NKHANGA ZAONA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 вер 2023

КОМЕНТАРІ • 21

  • @OmarMkwela
    @OmarMkwela Місяць тому

    Tikuyamika kwambiri a mmthanyyiwa po matitsekula mmakhutu thank you our comrade❤❤❤❤

  • @OwenNyangu-nv1yt
    @OwenNyangu-nv1yt 5 днів тому

    Nyimboyi ikungosonyeza kuti. Siyalelo ndiyekuti Mavuto ndikale kumalawi. Siatonse mukuyinamizilayi.

  • @PeterSuwack-ox6rj
    @PeterSuwack-ox6rj 6 місяців тому

    More 🔥 🔥

  • @user-qv4ko6ps4j
    @user-qv4ko6ps4j 6 місяців тому

    Boss mumakwana

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 9 місяців тому

    Big up nkhanga zaona

  • @HOMEAWAY-h7t
    @HOMEAWAY-h7t 5 днів тому

    UleMu ❤

  • @HarryZinyanya
    @HarryZinyanya 4 місяці тому

    Zaona ilikuti

  • @user-xd9fp2bw8j
    @user-xd9fp2bw8j 9 місяців тому

    Kkkkkk madeyawo tikawatenga kuti popeza madeya amachokela kuchimanga ndiye chimanga kulibe zativuta basi

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 9 місяців тому

    Bright Nsaka samayenera kupanga zinthu zimenezo koma wandikhumudwitsa zedi coz amaoneka ngati is one of our future leader in DPP 😂😂😂.

  • @user-fp6zi6lf4i
    @user-fp6zi6lf4i 9 місяців тому

    Kkkkkkkkk zaonetsetsa keep it up. Tilinko ku nkhokhi

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 9 місяців тому

    Comrade mwamutchula Ben mtelera nyan kod sir Charles adadyamoso mwa Patricia yu

  • @ritabani274
    @ritabani274 9 місяців тому

    Olo mutati tinyelele nyumba kuti tipange manyowa titha kunyelanso bvuto lomwe tili nalo manyiwo achokera kuti🙆🙆🙆

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 9 місяців тому

    Kkkkk nkhanga zaona

  • @Goliath461
    @Goliath461 9 місяців тому

    Kkkkkk tidya chani abwana

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr 9 місяців тому

    Iweyo kamandevu nsaka ndiiwe wankulu mutu ndiye mutuwo siungangokula opanda nzeru ayi nzeru uli nadzo yambisa chako chipani ndiiwe chiweto ku DPP ukuyenereka kuchoka .

  • @Goliath461
    @Goliath461 9 місяців тому

    Uthenga wabwino

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 9 місяців тому

    Mmmmm...inu Gagayo moti Anthu azidya ndi Njala yake imenei....mbwanji osawauza kuti azikumba Zimbuzi zomwe zinazaza ndi Manyi...!!!...n'kuphatikiza ndi Ndowe zambuzi.

  • @edwinlerwill6978
    @edwinlerwill6978 9 місяців тому

    Nkhanga zawona koma logo mwaika nkhukutembo😂

  • @leonardjika2100
    @leonardjika2100 7 місяців тому

    THAT'S NONSENSE TO TALK ABOUT MIKOZU FROM PEOPLE THAT'S STUPID GARBAGE EVIL IF IT WAS FOR GOATS AND SHEEP WAS BETTER DON'T TELL US USELESS EVIL METHODS

  • @user-dt8nr1zx6e
    @user-dt8nr1zx6e 9 місяців тому

    Nkhanga zoona morefire