BON KALINDO LERO PA 15 DECEMBER AKUTI COMMISSION OF INQUIRY YANU YAUCHISIRUYO ISAMUKHUNZE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 137

  • @OwenMindozo
    @OwenMindozo Місяць тому +1

    Bon Kalindo sir, God is on our side, may good Lord gives you health life. You are speaking on behalf of ordinary people in Malawi

  • @ChristinaChauwa-c6w
    @ChristinaChauwa-c6w Місяць тому +6

    Ambuye gwira ntchito yanu

  • @ChisomoYosefe
    @ChisomoYosefe Місяць тому +6

    aAkunena kut chakwera samadziwa kut SKC akupita kumaliro nanga ndalama ya chipepeso imene anatenga aVP yokapepesera maliro a kasambala 5 million chakwera anali asakudziwa akunena zoona koma chakwera Mulungu kumwamba alipo ndipo chilichonse chobisika chidzabwera poyera ukhoza kuzemba pamsi pano kaya kwa anthu koma kwa Jehovah yekha sitingazembe😢😢😢

  • @APOSTLEBJ-tc5fp
    @APOSTLEBJ-tc5fp Місяць тому +6

    Zachisoni ndizakuti ma pastors womwe amayembekezeledwa kuti ayima pa chilungamo chikwa chakumuwopa mulungu atengeka ndi dyera la ndalama.

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda Місяць тому +4

    Kalindo ndi wanzelu akutimenyela nkhondo osaukafe

  • @VeraChirwa-c5n
    @VeraChirwa-c5n Місяць тому +1

    Yomweyo DC ipatse 🔥🔥

  • @DouglasChimbiya-p7u
    @DouglasChimbiya-p7u Місяць тому

    One day is one day and that day is coming....Lord have mercy

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e Місяць тому

    The D.C. God be with you ❤❤❤❤

  • @ChimwemweChibisa-q3f
    @ChimwemweChibisa-q3f Місяць тому

    Angoonongapo ndalama zathuzo

  • @MphatsoGuzani
    @MphatsoGuzani Місяць тому

    🎉 Umakwan mfumu

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d Місяць тому

    The Dc 🎉🎉🎉🎉 muma tiyimilila kwambili

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo Місяць тому +3

    A yehova nikolen kumulomo ndine mama waumanyano let God handle this the truth shall set us free may their souls rest in peace

    • @tiongehezron
      @tiongehezron Місяць тому

      Wamkoleni ku mlomo kukana kupalamula 😂😂😂😂😂

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane Місяць тому

    Katengo kakang'ono kakafupi kamanganya kkkķkkk kagwesadi kkkk

  • @MphatsoLichapa
    @MphatsoLichapa Місяць тому +2

    May the Good Lord punish all the witchcraft government.

  • @EvanceHorresie
    @EvanceHorresie Місяць тому

    Machine bon kalindo ndiwe mphangala umakwana

  • @MadalitsoPonchi-m1b
    @MadalitsoPonchi-m1b Місяць тому +2

    Agalu awawa arikwana azipita bàs a2 okupha awa

  • @WillyNyirenda-l7h
    @WillyNyirenda-l7h Місяць тому

    A Msonda amvesere zime e akunena Bon Kalindo. Msonda a very bright man but stoops too low.

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Місяць тому +1

    Tikukavota next yr choke akanya oipawa

  • @ShideNelson
    @ShideNelson Місяць тому +3

    Ma ulosi akukwanilitsidwa monga momwe mabuku adanenera

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo Місяць тому +1

    Akutitenga ife opepera

    • @LOKAMJ
      @LOKAMJ Місяць тому

      Ndipo kwambiri,,akutiona kugona

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate Місяць тому

    ❤❤❤❤Dc

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 Місяць тому

    Anafa uyu Basi kunapita

  • @ThoccoMakiyi-q3l
    @ThoccoMakiyi-q3l Місяць тому

    Inuo pachilungamo munabwera

  • @ZainabHajj-q9d
    @ZainabHajj-q9d Місяць тому

    ❤🎉

  • @IbrahimDailes-j6y
    @IbrahimDailes-j6y Місяць тому

    Tisaname chakwele ndi boma lako wafika pokwana mwatitopetsa srs chokani apitiliza asilikali kwatsalaku apite kumene ndipo ambili tingaphe mbuzitu kkkkk😅

  • @Esther-t4l
    @Esther-t4l Місяць тому

    Malawi wathuu eeeeesh

  • @BridgetNtambalika
    @BridgetNtambalika Місяць тому +2

    Chakwera ambuye amukhuze ndipo achite naye

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Місяць тому +2

    Chilungamo tikuchidziwatu kuti anapha chilima ndi chakwera, palibe choposela apapa

  • @jezalakaphuka7325
    @jezalakaphuka7325 Місяць тому

    Koma pakuti president sanadziwe kuti VP wabwrako kunja muripoti sangayikemo...... Pokha pokha ngati opereka repoti analedzera. Report la ndege ndi kubwera kwa VP from Korea sizikugwirizana

  • @collengoma6542
    @collengoma6542 Місяць тому +4

    ambiri azathawa mu Malawi pano alitenga dziko lathu ngati ndi mkazi wawo azipanga mumene akufunira koma Mulungu ndiwowopsa kwambiri 2025 aziwona

  • @JumaEriya
    @JumaEriya Місяць тому +1

    Zonse akudziwa ndi murungu.roko atabisa maka Chotani koma nzinzawururika bas.ambuye wamwambayo

  • @JosephKwimbayan
    @JosephKwimbayan Місяць тому

    Ndipo live

  • @AbsalomKambova
    @AbsalomKambova Місяць тому

    Ndipo machende awo onse amene amapanga inquiry panyapanu nonse

  • @OwenNyambose
    @OwenNyambose Місяць тому +1

    The DC mwana opsa kwambiri

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf Місяць тому

    The DC , consider to contest as presidential candidate officially. I know you are a president already. Make sure to include the well known activists + Malawi sons and daughters of good will in your administration. I know there are good people here who can transform Malawi within 5 years, just like the way Ibrahim Traore is doing in Burkina Faso. Please, take this into account.

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Місяць тому

    A day is coming, komanso la ma albino.

  • @ChrispinSakhama-m8s
    @ChrispinSakhama-m8s Місяць тому

    Hahahah koma bon Kalindo

  • @MphatsoLoya-m2k
    @MphatsoLoya-m2k Місяць тому

    Truth will be known one day

  • @GladysMagadi
    @GladysMagadi Місяць тому

    Tunduwanji wa anthu😅😅😅😅😅

  • @NoelBurton-x1z
    @NoelBurton-x1z Місяць тому +3

    Boooon kaliiindooo the DC

  • @AhmedJali-xf3rw
    @AhmedJali-xf3rw Місяць тому +1

    Munali mgulu lobweresa mavuto dziko muno mumangoona kuwasokosa anthu

  • @cossaphyxo
    @cossaphyxo Місяць тому

    The DC

  • @RoseJoyful
    @RoseJoyful Місяць тому

    Mulungu akuyendereni ndithu inu oyendesa Boma tsiku lina muzayaluka tiyeni tipephere mwa mphamvu palibe WA muyaya mwina osafika tsiku la mavotelo

  • @DippedJob
    @DippedJob Місяць тому

    Akuti bwanji mwatenga nthawi osandimanga kkkkkkkkk anampa gwenembe

  • @AustenMapoto
    @AustenMapoto Місяць тому

    Oyees DC time is coming

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Місяць тому

    Mmene wangoti sikusinja basi ndi manganya aphanako anthu aja kkkkkkkk

  • @Donvaga
    @Donvaga Місяць тому

    Zokhudza kwambili but anyway tose tikupita komweko 😢

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni Місяць тому

    😢 Chakwera becareful ndiChirima. Athu amene munafufuza inquiry iyi mboro zamanu mwamva, machende any opanda madzi

  • @AwlysHussain
    @AwlysHussain Місяць тому

    Only God knows one day he will answer this issue

  • @James9t.r
    @James9t.r Місяць тому

    Ndye mwat katengo kakafupi😂😂😂

  • @MathewsMbaluko
    @MathewsMbaluko Місяць тому

    Koma winiko ,kantengo Kajang,Ono 😅😅😅

  • @ShillaShamil-v2y
    @ShillaShamil-v2y Місяць тому

    Mulungu akudziwa chiri chonse

  • @KondwaniChaponga
    @KondwaniChaponga Місяць тому

    Kodi anthu oyamba kufika pa Malo a ngozi anali ndani? Ndipo Kodi black box yili kuti?

  • @TalentGarage
    @TalentGarage Місяць тому

    Mtu gwa ngati nazikambe hay powona zimabwera mfon koma born kalindo sikufuna kukuwona mfon yanga

  • @ZelinaMchenga
    @ZelinaMchenga Місяць тому

    Agalu amenewa afikapo komatu Mulungu akuona adzayankha

  • @HappyBigWaterfall-xt1mn
    @HappyBigWaterfall-xt1mn Місяць тому

    Kwachema kumalaw

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f Місяць тому

    Kamtengo kakafupi😂😂😂😂😂

  • @KondwaniMaganga-v4d
    @KondwaniMaganga-v4d Місяць тому

    Zoonadi the DC, otsutsa boma Ali mtulo

  • @TapiwaBlack
    @TapiwaBlack Місяць тому

    The dc

  • @HarryignacioGazamwalak-h8r
    @HarryignacioGazamwalak-h8r Місяць тому

    kantengo kakafipi ndie kat koma

  • @MosesTangwe-q8o
    @MosesTangwe-q8o Місяць тому +2

    Chakwera ndi Richard chimwendo tsiku likubwera limene mizachimine ndipo muzayankha agalu inu

  • @UniceSauli
    @UniceSauli Місяць тому

    Iwe umati ndiwe wamalawi first osatulusa rako bwanji patumbo pamako uma dinyasa chichende chako

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji Місяць тому

    Very sad😢😢

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d Місяць тому

    Siku sinja sikusinja koma ku mcp tiwona zinthu paja kalindo amakhala ngati wamisala koma amanena zowona ndi makumbukila odeo Ina yake malemu chilima asana mwalile adanena zoti chakwela ndi chilima akupusitsana wokhawokha pano alikuti biyeni ngati tikumbukila bwino SCk adali ndi milando boma la mcp lidango thetsa milandu ya biyeni uku akumu sewela mamafiya bwa pano alikuti adamuputsetsa wagwa mtengo ndiye zinazi nama dram Yu akama kamba akhala mission yose wa iwonela patali kwambili

  • @vittazomba
    @vittazomba Місяць тому

    Kkkkkkkkk koma lero kwachema ambwiye akwiye koma zitondikomera kwabasi

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu Місяць тому

    Koma boma ili eshiii tikangova tiwonana 2025

  • @Maryjafa
    @Maryjafa Місяць тому +1

    Chakwela chimwendo kamajekete ndiomwe anapha chilima

  • @TadalaBirsonkanjanga
    @TadalaBirsonkanjanga Місяць тому

    Awapasa ndalama kuti afufuze zonama

  • @RosebbySitingaMfarinya
    @RosebbySitingaMfarinya Місяць тому

    Iwowa akhoza kubisa lero koma adziwe kuti chauta anona choona chake tsiku lomwe lika ndiye akungofina .kutinamiza.ndi zoposa zawozo koma Mulungu alipo ndithu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Місяць тому

    kantengo kameka ndiye kati

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane Місяць тому

    We don't need lawyers next year, aliyense adzayankhe yekha

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya Місяць тому

    Za report imeneyo kauzeni azimbuyanu, zibwezi zanu, azikazanu ndi azibale Anu not malawians yathu tizapanga mukachopa pampando chifukwa mukutitenga ngati amalawi mitu yathu sikugwira misaone ngati ngati mwachenjera zopusa zanuzo Mulungu akuona.

  • @LilPex-y3l
    @LilPex-y3l Місяць тому

    Kkkkkkk hahahaha bon walutsa

  • @PaulManyamba
    @PaulManyamba Місяць тому

    Panopa kulilongwe kuno akumagula 10 pin pano mavuto kwambili

  • @Muhammadshib
    @Muhammadshib Місяць тому

    😢😢😢😢😢

  • @MatthewBanda-g1v
    @MatthewBanda-g1v Місяць тому +1

    Mr kalindo, ing'aluleni basi.

  • @stormchatepa134
    @stormchatepa134 Місяць тому

    Nyo

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo Місяць тому +1

    Koma kuopposition nkumandadi eti. Tangobweretsani report lanu basi

  • @WilliousNyirongo
    @WilliousNyirongo Місяць тому

    Palibe wabwino apa,zonenena zanu zikuonetsa kut nonse ndinu zigawenga koma nthawwi ikubwera you wil face the righteous judge & you will be.accountable for every thing you do or say.

  • @WinnieJalasi
    @WinnieJalasi Місяць тому

    Kodi mesa chi tower cha tnm chimapanga record chili Chirichonse? Macra chimozi moziso nde sakulankhulapo kanrhu bwanji nde bola akanapanda kulengeza zosatira za ka fuku fuku

  • @MadalitsoMlogera
    @MadalitsoMlogera Місяць тому +1

    😂the DC mwana wachaaabe kwabasi 🙌🏼🙌🏼🙌🏼

  • @PaulMhango-x3q
    @PaulMhango-x3q Місяць тому

    Yatsala inguary ya ifa zama Albino Njaunju Buleya and area 24 Anthony

  • @AtupereSadiki
    @AtupereSadiki Місяць тому

    Ndi report yopusadi ndipo bola akanagosiya zopepera basi

    • @LOKAMJ
      @LOKAMJ Місяць тому

      Ndipo angoononga chabe ndalama zabomazo,

  • @william51448
    @william51448 Місяць тому

    Amalawi

  • @Lanjuzi
    @Lanjuzi Місяць тому

    Kalindo pita kapange yako commission of inquiry. Wasowa m'ndowero iwe🤣🤣🤣🤣🤣

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Місяць тому +1

      Next year chilungamo chonse chizabwera poyera zedi ndipo a MCP azakhaula koposa

  • @AustinTwaya
    @AustinTwaya Місяць тому

    Anangofuna kupezera powonongera ndalama osati Za inquiry
    Anthu oipa asatanic agalu afiti

  • @LiahRestoration
    @LiahRestoration Місяць тому

    Dziko la Malawi muli aneneri ambiri mbiri modzi wa Iwo ndine im'fa ya chilima mulungu anatiuza kale kale chilimayo Ali moyo. Shame on mcp 👹

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i Місяць тому

    Alick chamba ngati ukutukwana DC iwenso panyoo pako ndi cikangawa wako yemweo.ife timadziwa kuti lipoti likhala manyaka ndizi.onse amene anali mu imkwayale imeneyi kuphatikizapo cikangawa panya panu nonse kuphatikizapo Anabelo ndi nsambo panyampawonso conde uthengawu muwatumizile.

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick Місяць тому

    Chakwera anapha yekha anthuwa dziko lonse lapansi likudziwa kale

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO Місяць тому

    Ndipo ma steps amatsatidwa pa kafukufuku ameneyu aaaa bolanso anakawapatsa ma student a Polytechnic ndi Chanco a Second year. In another ways anakawapatsa a university of Malawi period!

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j Місяць тому

    Xpamene ndadabwa ndi pomaliza akuti aimbe mlandu athu amene ankajambula ndi amene ankagenda ku tcheu koma akufuna kuakwiyisa a malawi

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Місяць тому

      Nanga chinawapha anthu mmwambamo ndi chani??? Ndipo black box ilikutiko? Nanga anamuuza Chimwendo kuti yadzadza ndi ndani? Nanga zovala anavala anthuwa sizinapezekeyi zilikwaniko?

  • @MableNeliyo
    @MableNeliyo Місяць тому +1

    Ati mumabala mwaomwalirawo munadzadza mafuta andenge,atianthuwa sanatulutse magasi ati anavulalira mkati kamba kamphepo mmmmmmmm koma inu achakwera ndigulu lanu mukamanama mptisimkutsutsikai ?mkunama poti palibepo mubalewanu paanthu anatisiya aja mpake mkunamiza anthu,koma ife chirungamo tinachidzowa kale olo tsiku lomwe munkalengeza zoti atisiya anthu onse analimndege nkhope imachita kuonetseratu kuti mwachitakukonza.Akubanja akumva bwanji pazomwe mkunamazi?mmmmmmm

  • @trizamgomezulu-td5fr
    @trizamgomezulu-td5fr Місяць тому

    😂😂😂😂😂

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Місяць тому +2

    Ndiponso bola akanangosiya osayankhula koma zomwe zayankhulidwazi mm anthu awawa ndi mbuzi zawanthu

  • @KumbukaniKadzuwa
    @KumbukaniKadzuwa Місяць тому

    Kantengo kakafupi kakutenga ulamuliro ndiye ndani manganya? kkkkk

  • @OscarKathumba
    @OscarKathumba Місяць тому

    Kalindo tulutsa yako report unene iwe adapha chilima,,,

  • @MatthewBanda-g1v
    @MatthewBanda-g1v Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉😢

  • @KhumboPhomboniChakununkha
    @KhumboPhomboniChakununkha Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ZaoMaster-c7v
    @ZaoMaster-c7v Місяць тому

    Munali kuti osakapereka umboni muja amaitanira,,,,mabodza onse mmanena aja you can't bring evidence,,

  • @thomasthomson-rn5ch
    @thomasthomson-rn5ch Місяць тому +1

    Angodya ndalama zaulere nanga ka report ko angamve ndani