Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Am not his Church member but the way he answered questions makes sense . Ma missionaries anatidekhetsa kwambiri ,kwawo zikutheka
Muthu aliyese ndiochimwa unaaliyese akalangidwa Chi chimolake osamuweluza Muthu muthuyi waiwe iwolaka ayi
Nice
Mutha kupitiliza 31:44 Lukayo mumve
Zachuma cha munthu wina ukufuna utani nacho ndichaabiyako
Zaiiiiiiii akudziwa na ndiwereenaaa alobe choooonadiiiiiiii 😢😢😢😢
Kkkk anabwera limodzi ndi president ..but that's good chifukwa amazunzika
Luka 12:31 pepani apo👏
Plz Reya nex interview uzamfuse bushiriyo kuti chuma chomwe anachisiya ku SA pano akuyendetsa ndindani kapena analindidwa chonse?
Wina akuyendetsa galimoto ataledzera wapanga ngozi or galimoto lilindivuto ,yet kwa Amalawi ndi bushiri ... Tilimbikire kulimbikira ndikukwanitsa kupewa .
Linali funso lokongola abwanao angozemba mayankhidwe awo molingana ndi azineneli amene mulungu ankalankhuliramo munthawi zakale akafuna kulankhula Kwa wanthu amanena kuti mu mateyu 6=33, komaso mu yohane 12=3 nde abwanao asathawire Kwa anthu osauka ameneo azakhalapo mpaka kalekale zimamukondweretsa mulungu zimenezo osauka analipo asanabwere ma missionary akunenao, funso langa ndirakuti ndinu prophet wamu tchalitchi chanucho kapena wa mulungu kuti wakutumani kuzawayankhula anthu Ake?kapena ngati ndinu kamwa yamulungu uthenga,komaso mubadyo wake utiwo komaso mubayibo mukupezeka pati kuti Bible ikukhalireni khonde.chifukwa azineneli amulungu onse amene atumidwa ndi mulungu Ife timawaziwa ndi mawu amulungu samasusana nawo mawuo ayi.ndiye mwina atiuzenso kuti mawu ameneo anatha ntchito olo kapena tiwachosemo mu Bible?
Sorry Luka 12:31 osati 3👏pepani
Kuno unapanga mbiri prophet aliyense amandiyitana bushiri