Times Television can do better on other programs like Hot Current. Not this stupid program with Samuel Kalimila ndi Hure. Let Me Tell TTV the truth. It's only Hot Current, Kulinji and Times Exclusive. That Malawians Need to watch and Listening to it un endless without get tired. Zinazi Siilani Jacav podcast. Coz izizi or Tamia Jah can't do.
Do you think we can keep on listening those 3 programs the whole week 7 days are you serious? I can confirm that you are stupid Mr man and you do know nothing
After interview iyiyi inuyo a times mukuonakuti ife owonera itthandiza bwanji apa a times plz masiku anowa owonera ndiambili choncho musokeresa ambili asikana
Please people don't judge, judgement is only for God, let God change her life.
Mmmm,zomvetsa chisoni ,Pa nthawi yakusadziwa Mulungu analekerera
God will see you through and give you a better job in Jesus name
Eeeee umphawi si zinthu hevy cz umayamb zoti sukanapanga 😢😢😢😢😢
Remember this!! All of you whom are shaming the lady! Everyone's has a story to tell in this life
Ndipo kobass
I like her confidence she is not fake atha kusamala banja uyu
Mutengeni😂
Akazione eti
Aaaa munthu ogona ndamuna 10
Angakhale ndi feelings ya banja
Big no
For me
Kungo yambana pang'ono utha kumaganiza zoti ndiwogulitsa
Kkkkkkkkk
Mmmmm akulu.....ziwandatu izi
Mu umoyo uno wadziko la pasi nkhani ndichithandizo. Munthu aliyense amazionera yakha m'mene angamapezere chithandizo pamoyo wake. Uyuyu anapanga chiganizo chabola, enatu thandizo lawo ndikupha anthu anzawo. Aggie, sukubama amana ambilife chikondi tilibe. Timangozuwa kuchinda ndikukodzera una wathuwo. Mkazi akatenga mimba timakana kukanaso mwana obadwayo kukachindaso wina ndikumukodzera. Akaima mimba uuuuuuuwooooo wautali kawina. Ndikuthokonze kuti wabwera poyera. Tili ndizimfwamba mudziko muno zimachinditsa ngakhale mamuna alinaye ndipo alitu munyumba momwemo koma busy ndi amuna ena.
Pempo langa ngati utalhala nawo mtima oti aaaaaa izi ndapanga basi ndisiye, siya koma yang'ana tsogolo la thandizo lako. Mulangu akudalitse adalitseso business yako ndikuti apange njira ya m'madalitsidwe ake sitingupangire koma kungomupempha.
Koma zoti jahena iriko mukudziwa
Better kulapa ndikusiya ndikumtsatira YESU akhale thandizo lako aunt
Tikapuma kumwamba nkhan zomvesa chisoni kwambiri, mwana wa munthu kumalankhura izi choncho ambuye atichitire chifundo
Musiilen mulungu mwini wake
Uyuyu amadziwa chimene amakachita pamene am achoka kwa oko
Eti first day pa bar amuna 10 no mantha osatopa adali hule kale galu uyu
Mavuto Ake ati munthu Uli ndi luso lamanja
Kuganiza kusiyana ladies mmmh
Alibwino kwambili kusiyana ndamene anapanga zinthu mobisa
Miyambo 23 wobisa ntchimo sadzawona mwayi😂😂
Akukana banja amuna anamukhumudwisa nkaona anangoyamba zauhure
Fisi ndi fisi samasintha ngakhale atasintha tchira
I like the confidence
Amenewa akupanga promote uchitsiru uhule komanso zoipa. Adzaikenso zimenezi.
Koma times please makamela pangani improve 🙏
Uyu amachoka kwawo anali atayamba kale za uhule zo asatinamizepo apa
Eti nakha first day athu ten😢
Komano panopa osayanba business bwanji
Izi sizikuthandiza
Yesu akufuna moyo wako mama
Ati bola ogona pansife koma onjutawa😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkkk Koma 😂😂😂
Koma guys, Agi ndi Warrior
Akunama amapita ku uhule komweko bwanji adamufunsa wanjinga kt ukandisiye ku bar komanso munthu oti sadapangepo adakwanitsa bwanji amuna 10 eish , adali hule nkale ameneyo
Hule opanda ulemu mmh ati ngati sabwela 2dys timan'galula kwa mkaxi wake kupita komko hule sakhala mwana acc ndinu opusa mmh mutha ngati katani
😂😂😂😂😂 wakwiya nayetu😂😂😂 zinazo akungokometsera uyu
@LameckManuel-f3q eeh aise wanditengamotu angokomesela eti kkk ndudabwatu
Mulungu amene anasintha saulo nakhala Paulo asinthe moyo wa mzimayiyu ndikuti tsiku lina adzaperekere umboni ndikulimbikitsa wina wake,
Amen and Amen
Amen
Mkazi womasuka kwambiri komanso wozichepesa the only problem that I have seen is poverty
Zoonad
Zoona
This lady needs help. She can change I feel pity for the child.
Never she can't change after making 10kwacha she rent somewhere and looking for jobs
Zoonad
koma ofunsa mafunsoyu samatha kufunsa mafunso
Muli ndi bodza mufuna adzipanga bwanji
Mawu osasa masacheti amewo ambuye ntengeni 😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Kkkk ambuye mtengeni yemweyo bas kkkkk
Mahusha amakomo a secret mwabizika repent tu tayambani inuyo😂
Inu muthu amasitha mzanga pano alipabanja anakhazikika komaso ndiopephelq moopsa
Mmmmmmm zovuta
Asaname anali hule kale uyu, kumpemba nde kwawo kwamahuleko
Kkk eti inu hmm
Uyuyu Adayambila kwawo konko koma adafuna kutalikilana ndi achible the same reason adakana ku Lilongwe 😮
Dziko ayi koma yesu 😢😢
Dziko nd lachabetu ❤❤❤
Khristu mu nyimbo 137
Winawu ndi uchisilu ndithu ndemukamati akapanda kubwela azibambo okwatilawo ndemagoulula ndephidu lake mkukhala chani
Ma customer tonse tikumane kaye paselipa😂😅
Times Television can do better on other programs like Hot Current. Not this stupid program with Samuel Kalimila ndi Hure. Let Me Tell TTV the truth. It's only Hot Current, Kulinji and Times Exclusive. That Malawians Need to watch and Listening to it un endless without get tired. Zinazi Siilani Jacav podcast. Coz izizi or Tamia Jah can't do.
😂😂😂😂
Kkkkkkkkkk
Umbuli Inu akulu this is one of the best programs ku times it's fair and non political ma program ukunenawo ndi a politics and they are unfair
Do you think we can keep on listening those 3 programs the whole week 7 days are you serious? I can confirm that you are stupid Mr man and you do know nothing
When you say Malawians what do you mean, not all are politicians like you, usakhale uli mu gulu la anthu apa line
Koma za mtengo wa transport po nde wtinamiza 2015 sinali k1500 bodza😂😂😂
Tax
May God help her mmmm
Akanapitiliza za saloon Zo mmmm
Mwana uja ndikubeleka bwinobwino, what kind of question is that????
Choyakhula chikundisowa
Kumvetsa Chitsoni Mwanva
Zoona thupi limagonja,aboma athanizeni anthuwa,kkkk akuti amatuma Iwo anabwera okha
Mulungu ail nawe cholinga Angie Ngati uzavomereza ambuye ndikulapa ambuye adzakupatsa chokhumba m,tima wako mulungu amakukonda
inetu atolankhani mkulalimba mtima bwaanji kkkk mkabudula kkkkkkk
😂😂😂😂
Ati tsiku loyamba amuna 10.....ayi ndithu zikomo😢
Esh zovuta kwambiri chonena ine ndilibe
Mr kalimila mukugwilatu ntchito
Koma zina ukanva😂😂 aaaaa
Ndie bola ukanapanda kutchulatu dzina mpingowotu
Pa Mwana ku bar pokhapo zandiwawa
Aggie osatitchula maina eti
Akumpingo???? 😂😂😂😂 Satchula ayi
Zovetsa chisoni tsikana.wabwino bwino
koma zilipo ku malawi
Mtolakhaniyo mmene wayambira ku kusitha ma position koma ali bwino ameneyu
😂😂😂
Wayanba kuyaka
Uyu timuone bwino 🤣🤣🤣
Nthawi yakwana mayi mulape basi, bible limati, munthawi yakusadziwa Mulungu adalekelera panopa akuitanira anthu ake kukulapa
Hule ndi hule
Obisa machimo ake sazaona mwayi
Chisilu cha munthu ichi ndipo chamwano koopsa
Ukamaliza program Sam udyemo talawa man
Kkkkkkkkkkkk koma man apakule nawo nyemba za guluzo shaaaaaa
Ok
I think uyuyo ali ndi ufiti kapena ali ndi ziwanda
Nthawi yatha chemwa lapani . Taona yesu khristu ali pakhomo akugogoda.
Km mama mumatha pitilizan malangizo anu
God help us
Ambuye muticitile chifundo moyo uwu ndi wanu, mutithandiza mutumize mzimu oyela uzitizudzula
Eeeh koma Times itionetsa zinthu
Mmmmmmm awawa akhoza kukupha haaaaaaa kwatilani guys
Komano nkhani ndiyoti pesikayu🍑🍑🍑amatha lastic
Kufela pomwe anachokela
Mwamuna ameneyo
😢😢😢😢Umphawi eish sizinthu
Hule wa ku mzuzu uyu ku big 5.....
Eish what a life
Mwana wa BT 😆😆😆😄
Amuna 10 one day yooooh 😂😂😂
Osanvaso kukoma zaziii
Ambuye mutichitire chifundo
Kkkkkk 😢
Eeh ndusowa chonena
Ambuye amuyendele
Uyu uhule anayambira kwawo,chinthu choti sunachitepo sungalimbe mtima mmene anapangire Iyeyo amuna mpaka 10? Mmmm ndiwojaila ameneyo anajaila kale kwawo
Mwangokhala ndi nsanje
After interview iyiyi inuyo a times mukuonakuti ife owonera itthandiza bwanji apa a times plz masiku anowa owonera ndiambili choncho musokeresa ambili asikana
Feel sorry kwa mwanayo
Mbame🔥🔥😂
Chifukwa chani anthu oyemdayenda amakhala ndi mau osasa
Mowa then kulilira daily
Chifukwa chotsopa mbolo zosiyana siyana, mowa ndinso kusagona mokwanila
Kkkkkkkkkk
Amuna 36,500 kwa zaka 10
Masamu Ake ndiye mwa Atha Koma akhiza kudutsa ndithu
😂😂
She Iz young but mkazi sachepa Ku bed Mesa..
Uphawi sizinthu mmmmmmmmm 😭
Siumphawi uyu akutitu adali ndi saloon amvekele sizimayenda mmh adangokopeka uyu
Mzathu uyu sanabise cholakwa chake ndipo A YEHOVA amakhululukira. Aggie YESU KHRISTU akhale Nkhoswe Yako ndipo azakuchotsa chitonzo chako.
Kom mwanayo mmmm ay sizoon kom
Wabodza uyu uhule adauyambila kwawoko
Kķk kodi bundle umagula wekha eti kkkkkkkk ndimayesa umangopedzeka muzandale zokhatu 😂😂😂😂😂😂😂
Ku bt kwayakatu àpa
Ali ndi tsogolo uyu. Watopa nazo izi
koma Aggie
Koma xiazibambo zofunika kumafa ndi AIDS,mwatopesa
😹😹😹😹😹😹😹😹 mwawona mavuto okana mitala aaaaa zowona
Ndine owala
Eeee mavuto ariko
Mumatha Uncle Sam
Zovuta eeeshi
Waing'alula