MICHAEL USI WANG’ALURA OMWE AKUMAFUNA KUMAONEKA NGATI IMFA YA CHILIMA INAWAKHUZA KWAMBIRI KUPOSA IYE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 20 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 94

  • @FransBanda-z9g
    @FransBanda-z9g 6 годин тому

    Well articulated vice President, ngati anthu tili anzeru we have to learn something from this speech.

  • @masoyaonamunkhondya9074
    @masoyaonamunkhondya9074 13 годин тому +5

    If I was Michael Usi, I would have just stay quiet because during the days when Chilima was alive people saw you that you didn't participate in UTM meetings. Today because you were chosen as vice president accidentally by late biyeni you take for granted that people recommend you as leader of the party but on ground you are zero percent. Just eat what you have found .

  • @kumbukanikafwafwa
    @kumbukanikafwafwa 5 годин тому +1

    Utm ndi chipani. Malemu aja anasiyadi gap😢. Kma that will be determined when the president of utm will be chosen to take charge. what happens after zisakho will break it all.

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 13 годин тому +6

    Utsogoleri si umemewo a Michael Usi monga tsogoleri,osamatchula zolakwikwa za nyumba zake

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh 8 годин тому +2

    Program yazokonda amayidi

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 31 хвилина тому

    Who ever touches the word of God on world stuff.. Be careful.... Munthu amene yo God is on his side.... Be wise

  • @wezienyirenda
    @wezienyirenda 7 годин тому +1

    This guy speaks wisdom,sapanga nawo za phuma.

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 2 години тому

      Ndipo zoona apapa akakayasako makendulo kut anthu amunkhulupirire

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 44 хвилини тому

      ​@@FrancisNyayi😂😂😂leave the dead akulu makendulo achani

  • @abunaseem6866
    @abunaseem6866 4 години тому +1

    Zokonda amai

  • @pacharokoloviko1694
    @pacharokoloviko1694 Годину тому +1

    Kape uyu mfundo zonsezo atha kuyambira chipani chake azikagwirizana ndi MCP yakeyo. Sizomatipinda ndi baibulo nthira kuwiri iwe, olo chilima ataukisidwa ngati Lazaro utha kukwiya ndiweyo manganya.

  • @MacsJafali-d1m
    @MacsJafali-d1m 9 годин тому +3

    komatu osamangowoa pa mwamba pa znthu poyankhulaa km munthu uyuy amaganiza kooopsa end smunthu wambaa
    muzakhmudwa atawina

  • @AubreyShaba-b5d
    @AubreyShaba-b5d 4 години тому

    On the surface now, UTM is split into factions... Whatever the case, 2025 General Elections will be based on Regional votes based on strongholds of both MCP and DPP...by chance Northern Region could be a deciding factor who to align with.... Whatever the case, there will be no clear winner of 50+1, even a re-run will never change results... For the first time, expect a Government of National Unity....

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 9 годин тому +2

    Ambilinso akuwoneka ngat Ali ndi chikondi koma ayi ,mene dpp ikututumukila pa infa ya chilima zodabwisa kut awawa ayamba liti kumukonda chilima

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 41 хвилина тому

      Ndipo aise zodabwisatu dpp pretending to love chilima.... I will say it again imfa ya chilima... opposition thinks kuti it's a tool kuti agwilise ntchito pandale not what is going on.... If he was my father I could stop all this nonsense and put an order that no one must mention his name muzopusa zawozi

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 11 годин тому +2

    Azibambo a UTM mwachita bwino osapezeka pa zokonda amayi.
    Ameneyu ena amatikwana azingodya ndalama KU MCP konko.
    Zautsuru

  • @LukeSaka
    @LukeSaka 7 годин тому +1

    Kolani chipani A usi chileke kumala osati wanyakewo wakutaka Waka yaluuu

  • @MacsJafali-d1m
    @MacsJafali-d1m 9 годин тому +2

    kd iwe ka sound kapas ndy kachan chikutuu

  • @MosesChisiChimbalanga-te5so
    @MosesChisiChimbalanga-te5so Годину тому

    Wisdom guy

  • @WonganiKatchale
    @WonganiKatchale 7 годин тому

    Tell them

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 10 годин тому +1

    Mudzalira naye uyu akuti ndi munthu owumira kwambiri. Muzifunsa anthu omwe amapanga naye ma drama osamangomuchemera Azimayi.

  • @AnnastanziaMhango
    @AnnastanziaMhango 11 годин тому

    Good speaking

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 8 годин тому

    upangese conversation yako garu usanamizire buble ndulu ya ng'ona😢

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 13 годин тому +3

    Ausi mwawina kale inuyo mukukwana

  • @NosiphoMazwai
    @NosiphoMazwai 13 годин тому +1

    Usi yomweyo my vote

  • @IssacMateyo-u2d
    @IssacMateyo-u2d 9 годин тому +1

    Ausi umakwana akweni osatengela ayi ndiachibwana

  • @kabvutamoffat7149
    @kabvutamoffat7149 8 годин тому +1

    Koma usi akawina ku convention anthu enanu mudzachoka nokhatu kuthawa mnyumba mwako momwe

  • @PatienceMphuche
    @PatienceMphuche 7 годин тому

    Zokonda amai program

  • @AugustineTheu-of6nv
    @AugustineTheu-of6nv 4 години тому

    Micheal Usi ndiwe unapha mwana wa eni, Sailos Chilima ndi mabodza akowo mbewa komanso mbuzi iwe

  • @shadreckjumah
    @shadreckjumah 10 годин тому +1

    Manganya ndi wakwanthu ku mulanje kma ndikutha kuona kuti uchitsilu ulimo ndithu

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 8 годин тому

    Munthu iwe be careful that you do to chilima

  • @spargomw
    @spargomw 13 годин тому +1

    Kod nd ku Msonkhano kapena ku Milaga?

  • @PiusChawinga
    @PiusChawinga 3 години тому

    Akuwina ku convetion uyu

  • @HastingsChidyaudzu
    @HastingsChidyaudzu 11 годин тому +2

    Zokambila za MCP mchani? Alipo wavala makaka a MCP pamenepo? Kapena mukunenera kuiwopa MCP po???????

    • @HannahTulizoh
      @HannahTulizoh 11 годин тому

      Uchitsilu basi akuiopa MCP yo ndakuti

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 13 годин тому +1

    Akunama mbava ndi azimai a chikangawa party

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 4 години тому

    Koma nditukwana kwinako ........

  • @EthelKubalasa
    @EthelKubalasa 3 години тому

    Usi ndiwe wabonza spy wa Chakwera iwe, unamuphetsa Chilima iwe.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 10 годин тому

    Km satana alipodi ndipo ndionyenga zedi

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 4 години тому

    Zakubanja Kwako izo iwe usi 😊😊😊 ndichifukwa chake kulibe azibambo ambili, chifukwa chake zibambo wazelu zngapange nao zopusazo

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 35 хвилин тому

      Oraphael... Understand kuti other people have born leaders nd no matter the opposition they will always stand.... Usi is the guy who thinks for the poor since ku Addra... He is winning no matter what

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 11 годин тому

    Zawuwinenge waka Usi, vikukuyenela ivi

  • @MicyThobve
    @MicyThobve 3 години тому

    Ndipo muwina bwana

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 6 годин тому

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @MagieJames
    @MagieJames 13 годин тому +1

    Iweso manganya ndwe munthu oipa uli mgulu lafalise kumwalira kwa chilima unacita ciyani ukufuna kunamiza anthu iwe

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 3 години тому

    Chilima wasn't stupid to choose usi

  • @Lushaka
    @Lushaka 11 годин тому

    Zamanyatsi ziko la Malawi guys are sure this vp president of country no guys Malawi people be serous how we do this take funny guys drama guy be vp president no no Malawi we lost mind

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 9 годин тому

    Manganya ndidolo

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 8 годин тому

    Amanga patumbo panu mau onyasawo unasowesa chilima kamba ukharepo iwe iwe munthu waminyama iwe hhhhhhhh iwe suvafa ndi chamukwera wakoyo nyamanu

  • @ntombiunice8637
    @ntombiunice8637 8 годин тому

    Achenjere nayo uyu usi ...akumenya catacomb ameneyu

  • @KalongaWhy
    @KalongaWhy 8 годин тому

    Munapha dala kamba koti asalowe naye 5 year ikuzayi nyamanu

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 12 годин тому

    Kkkķkk manganya

  • @BiliatMzungudala
    @BiliatMzungudala 12 годин тому +1

    Amakosana yazichotsani chisaundi mumaikacho chimasokoneza apo ayi muzibweza voleum kut tizinva zomwe mwapostazo aaa

  • @MariaGatoma
    @MariaGatoma 13 годин тому +1

    Mukuzikolatu nonkha kkkkk kambani mfundo zenizeni,,,azimaiwaso akuoneka kuti ndi a mcp

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 10 годин тому

      Zoonadi asatipusitse manganya azimayiwa ndi a MCP asanamize amalawi ngati sakudziwa kanthu

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 11 годин тому

    Kkkkk❤❤ mr vp

  • @charleskunjawa6999
    @charleskunjawa6999 7 годин тому

    Azimayi 😂😂😂😂😂

  • @JibraanSharief-ol1yn
    @JibraanSharief-ol1yn 13 годин тому

    ❤❤🎉

  • @austinevance3964
    @austinevance3964 6 годин тому

    Triple ooo

  • @GraceMadewu
    @GraceMadewu 11 годин тому

    Yohane 11 chiukitso cha lazalo

  • @LenoMvulaMvula
    @LenoMvulaMvula 10 годин тому

    Iweyo usi watha basi salila komweko ku mcp ndie sokalo maudindo wonse anatha kale kaya uwona wekha zocita kuyambra mwenzi wamawau

  • @dysonmasiye5736
    @dysonmasiye5736 9 годин тому

    MCP m'makaka a UTM zosautsa zedi...

  • @JamilMchakama
    @JamilMchakama 8 годин тому

    Inquiry izadziwika pa 16 september 2025. Amene analamula kuti Iron Lady Martha Chizuma amangidwe sitikumudziwa mpakana lero.

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 12 годин тому +1

    Koma manganya azimayi okha kkkkkkk

  • @LinlyMatheweKufakwina
    @LinlyMatheweKufakwina 11 годин тому

    Usi ndiwe munthu oyipa kwambiri

  • @ChicoBanda-kq7py
    @ChicoBanda-kq7py 12 годин тому

    Iwendiwe mbuzi

  • @MagieJames
    @MagieJames 12 годин тому

    Ndpo manganya nd wa mcp anthu kaya simukudziwa gulisani mavote kwa manganyayo munthu oipa ameneyu akufuna azikunamizani iyeyu nd wa chakwera kuyankhula akuzikola yekha mizimu yakwiya

  • @SamuzySamuel
    @SamuzySamuel 13 годин тому

    Program yazokonda amai 😂😂😂

  • @JoelChanza
    @JoelChanza 9 годин тому

    ?Mu drama muja mumakamba mfundo zabwno kma zomwe mukulakhula apazi zamwana wakukhonde

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 2 години тому

    Usi wawinakale enawo atumidwa kut abe chipan

  • @DawoodIssah-mp1yi
    @DawoodIssah-mp1yi 12 годин тому

    Atengana wonse a chipani cha madazi cha ng'ona party chikangawa ndi kamwana kake kouluka nako
    Nkumanamiza amalawi apa ife tikudziwa za inu achina chikangawa chifunga chakwera

  • @GreyMsonthie
    @GreyMsonthie 11 годин тому

    Palibe chanzeru ukulankhula mbuzi iwe

  • @IbuAli-u3f
    @IbuAli-u3f 9 годин тому

    Wachikangawa uyu satana weni weni

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 8 годин тому

    Zitsiru zilipodi

  • @SamuzySamuel
    @SamuzySamuel 13 годин тому

    Koma kukhale kozokonda amai

  • @giftsululu4274
    @giftsululu4274 11 годин тому

    Kom muphana

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 11 годин тому

    Watambala uyu

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 2 години тому

    Nde adikira chan kut ichitike ahhh asatikomedwesepo kkkkk

  • @RazackMalawi
    @RazackMalawi Годину тому

    aaaaaa

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 4 години тому

    Zookonda amai

  • @AndrewNtagaluka
    @AndrewNtagaluka 8 годин тому

    Ngati kuli munthu zopusa kumalawi ndiuyu

  • @starlonJames-qr4xl
    @starlonJames-qr4xl 10 годин тому

    Vs president akuyenela ankhale ndi phuzisi owaphhuzisa malankhulidwe tsogoleli akuyennela kt azilankkhula modenkha komaso voice idzikhala olinkha osati peppuke voice yamunthu wakulu aaa kukhala ngati ochemerela mpila chochi komaso pepho phuzisiyo azichita kumulembela zomfuna kulankhula kugulu chifukwa nthawi zambili misonkhano yawo ine sindi matolapo kanthu ai chifukwa aamangolankhula izi kenako izoo drama yen yen aphuzitsidwe przi chifukwa adzibwela ndi mfundo

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 17 хвилин тому

      I think first it's you who needs to be lectured, (1) you can't even write chichewa chenichenichi, 2 you are pretending doing shortcuts on your English.... Man we know you don't even know the spellings of those words 😅😅😅 so just shut the fuck😅😅😅 up... Pitani ku school yakwacha it's not two late

  • @MariaGatoma
    @MariaGatoma 13 годин тому

    Zokamba zanu ausi,,,zikupangisa kuti mary asazakuiwaleni,,kodi mumafikako kokamuona muyakhe,,chifukwa?yakho ndinu yudasi,,zonse zomwe mukuyakhula zikuoneka kuti mizimu yakugwilani

    • @JoliumChakhala
      @JoliumChakhala 11 годин тому

      Anayankha Kale kuti amalankhulana nawo pakakhala pofunika kutero

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 11 хвилин тому

      Omaria go and learn how we punctuation marks in a sentence. 😂😂😂😂😂 Sizongobwebwetuka pano zopanda mutu zanuzo

  • @IssacMateyo-u2d
    @IssacMateyo-u2d 9 годин тому

    Ausi umakwana akweni osatengela ayi ndiachibwana