ACB LAPEZA KUTI BOMA LA MCP MWACHULUKA KATANGALE 🙌🙌🙌

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 3 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 45

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 дні тому +11

    Vuto la boma ili ndiloti, onse, maka MCP representatives, anali amphawi okha okha.
    Nkani pano Ali pa phwando la a kakowa

    • @Extratremendouszeus
      @Extratremendouszeus 2 дні тому

      Kodi Ku Malawi kuli Anthu oona patali ngat inuuuu...for sure its true

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 дні тому +5

    Corruption can say goodbye if only the Anti corruption bureau becomes non governmental organization

  • @RodgerChaula
    @RodgerChaula 3 дні тому +2

    Our Gorverment is lotain Asogoleli .anthu awa alibe umunthu othandiza ziko lawo

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 3 дні тому +1

    Ine ndikugwirizana zawo abambo ayambawo kuti bungweli lithe basi, likungowononga ndalama za boma.

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 3 дні тому +1

    Koma Chakwera ndi achina Chimwendo Banda akuti boma likuyenda bwino kwambiri. Eeeeeeeee! Anthu awa sadabwere kuthandiza dziko, koma kudzadya. It's a shame. Achoke basi

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo 3 дні тому +2

    Bakili mluzi TV adanena kale kuti MPC yasakaza koposa😂

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 дні тому +1

    Inu ana amahule adana naye bwanji katangale mesa bambo ao analowa kwa mao mwachinyengo😂

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 дні тому

    Katangale atha kuthesedwa ngati atsogoleri ndioopa Mulungu moonadi munthu wopana kuopa Mulungu angapange bwanji chilungamo.ziko la Malawi likusowekera atsogoleri achilungamo. Chawiri ACB isakhale yisalamulidwa ndi boma. Chachitatu kumalawi tinakula kuti ukalemera anthu azikupasa ulemu ndichimene atsogoleri akuba ndalama akufuna ulemu

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 День тому

    Bwezi akulandidwa katundu ndi ndalama zomwe akubawa bwezi kubaku kutatha koma from 1964 up to now palibe ndi modzi yemwe adalandidwapo katundu ndiye chifukwa chake kubaku zikukutha kumawalanda katundu ndi ndalama zomwe basi

  • @mathewsnachuma8086
    @mathewsnachuma8086 3 дні тому +2

    Anthu onsewa adali osauka that's why

  • @user-ni4ri2xe9e
    @user-ni4ri2xe9e 2 дні тому

    kumudzi kwathu kuno ku Malawi ndimadabwa kuti kodi bungwe limeneli la ACB likutani komanso why do we say that we have ACB yet corruption instead of coming down komano ili pa makwerelo kupita mmmwamba. mwachitsanzo passport ya MK50,000 kuti ifike mmanja mwa M'Malawi nde kuti akhala atagwiritsa ntchito makobiri opyola mk200,000. ngati otsogolera ali serious to deal with this nde kuti all juniors will be afraid.
    ndizovuta kuti katangale athe ngati otsogolera akupanga nawo.

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 дні тому +1

    ndi boma la mbava zokha zokha zakatangale ndi kupha chakwera ndi chigawenga cha kuba ndi kupha

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f 20 годин тому

    ACB yili ngati nthambi yoyima payonkha koma boma Lili NDI mphamvu kuwophyeza kuti milandu yisapite KU court.
    Waste of money KU ACB

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 дні тому

    Kodi kumalawi kuliso boma inesindikuona boma soapa ndikuona mbava

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 3 дні тому +1

    Ayi osati osaukafe koma umakhala munthu utatopa ndikuyemdera that is why umangopeleka ka deal kkkkkk koma zoona chakwera mmmm

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 3 дні тому +1

    Moti kuti munthu awadzudzule akum'manga, what type of government is this.

    • @SamJalie
      @SamJalie 2 дні тому

      Evil government full of intimidation and hypocrisy

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 3 дні тому

    Mtsogoleri sayenera kuyang'ana nkhani yakatangale ndi nkhope yachisomo ayi. Apa pokha akuyenera atchedwe kuti dictator pofuna kupereka mantha kwa onse oganizira zokachita mnchitidweu. ACB payokha singakwanitse. Komanso katundu ndi ndalama zidzibwezedwa ku thumba la boma, kuti zitumikire moyenera.

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z День тому

    Mmmm mm koma kumalawimu

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 3 дні тому

    I wish it's high time boma limayenera kuganizira zosintha malamulo athu okhuzana ndizakatangale ndikuika zilango zokhwima osakhala izi zomangoti basi abwenza ndalama ndiye takhululikira kapena akamangidwa kungokakhala Chaka chimodzi kenako aziti amachita behave bwino ndiye boma lawakhululukira, mmene tikupangira ndimilandu yogwililira kapena murder zomwe zomwezo zitabwera kukatangaleku, munthu azikakhala even 9 years alipa alimand anthu tiziopa kugwira chaboma,panopo chinthu chomwe chikutisaukitsa amalawi ochuluka ndikatqngaleyu,ine ndimaona kuti mmene tinathana ndiulamuliro wankhanza wachipani chimodzi wa MCP ndimaona ngati pamafunika pabwere Chihana kapena Muluzi wina yemwe angatimasule kusinga zomwe zatimanga kukatangale

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 2 дні тому

    Nthata za njala izi ndipo mistake yomwe tinapanga a malawi mulungu atikhululukire ndithu...

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 дні тому +1

    Ngati anabisa black box kulibwanji report ya Chilima?

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b 2 дні тому

    Ndimbamva zokha zokha zimenezo mcp anthu onse anali alimi ndie atani anthuwo akhala ali pa ulimi kwa zaka za mbili ndie asabe Mesa khotse mu mteza simukuona pamenepo kuti mbuzi aimangilila pa mbale ndie mumati ingatani Mesa kungodya mbaleyo mowonongaso ka kuti mwai umenewu suuzapezekaso ka 😂😂😂😂

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d 2 дні тому

    Katangale sangathe chifukwa ose ali m'boma akuba

  • @SamJalie
    @SamJalie 2 дні тому

    Kupeza apeza nanga akupangapo chiyani pofuna kuthana ndi katangale?

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 2 дні тому

    Katangale kuthi athe ndi mopweka vuto mukumasakaniza ndi school opezeka wapanga katangale asamangidwe koma amenyedwe paulu kumumangilila pa bwalo athu akuona athu atha kusiya

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 3 дні тому

    Chakwela you mast go

  • @bornface4786
    @bornface4786 2 дні тому

    Katenga okhoza kutha ndinthu komano anthu akupanga dala chifukwa choti malamulo anthu Ali so week let's we say titati tipange lamulo loti aliyense ogwira ntchito m,boma akapezeka ndi mulandu wakatangale azipatsidwa ban kuti sazagwiranso ntchito m,boma mpaka kalekale. Ndithu vuto limeneli likhoza kutha ndithu

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 2 дні тому

    Pakufunika kusintha malamuro ena ya dziko lino, munthu akapezeka ndkatangale anyongedwe bas mzaona kuti katangale wayamba kusika chifukwa anthu azawopa kufa, komaso acb ithesedwe chifukwa palibe chimene ikuchita.

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw День тому

    Basi tu kusazikana kumeneku achakwera muusiya mpando bola tiwone amanganya wo

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f 20 годин тому

    ACB is useless
    Atsogoleri kuyambira 1994 akhala akuba ndalama koma milandu yawo siyithera Kuma khoti.
    Ndiye justice system NDI useless chifukwa amavomera kutseka milandu popanda chigamu

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni 2 дні тому

    Cover the boss

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p 2 дні тому

    Chakwera must go

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 2 дні тому

    Ife izizi tatopa nazo ameyo achoke basi. Chifukwa mmutu mwake mwadzadza mamina.

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 3 дні тому

    So sad💔💔

  • @user-xs3pk1vp8i
    @user-xs3pk1vp8i 2 дні тому

    Mabodza okhaokha

  • @PatrickMulangala-os4by
    @PatrickMulangala-os4by 2 дні тому

    Achoke

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx 2 дні тому

    katangale m'malawi mkovuta kutha chifukwa president ndi nduna amapatsidwa mphavu zambiri so mkovuta kut zinthu zina zikomzeke m'malawi muno

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 3 дні тому

    Pali boma limene lingabwere lopanda katangale palibe chachilendo zidalipo kaleso

    • @GospelSoldiers-sr7np
      @GospelSoldiers-sr7np 3 дні тому +1

      Bwana apa zawonjedza koma inu muli dziko liti....tatiyeni. Tizimvako chisoni plz plz

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 3 дні тому

      @@GospelSoldiers-sr7np mpata ulipo ositha boma koma musaganize kuti mavuto amene alipowo angathe

  • @user-pl2lj6mh1z
    @user-pl2lj6mh1z День тому

    Tingovomela mavuto kumalawi