi, page iyiyi si yake chifukwa wa bakili muluzi sanganene zimene zija ai, DC ndi zache weni×2 wa bakili muluzi tv nduyu akunenanso kuti si wa bakili muluzi anthu ndi propaganda ndipo ndizoona chifukwa iwowo amalankhulana dairy ndipo awuzana kuti siye koma anyamata a mcp inenso ndinadziwa kuti ndi propaganda koma ojiya amenewo apezeka chifukwa naenso wa BM tv anafa kwambiri. Mcp kudzangobela mavoti ndidzakhala nawo mmodzi oyambitsa dziwawa mmalawi muno chifukwa ndikudziwa kuti sidzawina nde wina adzanene kuti cikangawa wawina kunena kwa DC kudzacitika zoti cikangawa sanadziwone cibadwileni yelekezani muone.
Ilili ndi bodza kalindo page sinapangdwe hack ndi iyeyo osanamiza anthu apa
Wanvako za Bakili TV
Iweyo ndi azko ndi amene anapangsa
Zaziiiiiiiiiiiii
Zaziii ndizanuzo anthu osakonda dziko lanu inu
Mazilako ase wamva usamale kwambr 💪
Kamwe nchape
Iwe pamtumbo pako ndi mtundu wakwanu onse wava
❤❤❤❤❤