if what he wishes done at the visited companies is what he does at his own company, bravo but if he mistreats employees at his own company kumenekuti kukhaladi kushayina. Otherwise, this is commendable.
Kumbali ya anthu omwe sanalembedwewo amayera kuti awapasa mwayi cz malamulowo anapanga ndi amalawi omwewo komanso mzipanimo onse akufuna kuti a mec alole anthu kuti alembese despite boma lolamula sonu mkamati malamulo anapanga ku parliament nanga bwanji sakufuna kumva za zolankhula za a modzi mwa anthu aku parliament, nkani anthu a kunena kuti this election is forged cz a mec akufuna kutenga lamulo into their hands ndipo they don't want to listen kwa omwe anapanga malamulo, kodi akalora kuti alembese anthu chomwe angaludze a mec ndichani
I like this program keep it up
Watching from Pretoria....u guys ur the best ❤❤❤❤❤
Watching from Johannesburg
Am always watching you guys,,,you always talking the points,,,Obert watching from South Africa,,,,Capetown
Watching from krugersdorp south Africa
Watching from joburg... Wishing you all the best guyz
We like so much my brother and sisters ❤️
Watching from Chicago
I like this program
Mumatiimilira keep it up 🔥🔥🔥🔥🔥
Bravo Mumba, Inu a MCP ntchito yanu ndi imeneyi munakatere poyamba paja bwezi tili patali,koma guys
Watching from Johannesburg RSA. Ndikunyadilani
Bravo......Mr man thawi zonse ife timaonera kuti tizimvanao
Plogram yokoma keep it up guys
Great work.Keep it up guys.Following from Johannesburg.
Paja Ibrahim Traore ndi Burkina Faso leader osati Guinea tikonze pamenepo.
🔥 🔥
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Bravo guys
Timaikondad gwede gwede
Very good selina and Steve banda
Even ifenso kuno ku Mozambique timaikonda program ya gwede gwede pitilizani
Anthu sakutulukatu .... Zikuoneka zovotazi kukhala zopanda ntchito
I agree with you a malawi ena sakukondwa nazo.. because some malawians do not love this country
More 🔥 gwedegwede
Bravo Selina n Steve
Mumalwana guys
zoonad nduna zina sizikukundwa ndipo zikudana naye kwambiri koma apitilize kutimenyera nkhondo ife a Malawi 🇲🇼
Izi ndizoona kuntchito kopanda mtendere mmmm sikwabwino umapita mkhawa ili biiiii anduna akugwira ntchito yabwino
Anthu munandmvetsa kukoma, ndpo musamasowe
Akuti zayambika kale nduna zina zaulesi zikukamba izi ndi izi, kuzolowera kudya zaulele.
Nice
Kankhanthani guys mumba is the right person paudindo wake and enawa angokula zimimba koma palibe chomwe akuchita angokhala pzende
Sowons
Eeya tilipo ambiri ndipo mumatiyimirira
It means u are standings in honest
Inenso kuno ku Pretoria ndimaikonda
Komaditu athuinuyo ifeyo timakutsatilan kuno kusouth Africa ulem wanu guys
Mumatiimilira a Steve ndi selina
Inuyo ndye mmakwana
if what he wishes done at the visited companies is what he does at his own company, bravo but if he mistreats employees at his own company kumenekuti kukhaladi kushayina. Otherwise, this is commendable.
Ndipo timaikondadi
Ifeso kuno ku USA timaikonda Gwede Gwede
Kumbali ya anthu omwe sanalembedwewo amayera kuti awapasa mwayi cz malamulowo anapanga ndi amalawi omwewo komanso mzipanimo onse akufuna kuti a mec alole anthu kuti alembese despite boma lolamula sonu mkamati malamulo anapanga ku parliament nanga bwanji sakufuna kumva za zolankhula za a modzi mwa anthu aku parliament, nkani anthu a kunena kuti this election is forged cz a mec akufuna kutenga lamulo into their hands ndipo they don't want to listen kwa omwe anapanga malamulo, kodi akalora kuti alembese anthu chomwe angaludze a mec ndichani
Timakunyadilan
Mibawa mumakwana
ngati safuna kuti ajambulidwe nanga bwanji nthawi yazoperekapeleka ikafika amajambulidwa
Mwayamba kusithadi Justina ndi kale
Guys tikukunyadirni popanga ntchito yotamandika yomwe mkupanga ndipo tikuti pitir8zani monga kuno ku South Africa timakunyadirani kwambiri
Muwauze a nduna muyenderetso muma bank umu kkkkkk
Inuyo ɓàmbò Steve ndimunthu olimmtìma ndipo simuop amakwiya ndi mfiti.
Adzikati atibela kkk mcp imamwazana kumene kkkk
Zoona timayikonda
Mumatha inu