This song remains one of the best campaign songs ever! I am not affiliated to any political party koma every time I hear this song I can't help but dance 🎉
A malawi tisapusitsike Dan Lu wayimba bwino koma zitukuko zose zomwezikuwoneka munyimbo anapanga ndi malemu bingu zimuwake uwutse mumtende chitukuko cha APM Chawonekapo ndi kutsengulila mwala wamaziko basi ambili mutha kundiyikila umboni komaso angoyiwala kuwonetsa majenileta chifukwa ndichitukuko cha Dpp basi a malawi tiyeni tilembetse mukalembela wazisakho 2019 kukasakha mwazelu.
Aja amanena kt chakwela sali boma pano ali boma tikuti ....... tikudikililabe ife kt aloze zawo ndi 2024 iyi kuli ziiiii ....... mmmmmm km gyz a dad omwewo 2025
Dan Lu wadya kale ndalama za Pitala chifukwa cha nyimboyi, koma pitala sakuzindikila kuti dan lu akunena iyeyo kuti aloze zake yomwe ndi ma generator ndi miseu yophotchoka. Kkkk koma Dan Lu achezele bwino apitala
I can't comment this,even Dan lu he start to sing politicians song this is enough now and too much think about it and think about your fans Dan lu who listening your song each and everyday,how they feels now?
This song remains one of the best campaign songs ever! I am not affiliated to any political party koma every time I hear this song I can't help but dance 🎉
Ur right bra
Kungoti dpp have good songs for campaign 🔥🔥🔥
Up to now lozani zanu remains one of the best campaign songs❤ who agree?
Of course it's a masterpiece koma angwazi senderani is greatest
Coming back after loosing our only hope skc😢 adad tabweraso ife Ana anu
Joni mutipukuta misosi a malawi mukubwela bho❤
Kma ichi campaign nde inaipweteka🥳🥳🔥♥️
Siine wa DPP kma ichichi chinaipweteka🔥🙌
Basitu come here to refresh my Day...🤣🤣 Koma DPP naikonda ine eh eh
Anyone still 2024 listening notify
A malawi tisapusitsike Dan Lu wayimba bwino koma zitukuko zose zomwezikuwoneka munyimbo anapanga ndi malemu bingu zimuwake uwutse mumtende chitukuko cha APM Chawonekapo ndi kutsengulila mwala wamaziko basi ambili mutha kundiyikila umboni komaso angoyiwala kuwonetsa majenileta chifukwa ndichitukuko cha Dpp basi a malawi tiyeni tilembetse mukalembela wazisakho 2019 kukasakha mwazelu.
Kkkkkkkk ndaonaso kuti zitukuko akuonetsazi zayeni
Nkhani ndiyokut inapanga DPP
Akuti DPP
Akuti isabwere Dpp
Eeee we are here to take wat belongs to us😢🎉🎉🎉🎉alozedi zawo😢🎉🎉🎉
Ndipo inu
Osafooka Dan lu we need u now campaign
This masterpiece never gets old🔥
Mulibe kanthu munyimboyi coz what I am it's all about Bingu. I think as the sounds itself akut aloze zawo, I could see Peter's works in this video..
Guy is talented...respect his hustle whether you don't agree with his opinion....
Arrangement of the song on point despite whatever 👏👏👏
The guy on 3:04 is a whole vibe! 👏🏽👏🏽😃😃😅😅❤️❤️ Great Song Dan Lu! 👏🏽👏🏽💯💯💯
Big up to Dan.music is about hustle.make money bra n grow big in music.DPP ndi boma
Danlu ulibe nzeru ukuwona ngati tikuvotera wawupoda walemba m,madzi. UTM patsogolo zinazi ndi zopanda pake , Iwe danlu ngat ufuna kuti uwine bwera ku UTM .
Yomweyo bas 🤣 😂💪💪💪🔥🔥🔥
adan uyu ndeye aaaa. kuchenjela ayi chenjelani 2b quaint is very enough 4 everything.
That ShakuShaku a beg! A bi cool like cucumber and salt!
Inde iwe❤❤2025 ddp boma❤
Watching this after seeing adad dzulo ku maliro
bro Dan LU ndinu dolo ngat siwakwathu kumangochi mwaveka a bro pa dziko lose koma MMMMMM ndale aleche wawo
This is still the best song for campaign till today 30 December 2023🎉
My late father loved this song..
DPP more fire,,,the winning team 🔥🔥🔥🔥🔥
1:53 we are here to take what belongs to us 🔥🔥🔥🔥
Today is 12 may 2024❤❤
Nyimbo iyi hit sizaguga🎉🎉
Tikadalibe pa mbuyo panu adad love u dan lu
Musatinyase a Dan lu mwangovutika mukuona ngati akuponyelani la fanta.Musavutike ovota ndi ife ndipo amalawi pano anachengela sizoika khalamba komaso mbava kapena kuti apumbwa mmipando mukhaula mkuona 2019 UTM BOMAAAAAAA
2023 we're still here
this was the best campaign song ever. Bravo Dan Lu
Nyimbo unayimenya bwino kwambiri.....
Aja amanena kt chakwela sali boma pano ali boma tikuti ....... tikudikililabe ife kt aloze zawo ndi 2024 iyi kuli ziiiii ....... mmmmmm km gyz a dad omwewo 2025
Mukutionesa zitukuko zomwe anapanga Bingu
But those development are still under dpp...it doesn't matter that its bingu or peter who built them.....dpp ndi motto!!!!!!
Izi ndi zipaso Za chipani cha DPP nanga munganene KT ndi zipaso za ulamulilo wa MCP?
Chimoto buuuu!
Dan lu akufna ponyera et zitukuko zimene akuonesa ndza bingu
wow what a nice song dan we love you ☺☺☺☺
kachaso ndiwamafilu ndipo boma livomereze kut jada ali khenge osat kumamanga anthu ogulisa kachaso chifukwa kachaso ndamene amabweresa nzeru
Dan Lu wadya kale ndalama za Pitala chifukwa cha nyimboyi, koma pitala sakuzindikila kuti dan lu akunena iyeyo kuti aloze zake yomwe ndi ma generator ndi miseu yophotchoka. Kkkk koma Dan Lu achezele bwino apitala
The best campaign song ever ♥️♥️
The best one campaigning song ever and forever
dan LU ANAPHA NYIMBOYI....EEEHHHH SALUTE
Iwe umatii 🔥🔥
Love mpaka pano 💙💙💙💙
Lovely tune🔥🔥🔥
AFUNE WINA APETAR OOOO WOYIMBAOO ASATI IWEE NDIWAMINYAMA IWE
Mmmmmm ndne wa MCP but iyiyi anaika mmm
I can't comment this,even Dan lu he start to sing politicians song this is enough now and too much think about it and think about your fans Dan lu who listening your song each and everyday,how they feels now?
ndichitsilu Dan lufan
Eat the money bra. Much respect to Bingu though...
Ine nyimbo iyiyi imandiwaza ndipo sinzasiya kuikonda
nyimbo yabwino koma sitingavotele achina Dausi chifukwa cha iwe
anthu akuba amenewa
This song is a classic!
Nice nice @Dan lu
Dan lu ndilaka umandivesa kukoma
Hit song until now 2024
Za uchitsiru basi a dan lu anthu ozindikila ngati inu kutsatira nkhalambayi
this song still hit bg up dan
E-Classic respect bro
U re there bro
#RespectAkumvapainmaster
Next year tivine basi.
Wachinyamata iwe watani kodi, ndinkayesa kut ukuona nawo mavuto tilinawowa. Shame poor mind Dan lu. Tidzalila mpaka liti kodi osaukafe
Apa Nde mwaliradi 😂😂😂
Dpp woyeee!!!!!!!
More fire😜😍😍😍😍
Masala eti
Dan lu zachamba mayambizi mupuza nazo
Dolo ka 1,000
kkkkkkkkkk stadium sanamange bingu and parliament sanamange bingu za ziiiiii otsangoti umapempha ndalama bwanji akugayire akumva pain ndi ndani apa
Hozaaaaa
❤grate🎉❤❤😊
Fadah😂🔥🔥
Dan Lu apa nde waonetsapo uchitsirutu , peter muntharika alibe chomwe wapanga dzamalemu dzimenedzo hahaha
ndale sopano mwafuse akasa manyazi pano akayima uyu manja mmwamba uyu mmwamba pano eeeeee ndevu zokha pwiiii kusowa kopita wasala iwe mphaka
Tell him idiot
Lonzani ZANU, makape inu .DPP .boma
APM my vote🔥🔥🔥🔥
Nyimbo iyi inakoma pa njamba 😂😂
Serious
Dpp bomaaaaaaaaaaaaaaaaaa
Dan Lu ndidada 2019 boma
APM my vote 💙
Uyuyu anali dada
i love the video
peter utsampatse ndalama Dan lu tsanga Ku votere ndi wa utm ameneyo akufuna akudyareni
Rooney Master akungofuna Dolla ada awa
Kkkkkk Kkkkkk zoonadi2 Koma... Coz sindikuona wachinyamata akusapota APM
Nyimbo yako ndi ya bho koma wayilakwitsa wayimbira zipan
Adad takusowani 😭😭😭😭
Zopunsa bc ulibe nzelu ndipo si ndizagulaso nyimbo yko
My lovely song
APM my vote 🔥🔥🔥 2026😂😂
if DPP is to win Malawian's will suffer than never b4 , let's open our eye's my fellow Malawian's.
🤣🤣🤣 Pano tikujoya et?
ndioooopusa iwe paliyamenti yooo ili kunyumba kwako
Mumakwana mani😅😅😅
Ife tikudikirabe kut aloze zawo . this is 2022 Koma kuli ziiiiiiiiiiiii
APM my vote
DPP moto kuti buu!!
Mbuzi
Yomweo
yapyeteka 30,000 DPP ili madzi ndi utm 2019 peter uzakomoka anyamata tonse tagwiritsana Ku votera utm bomaa
2025 boma
Best song