They just book him to sing song for their chipani and Peter can also book him as well because Dan it's just a matter of business remember money talks 🇲🇼🔥🏃
This song is breaking Malawi song audio recordz the Second biggest after controller remix..... Malawians have loved the song I will come to check after a month
You are on the right direction Dan Lu ,a dpp aja akanakupha good kuti wazindikira kuti unazungulilidwa ndi adani ,ife takulandira ,wina atsekula mmimba ndithu 😂
Apa mtima wanu waphwaaa . Mudzidandaulaso kut anthu sakupangan sapoti . This is nice business you have joined uwe wachiyao tukwete malowe panandi kwa wao . Ayiyi akaikosza wawo ya ndale yangakawa kuwa
Congratulations nice business ndalama zikufunika or ndili ine Koma vote ndi muntima osaiwala Nyimbo singawinise muthu 😅😅😅
Finally someone has said it😂🎉
Inu ndiye mwasokera sure ngati mukufuna ndalama, mmmm mwaonjeza. Iwe ndiye ugendedwa
Salute
Never trust anyone in this world,
WHO'S WITH ME ❤️
THIS IS TRUE BROTHER
@JusticeNyirenda ndipo zoonadi
That's true
Yeh
Precisely, trust nobody
You know how to compose politics songs big up 🎉🎉
Adhawa avetsetseni🤣🤣✋ no hit song since sweet banana🤣👌 adyeko cash
😂
Koma ndiyetu
@@ChifundoNowa ndipo live adha awa basi anatha ,apa ndukupasangaso unfollow
Ndiye akut kwawo mkumenya nkhondo yapasi pasi.chikangawa😂😂😂😂😂
Chilungamo chabwanji ichi 😂
Eishi iyiyi mwapha malume , ndikunena Pano ili pa Repeat ❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Reducing yourself from 99💯as a pure musician to 50💯 as a DPP singer NOW Lowering yourself up to 3💯 as an MCP 🐊🐊chikangawa singer.what a shame Dan
Kkkkkkk paja iwe ndi wake weniweni wa DDP😂😂😂😂😂
Poti wapanga zosemphana ndi Inu? 😂😂😂
Hahaha osadanda muchila
Ndie mumadzatani kunoko.. Mumadzanvera nyimboyitu
Phala lenileni
More Fire Dan Lu.
Nyimbo wakwapula iyi.
Nyimbo koma iyi.
OIPAYO wadana nayo ndipo wapita Milomo.
Ndipo wanyetsadi zeni zeni.
Waimba bwino kwambiri
Boma nd lomweli😂... Palbe kusintha tikuti 😂😂🔥
ewen
They just book him to sing song for their chipani and Peter can also book him as well because Dan it's just a matter of business remember money talks 🇲🇼🔥🏃
This song is breaking Malawi song audio recordz the Second biggest after controller remix..... Malawians have loved the song I will come to check after a month
Uzabwere uzayimbe ku ndilande komaso Bangwe nyimbo yakoyi 😢😢😢😢😢 ndpamene ungaziwe kut walakwisa😂😂
Kkkkk
😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣
😂😅😂
😂😂😂😂😂
Mwapala sikukoma nyimboyi 🤣🤣🤣🤣 DPP MY VOTE
eti bwaaa🤣
Kwa amene amatapota DPP singamuvekele bwino kumene ndipo wapaladi kwa amene ali wa DPP
Mmmmmmmm😭💔ayiii ndithu zikomo opusa ndiney pogula bundle kt ndimvere zopeperazi mxieeew 🙌
Ndikuuza iweyoo😭😭😭
Kodi alipo president amene sanamangeko museu? Miseu ndi chitukuko chisavuta kambani zina
Mayo bundle yang a ndaonongela zaziii ngat izi mxieee🤣🤣
Mayazi galu ndine😂😂😂
@@JaneNthala 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Akugailan kandalama mukatero😂😂😂😂anyways APM is the best and you onw it,saluza coz wamutulukatu kod😅😅😅
Ku Malawi kuno ngat kuli amene amatha kuimba nyimbo zachipani nde ndiiweyo aise
Ndipo mupatseni maluwa ake
Chilungamo ndichija munang'alura kale mu Tulan pansi Udindo🌝
Ndipo live izizi zikuchita kuonekeratu kuti zikuimbazo ndi ndalama
Mwapala jomba lozani zanu yija ndi hit payokha walla bilaah😂😂😂😂😂
😂eti bwaaa
Lozani Zanu, Winaso ayi Tulani pansi udindo🎉🎉🎉
Indeed iyy aaaaaaah skundfkapo any way
Exactly 😂
Ndipo live ine phe kuveraso tulani pansi udindo
Waimba bwino
Uli bho🎉🎉🎉
Chakwela ndi lion 🔥🔥🔥🔥🔥
This song deserves an award As the song of the year ❤😊
Chisoni kwambiri
Ndipomnso 🎉🎉😅ine mbali yakuno kumva kukoma
Indeed you'll find that it's the best song indeed of the year 😂😂😂, a opposition akungolira ndi kukukuta mano
Nyimbo yokoma iyi🎉🎉inu Boma Ndi lomweli
Koma the sounds really good chimatha kuimba🤣🤣🤣
Zachipana Ada awa sapala
😂😂😂😂
Eee chakunga chikhazula gulu
Chaimbaditu bwino
😂😂😂😂😂😂 live
Iweyo ndi pangolin ase @Dan-Lu🔥🔥🔥
Welldone Dan for the first time following u
Nice one.. Dan u have freedom of association. Ignore the stupid comments. Politics aside, misewu n magetsi nde job well done!
Pena ndalama zimaonongadi dziko💔💔💔💔💔 mmalo momenya nkhondo kuti Malawi atukuke Danlu muli busy kusapota za ugalu ngati izi💔💔💔
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 akudyesani banzi 🤣🤣🤣🤣🤣 tulani pansi udindo,lozani zanu ndima hit dpp moto❤💥💥💥💥💥💥💥💥💥
Nyimboyi Ndie waphaaa Eeeh 😂😂 MOTi ine ndaimvera Mpaka ka Folo komabe ukuziwa mumtimamo kuti kakwacha kaja kanasiya akugwira ntchito
That's Why I love Dan lu .he is my model.... U know I just feel the beat and voice kkk the message is yours 😊😂
@@Chichiwestfada-en9zi 🤣🤣🤣🤣
You are on the right direction Dan Lu ,a dpp aja akanakupha good kuti wazindikira kuti unazungulilidwa ndi adani ,ife takulandira ,wina atsekula mmimba ndithu 😂
Aaaah iyiyi sakubisile wapala😂😂😂😂😂lozani zanu ija unakwapula aise😂😂😂
Mwapha mwene track ili bho😍😍 a opposition sangayamikire yawo ndi misonzi😭😭😭 ndipo ikanagwa mpaka 2060💪
😂😂😂😂😂😂😂 wapala man Joy aaah mwanyikatu baba
Jealous down Dan kunyimbo za ndale amapha ma hit heavy Dolo kwambili keep the fire burning Dan Lufani
WA nsanje yekha ndamene mumumva kut nyimbo yi njoipa koma the truth is yawama🤩🤩🤩
Ndipo wakazinga Maka APA Amati malilo akatuluka sabwelela😂
🤣🤣🤣🤣🙌manyi ake awawa bas gawo lake wapakulapo🤣🤣🤣🙌🙌zikundisekesa nyimboyi mpaka akut chilichose chakwera ndi chakwera🤣🤣🤣🤣
Olakwisa ndi ine kugula bundle kt ndiziva zamanyizi chipani ndi chomwechija bc DPP ❤❤
Now am following you bro💥💥💥 osat komwe unali kale kuja umakwana keep it up
Indeee iweee🔥🔥🔥🔥🔥🔥boma ndi lomweri
Ola
Zikuchita kuwonekeratu, akazi umkawaduera ndalsma aja, anakutulukira ndipo anakuwelenga, kutha kwako Dan 😂😂😂😂😂😂😂
Dan Lu wabwela booo. Boma ndilomweli sitikusintha. Odana nawewo alibe ntchito ataye anamasikini
Asaaa owo nthaw ijayo umati achoke apa ukut sachoka machende ako ndithu Dan Lu 10million nkachan asaa mwayalukat man.
Km chi nyimbo ichichi eeh wachipha🔥🔥🔥MCP boma 🔥
boma ndiloweli basi, my vote goes to Chakwera
💯💥💥Znazo zkhale poteropo km nymboy ndye ndayka pa repeat 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Adha inuyo you know how to survive 🙌😂
Am dead😂😂😂😂😂
I've never been a fun of DPP koma Lozani zanu ija inali hit. Koma iyiyi zabwino zonse. 🙌🙌🙌
Osamanyoza akuluakulu, his choice. Money is not resistable, not simple
Mbola man..simunakomzekere..dpp ndi dirlu...ndinu achisiru takutulukani..musiyedi kuimba.. production yofoila ngati iyi sindinaiwone
Ine bwanji zundibhebhera❤❤❤😂😂😂🎉🎉🎉
Apa mtima wanu waphwaaa . Mudzidandaulaso kut anthu sakupangan sapoti . This is nice business you have joined uwe wachiyao tukwete malowe panandi kwa wao . Ayiyi akaikosza wawo ya ndale yangakawa kuwa
Akatuluka nyumba sabwelelaso kkkkk😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
😂😂😂𝕦𝕜𝕒𝕥𝕙𝕒 𝕞𝕦𝕟𝕥𝕙𝕦 𝕦𝕞𝕒𝕜𝕙𝕒𝕝𝕒 𝕨𝕒𝕥𝕙𝕒 😊
Am on ur side fire aisee😂🔥
Money is good ask onesimus😂😂😂
Koma ndiye eeeee .kutha kwa shasha
Ndpo live
😂😂😂Mcp iyayi koma nyimbo ndi yokoma iyi😂🔥
Wabwera iweyo..my vote ipita kwa iye chakwera❤❤😂
fetu
iweso opusa bwanj
Oky
@@UsumaniYasidu uthin wen
The best song ever 🥳🔥
Kumenya kugwetsa kwacha kwaera🔥🔥🔥
kd simbali ya kwanu ija akudya chiteze anthu ijah 😉 comfidence its more important than money
Etiiii inu anthu ena nd ofoila too much
Iyi wayikunga bwino aise🔥🔥
Kod ujayu anaimba lozan zanu uja ndi ndan coz mawu akufufanana ndi uyuyu koma ngat ndiyemweyu 😅😅😅😅 aaaaaa iyiyi mbola man dan🤣🤣🤣🤣
Bas man idyani ndrama zamagazizo big up koma fans ndiye ikutuluka mwanyooo 😅😅
Are you sure?
Madala inuyo mmaimba bwino anthuwa alichabe udan ndi mcp, about song is very hit boss........ Big up shout out u muyao 🙌🙌
Am now following u bro keep the fire burning
Kodi sizimatheka kudilita comment yazako
Chayiphika ndipo yapsa 😂😂😂❤❤❤
Ndipo chimaganiza ichichi asee
Ndi shasha@@ZainaMussa-tj2lf
Mfundo zikuchita kukusowa 😂koma umphawi sizithu 😅awuze aloze zawo
Real definition of money can speak
All lanuages
I'm telling you😂😂😂😂😂
wachiyao wangalusa brazaaaa! boma ilooo!
BOMA iloooo🔥🔥🔥🔥
Mbola man Joy...
Odi nkavele lozani zanu ine 😅
Tulani pansi udindo on repeat
Ndlama zili pamingadi eeeee....ineso ndipase ndlmazo ndiimbe yanga 😂😂🤣🤣🤣🤣
Only legends who loves their country will like this song..... mcp fire 🔥🔥🔥
aaa nyimbo yokoma ndi Lozani zanu iyiyi simudyera bro... komabe all the best
MCP iyo 🔥🔥🔥🔥🔥💘
Dan mapaz ako ndithu 😂😂 kod mmationa ngt zitsilu zanu et 😂
Ndan akumver lozan zanu kuno ngat ine apa🔥
Wekha 😂😂😂😂
Mbambande 🔥 boma ndilomweli la MCP 🔥
Boma ndilomweli
Msiyen Dan Lu apakuleko gawo lake kwachakwela😂😂
Wow kwacha kwayela basi
Nditukwana kwinako but still DPP my vote 🔥🔥🔥🔥🔥
Ndalama inampereka yesudi....galu uyu kwabc
Oimba omvesa chisoni kwambiri
Mwapalatu apa ase ,hit ndi Lozani zanu yomwe ija bas osati izi aaaaa
Dr chakwera my Right choice enawa ndi MANYI enieni
Umwachani
Dun lu iweyo mbolo yako mwava ndipo kungobwela ku mangochi tisakusanduza mtembo muthu wako tisaumangila panjinga 😢
DPP my vote
Kujaku tabwerako,,, Maliro akatulu tabwera ....akunena ndani uyu😂😂
Business man
Koma ndiye😂😂😂😂
Bro lozani zanu Ija ndi deal 🤣🤣🤣🙌🏻
Dani lu, congratulations everyone has rughts sing ❤❤❤❤
Mupheni mesa amati ndinu ng'ona watha Dan lufani ndipo ufa ngt ena aja ,tula pansi udindo chakwera ndi iweyo
Nyimbo komano Tulani pansi udindo 😂😂😂😂😂😂 Komano ndikudziwa wayimbira matha home boy 😅😅😅😅😅😅😅
You have nailed it bro. Camp B ikumva pain. ❤❤
Zisikubeba ataaa ndalamayo yangobita pachabe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 zisikusekemela ata 😂😂😂😂
Zoonadi chakwela atangomenya kamoz chilima anamugwesadi 😂😂😂😂 dan lu pamutu pako sipanasiye kudikula😂😂😂
Dpp my vote,,iz zikundimvekela mwamanyimanyi chotcho
Dan luu naa nyimbo iyiyiii, wanyikaa heavy ndipo this song ilibe chikokaa ata oloko pang'ono
ku Dpp ko mukunva bwanji M'bebe MCP bommaaaaaaaaaaaaaaa dan lu nyimbo za ndale umaitha aise welcome to the mighty party MCP
😂 😂 Mesa amkati asiya kuimba awa kd aaaaaa
Lozani zanu ija ndi hit 🔥🔥🔥
Iyi singakhale pa repeat 😔
Lozan zanu on repeat kuno
Honest Dan lu nyimboyi wapala
Komano Bola wadyapo ndalama zako😂😂😂😂😂