NKHANGA ZAONA KOMANDA KWA SING’ANGA MZIMU WA BHIYENI WAVUTA NDE KULIBE TUROTU ABWANA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 225

  • @BatumeyoChikopa
    @BatumeyoChikopa 2 дні тому +3

    😢😢😢 Mzimu wa chilima and 8 others uwakanthe oipawo mhsrip, thanks comrade Ntanyiwa

  • @BenardThomas-p6o
    @BenardThomas-p6o 7 днів тому +22

    Kmatu mtanyiwa ndikatundu

  • @Alkalinebalakas
    @Alkalinebalakas 7 днів тому +15

    Amalawi anaiwala izi pano chiwanda chalowa mwa anthu avekele m'boma ndilomweli 😢😢😢

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 7 днів тому

      Ndipo akuyesa kuchemelera kuti boma ndi lomweli
      Ndipo akundinyasamo anthu amenewa

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 7 днів тому +9

    No peace for the wicked. Rip 9 souls 😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 7 днів тому +8

    Mr Comrade, well come back , mumatimvetsa kukoma

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 7 днів тому +10

    Ayaluka ndipo chilungamo chidziwika ife sitisiyabe kuyankhula za chilima

  • @JessyNellohThom
    @JessyNellohThom 3 дні тому +3

    God protect you comrade.son of the soil

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 7 днів тому +1

    Comrade Nthanyiwa may God protect you with the blood of Jesus christ.

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 7 днів тому +6

    Chakwera ndi nduna zake pamozi ndi satana wawo bushiri azasowe muziko lamalawi

  • @ChipanganoMajawa
    @ChipanganoMajawa 6 днів тому +2

    Ndiri okondwa kuti kumalawi kwadzuka anthu olimba mtima ngati inuyo kuulura zinsisi zakuya ngati izi opanda mantha,May God protect you sir

  • @HawahMussah
    @HawahMussah 7 днів тому +4

    Wathu wathu comrade ntanyiwa Amos pa cape town salute

  • @GibsonMithi-n4y
    @GibsonMithi-n4y 5 днів тому +3

    Inenso ndikhumbo langa Kuti mzimu WA chilima ndi anthu ena aja mizimu yawo isagone ndipo isawasiye onse amene anatengapo mbali ndi moyo afe ndithu ifa yowawa

  • @lyiemax
    @lyiemax 6 днів тому +1

    Eeeeeh koma anthuwa ndi zilombo, very happy to have you comrade our redeemer, proud of you always ❤❤❤❤

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 7 днів тому +8

    Chakwela olo atafa wa chititsa manyazi dziko la mw

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 7 днів тому +27

    Bushiri 2025 asowe mdziko la Malawi

  • @LuciaKalumo
    @LuciaKalumo 7 днів тому +8

    Ambuye adzikutetexan bro

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 7 днів тому +1

    ❤❤❤❤ambuye akudalitsen mukuwaza kwambiri Mr ntanyiwa

  • @moureenmolesi
    @moureenmolesi 4 дні тому +2

    chikangawa mulungu akulange pansi pompano ndipo muyaluka simunat a ntanyiwa ulemu wanu 🎉🎉🎉

  • @FunnyDimSum-hk1so
    @FunnyDimSum-hk1so 7 днів тому +3

    Ndipo sanati amva nyunyu mumakwana atanyiwa

  • @BlessingsMphamba
    @BlessingsMphamba 7 днів тому +7

    Ameyodi ayenda mwa sing'anga sanatiii....mzimu wa munthu ndowopsa 😢💔😢

  • @fedson2050
    @fedson2050 7 днів тому

    Bwana Comrade Ntanyiwa mumakwana, ndipo mulungu azikutetezerani thawi zonse.
    Amen

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet 7 днів тому

    Tili naanu ANTANYIWAAAAAA ❤
    Ndipo MULUNGU adzikudalitsani ndikukutetezelani ameen 🤲

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 7 днів тому +3

    Ndipo a Malata sakupuma nanu bwino. Koma Osadandaulayi, munthu akamathamangitsidwa kenako okuthamangitsayo ukanva akukutukwana dziwa kuti wakulephera ameneyo. Asiyeni agaluwa adzikuwa, galu samakuwa galimoto yomwe yangoyima, galu amakuwa galimoto yomwe ikuyenda

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 7 днів тому +4

    Verentino kukamwa ngati wadya manyi😂😂

  • @AnnieKalipo
    @AnnieKalipo 7 днів тому +1

    Mumatimenyela nkhondo , Mr m'tanyiwa mulungu yekha azikupatsani Moyo Wautali .

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 7 днів тому

    My role model mtanyiwa almighty GOD protect u.

  • @LuskaMoses
    @LuskaMoses 4 дні тому +1

    Iwo akupita kotenga kakhara ife pomwe tupinda miyendo kupepherera kuti asowe mtendere ndi imfa ya chilima😢😢

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 7 днів тому +1

    Welcome back mr comrade ntanyiwa Allah alipo
    Akatisungabe mpaka Inshaa Allah next year achoke crocodile 🐊 pampando wakupha ameneyo ndi manganya koma Allah akulangani ndithu

  • @HameedSaleem-o4v
    @HameedSaleem-o4v 7 днів тому +3

    God bless ntanyiwa tikuziwa kut MCP sikufunizabwino plz be safe Mr ntanyiwa

  • @thatgirrroskrr3570
    @thatgirrroskrr3570 7 днів тому +6

    Timava nanu kukoma bro

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 7 днів тому

    May gud Lord almighty protect and bless u broh poima pachilungamo kkmas poima ndi Amalawi osaukafe mavuto aliku Malawi ai tingomusiira Ambuye Mulungu

  • @EllenGomani-i4f
    @EllenGomani-i4f 6 днів тому

    Best Radio ever❤❤❤🎉 mumatimvetsa kukoma Comrade

  • @jeanbotomani9081
    @jeanbotomani9081 7 днів тому +6

    Auze ntanyiwa kuswakuswa

  • @edwinnyasulu2088
    @edwinnyasulu2088 7 днів тому +2

    Welcome comrade

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 2 дні тому

    MCP ndiyozunza tiyichosabay amutanyiwa ❤❤ mumatiyimilila tilipambuyo pa UTM

  • @josephjana695
    @josephjana695 7 днів тому

    More fire Comrade always proud of you

  • @LuyoloTlhapane
    @LuyoloTlhapane 4 дні тому

    Mhu Koma kaya ,misoz yaanthu Osauka ikugwela pathaka tilibeso mphamvu ndife osauka mau athu sapita Patali .God protect u all the time

  • @CassimJafali-g4l
    @CassimJafali-g4l 7 днів тому +4

    Chakwela agwa BP pompano

  • @BeatriceKennedy-b1b
    @BeatriceKennedy-b1b 5 днів тому

    More fire comrade mtanyiwa

  • @YonaPearson
    @YonaPearson 7 днів тому +3

    Mwatulukira mundu wakulu tinakusowa kwambili nditu mulungu Akupase moyo wautali

  • @LuskaMoses
    @LuskaMoses 4 дні тому

    Amaiwa ndikaona Ngati Mai opeohera opa mulungu omva chisoni Mwana wa amzao eish Mai inu pepheni ambuye Sanga akukhululukireni mudzafa imfa yomvetsa chisoni ndachikangawa anuwo 😢😢 Mai mwandikhumudwitsa sure😢😢

  • @Yoxym
    @Yoxym 7 днів тому +2

    Usamasowe choncho mtanyiwa uzatipha ndi bp🎉😢

  • @FunaniChagwira-ue5pl
    @FunaniChagwira-ue5pl 4 дні тому

    Mtanyiwa ndiwe a katundu God bless you

  • @daviskamonde4882
    @daviskamonde4882 7 днів тому

    I missed you my journalist!!

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 7 днів тому

    a comrade.ntanyiwa inu ndi inu katundu, womanga manga eish zikom Kumwamba. Potipasa inuyo litetezeni bas dziko la malawi li, ipase moto kuti buuu antanyiwa ❤❤❤

  • @MussahWilliam-py1ff
    @MussahWilliam-py1ff 6 днів тому

    On fireeee comrade ,timakunyadiran bro

  • @TimeAbilu
    @TimeAbilu 4 дні тому

    Umakwana a comrade mtanyiwa more fire

  • @EmilyBanda-xx8gd
    @EmilyBanda-xx8gd 7 днів тому +1

    Munasowatu timaopa kuti akupezani kodi your welcome Mr

  • @CassimJafali-g4l
    @CassimJafali-g4l 7 днів тому

    More fire ntanyiwa mzimu wachilima ukuyenda ndipo anthu avutika kwambili sanati

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 7 днів тому +2

    Ndasangalala potidziwitsa zambili lero,mulungu akudalitseni komanso akutetezeni

  • @berlz12k
    @berlz12k 7 днів тому +1

    UDF ikupanga ubale ndi MCP Kodi mesa anawaphera shanil and kuli ana komatu ndalama inamperekadi yesu mwamva🙌

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 7 днів тому

    We love you brother ntanyiwa

  • @AsiyatuAkila
    @AsiyatuAkila 6 днів тому +1

    Ndimakudyadilan mr ntanyiwa A .k from keptow god bless you 🙏 ❤️ 💖 💕 ♥️

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 7 днів тому

    I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa

  • @HarryMakwale
    @HarryMakwale 7 днів тому

    You are number one mr

  • @ZikaniJere
    @ZikaniJere 6 днів тому

    Long live mtanyiwa. By the way I need those tracks there's content in there

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 День тому

    More fire comrade ntanyita osaopa osatopa osafooka Allah alipo mpaka tituluke mukaporo tilinawo pano ndi boma ra crocodile

  • @OjessTetezan
    @OjessTetezan 6 днів тому

    Mmakwana inuyo keep it up to inform us .

  • @EphiehkariPhiri
    @EphiehkariPhiri 3 дні тому

    Loud and clear here in middle east

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 3 дні тому

    Umakwana comrade chakwera achoke basi sitikumufuna

  • @RachealPongolani
    @RachealPongolani 7 днів тому +2

    😂😂😂😂kom Mtanyiwa kuseka kokha utha kugwa nd BP 😂😂🙌

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 6 днів тому

    Nthanyiwa achikulile Ali kumwambaku anaolosa ana aizalaeli aolosetso nthanyiwa

  • @TioneManda
    @TioneManda 7 днів тому +1

    Mr mtanyiwa mulungu azikudaliseni nthawi zonse akutetezeni mumativesa kukoma tili pa mbuyo pano

  • @AyandaPhungula-bg9ql
    @AyandaPhungula-bg9ql 7 днів тому

    Biggup good job bro❤

  • @anastanziaelia-gk3tt
    @anastanziaelia-gk3tt 3 дні тому

    Ntanyiwa muziseka bwino Pirato aziphatu 😂😂

  • @violetpotani
    @violetpotani 3 дні тому

    Mumuwuze Valentino yo kuti nkhope ngati khasu... Ifetu mulungu amatikonda

  • @MussaMtalika-g7d
    @MussaMtalika-g7d 7 днів тому

    God bless you baba

  • @SalomeManda-c1i
    @SalomeManda-c1i 7 днів тому +2

    Ndimadabwa kt a ntanyiwa not tingogona osamvera nkhanga zaona?

  • @StarchJonas
    @StarchJonas 7 днів тому +1

    Ma MP amenewo adyeretu ndalama zamagazi zawozo koma mizimu izakwiya 2025 sakuzalowanso m'boma

  • @RodrickPhiri-j8e
    @RodrickPhiri-j8e 7 днів тому

    Mr comrade Mulungu akuze malire achitetezo chanu komanso kukupasani moyo wautali

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 5 днів тому

    Nzaulula ija Sananame di esh

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 3 дні тому

    Mmakwana big

  • @kasimmussa-c5v
    @kasimmussa-c5v 6 днів тому

    Mr Tanyiwa Tinakusowan ❤❤❤

  • @finessechikaphonya2445
    @finessechikaphonya2445 День тому

    Mulibwanji anamajekete😂😂😂😂😂

  • @LuyoloTlhapane
    @LuyoloTlhapane 4 дні тому

    God protect you

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 6 днів тому +1

    Tchimo rimazunza orichita rero ndi izo ndarama murinazo km simukugona usiku baibo rinat munthu wachuma ndikovuta kukondweresa yehova siizi kodi chakwera panopa aribeso nthawi or kungo ganizako kt kumwamba kuri chauta

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 5 днів тому +1

    Nzaulula ija sinyimbo wamba esh

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje 7 днів тому

    Number 1 program

  • @MarkDominico
    @MarkDominico 6 днів тому

    Ena tidakwera yachakwera ❤❤

  • @ZioneDinala-z3h
    @ZioneDinala-z3h 6 днів тому

    Grace chinga ananedi koma anthu amati ndizaboza lelo siizi zikuchitikazi amalawi bwanji pamenepo

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 7 днів тому

    Anya nayo sanati,angolubwa lubwa game yawo sikuyenda😅😅😅😅😅😂😂😂yomweyo Chikangawa Silimangeni 😅😅😅😂😂😂😂

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 7 днів тому

    Musamasowe mr Ntanyiwa 😅😅😅😂😂,mbuzi yamunthu malata

  • @charlesmbewe4001
    @charlesmbewe4001 7 днів тому

    Mr Ntanyiwa mumatiomilira kwambiri Mulungu adzipitilira kukuteyedzani nthawi zonse

  • @BysonPhiri-gu4io
    @BysonPhiri-gu4io 6 днів тому

    Fire 🔥🔥🔥

  • @FrankJumah-l7f
    @FrankJumah-l7f 21 годину тому

    Komuled sangagwidwe

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 4 дні тому

    Gyz ma church onse a bushiri tikuenela tiwawotche chisilu chimenechi chikutionongela dziko, walowetsa satanic mmalawi tiyamba kuotcha ma church ake pomaliza pati pakumane nae ife bushiri timuotchela pompo ana opanda amawo alibe ntchito

  • @khoviwaedward
    @khoviwaedward 7 днів тому +2

    Comrade Ntanyiwa ndiwe no 1 bro palibenso ayi. Joker yo musunge pa bwino brother adzapweteke mcp next year before election.

  • @EdwardBotha-h1i
    @EdwardBotha-h1i 3 дні тому

    Amalawi amene anakhuzako thupi la chilima a vutika kwambiri chifukwa mwakhuza thupi la mwana wa mulungu

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 4 дні тому

    Commander amenei chisilu ch a mache amenei bushiri,chikangawa pamodzi ndi MCP yonse akuyenera kufa ndithu.Mizimu imenei yonse isonkhane iwakutumule onse anthu a satanic opanda a mawo,zisilu inu tachioneni chimutu ngati fuwa la kachaso APM voti yathu.Ntanyiwa,kalindo ndi ena nonse timakunyadilani god bless u gyz we are in this 2gerthr

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu 3 дні тому

    Bushiri 2025 ,,, south Africa ikubwera izakunyamule,,,, 10 yrs ukugwira jere ndi azako a MCP ( chikangawa imvi zizaonekera)

  • @idahntchito
    @idahntchito 3 дні тому

    Amtanyiwa #1

  • @EmmanuelMgala-y5d
    @EmmanuelMgala-y5d 18 годин тому

    Mlungu si James mzimu wa anthu 9 aja sikugona

  • @BandahLemos
    @BandahLemos 7 днів тому

    Timadalira inuyo bwana ❤️

  • @GIFTPAUL-c9s
    @GIFTPAUL-c9s 3 дні тому

    Ukunamatu iwe umango lubwalubwa kuchikamwa konyasako garu wacha bwechabwe iwe

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 7 днів тому

    Welcome the comred mtanyiwa

  • @AtupeleChitenje
    @AtupeleChitenje 7 днів тому

    Koma yah ne rest in grace mama chinga 😢

  • @DeodataKachapira
    @DeodataKachapira 6 днів тому

    Mulungu alowererebe pa nkhani za mdziko mwathuzi

  • @georgealabih8979
    @georgealabih8979 День тому

    Commander yu ndi mfiti yeniyeni idaika Sambalopa kuti afe nawo

  • @isaacthawani5442
    @isaacthawani5442 2 дні тому

    Kodi azanu a born kalindo bwaji atiii ziiii ka 3 days kameneka kapena adya Chimbaziii

  • @AndrewSimakweli
    @AndrewSimakweli 6 днів тому

    Bravo ntanyiwa