Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
I concur with you comrade, palibenso pa ma candidate onse amene angathandize dzikoli than Kabambe honestly
Koma tifune, tisafune dpp ndiyomwe ikubwela kulamulira dzikoli idzidzi nde timvomeleze dpp inamanga maziko paliponse mmalawi muno bingu anayika maziko olimba kwambiri ku dpp.Mcp ikuganiza kuti akamanga a dpp nde kuti awina akudzinyenga ndi chala APM wawina kale utm ili pa no 2, udf 3, mcp 4 kusonyeza kuti chikangawa palibe cake adzingopakila wakukasiya 💙💙💙💙💙💙boma!
Wotching from kenya, chikangawa watikwana kwambiri tikumuwona ngati manye enieni
Dpp my vote mcp no
Mr Lwara good point what you are talking God bless you
DK is the best
Happy birthday to our comrade Lwala
Good speaker..DK2025
Happy birthday to u samuwell❤
Kodi mukuona zimene zinachitika ku kenya mutegelepo phunziro maiko amene anabela ma voti sitikufuna kuti kwathu kuno zichitikenso tili ndi ana odwala
Anthu akuyikonda dpp pa kusiyanitsa umoyo wa tsiku ndi tsiku mitengo ya zinthu tsono tione zinayu anthu sakumufuna kabambe kuti alamulire apange gwilizano ndi dpp APM amusiyira udindo thats it.
Iweyo ndiweso onama chitsiru kabambe sangalamule Iweyo ukufuna kabambe wakoyo dpp ili bwino kwambiri
Takulandilan kuti mwabwela wankhulu
AKUGULANI BAMBO
ndipo apakile anyamuke Palibe chimene akupanga ine yo ndi wa kulilongwe komwe kuno zinthu sizili bwino ayi pa ground pano sizili bhooooo