Mr comrade Namiwa I salute u let me tell u this anthu onse amene anatengapo mbali popha anthu onse aja mizimu yakwiya. Ndipo zikilani kut amalawi siana ai ndi chachiziwikile kut munawapha ndipo ndi choncho nthawi yasala pang'ono kut muonekele pambalambanda muzayankha
I understand the guy does not mean someone was tampered with those bodies but,,,,he who mismanaging the situation,,,must be held accountably ❤❤❤we salute for madhala
tingodikira adad akawina mu September mu azaika commission of inquiry yovomerezeka ndipo onse omwe adachita upandu umenewu , adamangidwa simple koma agalu awawa akubisa chilungamo , time will come
Kunkuyu anati black box ilipo ndipo yasungidwa pabwino and kunkuyu nkhani Blackbox sayankhapo always,but Malawians really need Blackbox although MCP ndi ma Shasha akhiza kysinthusa Blackbox
And also commissioners of inquiry ya Martha Chizuma azamangwidenso Chakwela akachoka pampando chifukwa anapanganso za chibwana posayankha mafunso ofunikila.
Long live Namiwa🇲🇼🔥🔥🔥
Namiwa amakwana kwabmili. Ndipo akune ndi zoonad kwabmili 🔥🔥💪💪🙏🙏
Thank you Mr. Namiwa and Malawians for your diligence on this matter. Let justice reign.
Mr Namiwa you give us hope for a better Malawi. Aluta continuea✊🏾💪🏾🇲🇼
True son of the soil🇲🇼. We are fixing the country this time
Mr comrade Namiwa I salute u let me tell u this anthu onse amene anatengapo mbali popha anthu onse aja mizimu yakwiya. Ndipo zikilani kut amalawi siana ai ndi chachiziwikile kut munawapha ndipo ndi choncho nthawi yasala pang'ono kut muonekele pambalambanda muzayankha
Namiwa uja osamuphwekesa ndakatundu💪🤸🏽♂️🏋️
Our voice of reason Mr. Namiwa thank you. Tizingofa ngati nchenche, we are setting a precedence. Never again Boma Lankanza. Boma lo nama.😡👹☠️💀
Amalawi please let's support this guy, nkhondoyi siya Namiwa koma amalawi tonse
I understand the guy does not mean someone was tampered with those bodies but,,,,he who mismanaging the situation,,,must be held accountably ❤❤❤we salute for madhala
We are looking for justice ✊
Koma apa mabwana sizamasewela🎉
Isaac ataba madalitso aJacob inu Mulungu chilungamo munachionetsa kt anaba ndi Isaac. Kaini atapha m'bale wake Abel chilungamonso munachionetsa poyera ngakhale kaini amkakana.Mose ataphanso munthu ndi kumukwilira mu mchenga chilungamonso munachionetsa.Sikusinja atapha Gwenembe, munakatuma ka mbalame kaja kut kakayiimbe nyimbo yachilungamo yodziwitsa za imfa ya sikusinja. Kambalame kajatu kamakumanaru ndi deya zipatso, mbozi koma sikanayime kt kadye mpaka kukanena za imfa. Leronso ndipemphero langa kuti amene mwawatumawa kut akhale patsogolo pa Malawi kufufuza za imfa ya SKC mwadekhetse mitima 25:01 kut asalandire ndalama kufikira chilungamo chitadziwika kut Malawi 🇲🇼 wathu akhale okoma.Amen.
Namiwa amakhwana keep on fighting for Malawians
Ndare basi...pa Malawi
Chakwera ndi mbuuuzi kwabasi ndipo MCP kutuluka muboma believe me sizalowaso muboma
Iyi ikather kuwaya
Exactly
Kukuyu amaoneka ngt ofatsa bwanji
KuMalawi kuno achilima alipo anbiri
Iweyo ndi katundu
Wait for the final report
Zodiac nde ayitu,inatha
Justice is coming 😢
Shame of highest order. Thembelero o empa yoomwene wa Muwella.
tingodikira adad akawina mu September mu azaika commission of inquiry yovomerezeka ndipo onse omwe adachita upandu umenewu , adamangidwa simple koma agalu awawa akubisa chilungamo , time will come
Anamwiwa munabwera inu kuzakhala
Standup Malawi, how can these lies continue in 2025? That we loose Malawians and just look the other way. A whole vice President. Smh😢
Black box atulutse kodi akusunga ndindani abale koma ambuye atithandize chowona chidziwike
Kunkuyu anati black box ilipo ndipo yasungidwa pabwino and kunkuyu nkhani Blackbox sayankhapo always,but Malawians really need Blackbox although MCP ndi ma Shasha akhiza kysinthusa Blackbox
Kkkkk atipatsa ndie akuisunga kut ndiyake😢😢
Namiwa ndamutaila ka ntengo
And also commissioners of inquiry ya Martha Chizuma azamangwidenso Chakwela akachoka pampando chifukwa anapanganso za chibwana posayankha mafunso ofunikila.
enaso osakusa kumene
Kkkkkkkkkk akut paja mwayamba kupatsana maina kut ena ndafarao
Namiwa ulemu wanu mulungu anakupasani zelu
Anamiwa kuima pachilungamo ngati bishop nsusa
Nde ngat asachose ife ngat Malawi titan naye chichakwelacho
Kodi osafunsa ma expert a aviation bwanji?
Anagulidwa kale ndi ndalama zamagazi Za MCP Aaviation
Ma expert anakanika ntchito pano ti user manual bro
@@JacobMsukwa-q6v vuto lagona poti mufuna report linene zomwe mukufuna osati zomwe zinachitika.
Awowo awonetsa umbuli wawo paza mayendedwe a ndege. Akanapanga research kuti akhale ndi basis yabwino.
Anthu otumidwa awa!